Barbarism in Malawi army: A minority tarnishing the image of the MDF

MDF

Soldiers in Blantyre have severely beaten a civilian whom they accused of pummeling one of the soldiers.

According to reports, the civilian who resides in Chilobwe beat up the military officer at a drinking joint on Saturday.

The disfigured soldier then went to Chichiri camp where he somehow convinced his fellow soldiers that beating the Chilobwe resident was a good idea.

MDFJust as they would when going for battle, the military officers on Sunday boarded their dreaded Tata Truck and went looking for the soldier beater.

They found the person and took him to Chichiri camp where they heavily beat him.

When they decided that it was enough, the soldiers took the man to Chilobwe Police and told the cops that he was a suspect who was caught beating a soldier.

But the law enforcers refused to keep the civilian fearing that he may die at the police station.

As we published the story, the soldiers had taken the man to Limbe Police.

Advertisement

228 Comments

 1. Being a civilian siumunthu palimumafuna ma civilian ena amaganiza pamene enanu ndinu mbalame za anthu ndithu mungonena osaganiza mumafuna muzitilowa mchala ndipo ukulankhula zoduka mutuwe uleketu once kuzakupeza uzasimba zoona anthu tikuvutika ku dziko laweni kuno chifukwa chainu muzikanyanso mwana anthu osayamika inu muzatifuna chikazatuluka ballow ku malawi

 2. Aonetseni kuti ununso munali Ku xool zopusa zimene mwayambazo vuto nchani ngati achepa malipilo zisakhuze anthu odya mbewa ndima grasshopper galu MDF menyani njala osati anthu osadya

 3. Kodi anakakhala kuti Munthu yemwe anamenya soldier yo wamenya m’bale wanu inu mukanatilanda?Inu mukunena ma soldier inu kodi anayamba a kumenyaniko musanawayambe? Sometimes wen u tlk muziganiza mwamva.lets respect dis pple they are doing a gud job.Ndipo ma Soldier osasiya kukhaulitsa onse opanda mwano ndi owononga mitengo. We love u vry much

 4. Zoopusa Basi ! Kod Tiziopa Gululo; Ngat Muli Madolo Bwanj Osatisakila Amene Akupha Azibale Athu Achi Albino, Ndye Mudzilimbana Mkumenya Anthu Mesa Munalumbila Kut Mudzidzatilondera Ndye Mwayamba Chani

 5. These Soldiers desire to be removed from their position. How can they take law in their own hands, no one is above the law .The very same citizen they are beating are the ones who pay tax for them to get paid.Being a soldier does not mean you are superior that anyone. They are damaging the name of the country and the reputation of other soldiers who are there to serve the nation.
  Shame on them they must be prisoner at Maula prison and use their energy to do hard labour .
  Ministry of justice should take charge of this, we cannot leave in fear of the people who are employed to protects us.

 6. Ur busy camparing mdf with USA soldiers,dont u know that war is too expensive? You cant win it without enough resources. Our MDF is full of world class soldiers if u dont know. Our soldiers are the best in the world. But what matters is resources.. Don’t 4get that it is only fire that can stop fire

 7. the problem of most of our soldiers they never been at war since they came from trainning! they are trying to show their powers on civilians? I thought soldiers and police are protecters to civilian citizens? zinatha kale zoti nsilikali mmodzi akapanga misbehave namenyedwa pamatchansi kuchilinde kamba komwa mowa wa eni, inu nkumakabwela ndi ma tata 47 odzadza nkumazalimbana ndimudzi onse?

 8. Ife tikudziwa kuti ku America nkomwe kuli asilikali eni eni. Ku Malawi muli ndi ma jets angati? nanga Special forces, nanga battle ships? muli ndi ma satelite nanga nuclear weapons? munayamba mwamva kuti aku American abwera kuti mudzawaphunzitse kuchita detonate mabomba? Guns,bombs,tanks,vehicles,uniform made in USA, even support and command from azungu through UN. Mozambique kuchita detain boat, kuotcha ma truck a Malawi. TZ kuopseza pa Lake Malawi. Inu mukutibula ma civilians

 9. soldier akakhala savage akafika pamowa amafuna aliyense amudziwe koma aliponso ena ozindikila chikhalidwe akafika pamowa sungabziwe kuti ndi soldier,komanso omwe amatengana kukabwezela nzawo akamenyedwa kumowa amakhala opelewela m’maganizo.

 10. Asikali adziko lino kwambili chimene chimawavuta ndi umbuli, mutha kundikhulupilira amene geri yamukanika amathamangira ku usilikali, Munthu amene amumenyayo amamenyana ndi nzake ku mowa yemwe nzakeyo m’bale wake ndi msilikali, ndiye anakamema anzake nkuzamumenya kumutenga atasamba magazi, nkhani zoti nzakumowa, kodi anthu amene ali ndi abale awo ku usilikari wa aziputa dala anzawo pomadalira kuti ma TATA abwera? UMUNTHU ndiomwe ukusowa usilikari sichoopsyezera anthu ayi

  1. if you don’t know you better shut your mouth mdf has the only nco academy in Africa and they are training Zambias on airborne why is it Malawians you don’t appreciate what your men in uniform are doing go to Congo you will see how good your army is those with everything they fail to fight

 11. Very weak army .when one is beaten by civilian. They run and call everyone with gun to revenge,if ur strong stand our own .

 12. Soldiers are there to protect citizens not to marshal against them, I know also of some pple who stop at nothing to provoke the Army or police ,exercise caution, love peace.

 13. sometimes I feel like loosing tym by commenting such army issues, coz I understand them that many of them behaving bad are not educated, and sangathenso kuwerenga commen yangayi

 14. Tazilankhulani…tikuwerenga nawo…Onyoza tinyoxeni,Olangiza tilangizeni,Opeputsa tipeputseni,Onyadira tinyadireni…In da Army we believe in Discipline,Team work n ……………………………! Kma zikaonjexa nde iiiiih athemule munthu.Chala pansi,rolling,shower ndi zina zotero zidzamfikira…

  1. Ndinkona mumamenyadi anthu chifukwa mwaiwalapo chimodzi. Yesu. Mmesa mumakafola pamnzere nkumapemphera inu. Ndiye mumapemphera zichani

  2. Its a criminal case if he loses his life, you are trained on how to handle civilians who happens to breach the law without causing death and heavy injuries, you are part and parcel of law enforcement agencies such that you know many ways of correcting a civilian with such kind of behavior, unlike the way you have done. Learn to put a demarcation between personal issues and official or business issues that needs to call support from your fellow armed forces men.

 15. KODI MA CIVILIAN NDI ASITIKILI MUJA AMAMENYANA PA CIVO MUJA MWATI ANAWINA NDI NDANI????? AMENE ANAWINAYO NDI AMENE AMATHA NKHONDO.

 16. Both Soldiers and Civilians are Powerless. GOD ndiye shasha, wamphavu. No man is an island. Kunali Gadaf, Shamola ndi wina wa ku Irran ali kuti lero? Tamazitamandileni ndi kupha makwacha kuti ife tisilire ndi kufunsa nzeru kuti nafe tiphenso makwacha osati zomenyana, zophana ayi. Mtendere ndi ofunika kuposa kusowesana mtendere

 17. Amalawi kkkkkkkkkkk ndiye akubwelanso2 lerolo mu Chilobwemo tione ngati muzizatulutsa mau.Mukazaziwa kuti Malawian Soldiers r th best soldiers world wide muzachileka ngati Tanzania inapeleka ulemu ask pipo frm DRC,RWANDA or Ivory coast osamashosha mavu 1day ma degree anuwo muzawasiya mnyumba nkumathawa chitalila zenizeni b serious popanga zinthu

  1. Kugwililako ndiye usilikaliwo mai ikazabadwa nkhondo pa Malawi pano inunso muzachidwa mosafuna mukukamba izi poti simunamve kuti GPMG ikalila zimatani mai keep on talking

  2. @PENCIA sakuziwa mabulutuwa tht army ndi shop ya boma dzikoli likuyendetsedwa ndi dola zaku peace keep frm U.N koma poti umbuli ndi matenda thts why they can tok and shout.Ku Army xul ndiyachani popeza usilikali ndi Heart,blood and fitness inu muli ma pepala andi koma ndi ndege yomwe simunakwele koma a Malawi

  3. Iweso Jonathan ndiwe omvetsa chisoni kkkkkkk kuzolowera kudya ndi kuvala zolandira basi mbuzi zachabe matama thooo amphawi mxiiiiiw

  4. Iweso Jonathan ndiwe omvetsa chisoni kkkkkkk kuzolowera kudya ndi kuvala zolandira basi mbuzi zachabe matama thooo amphawi mxiiiiiw

  5. Agalu ojiba pa thalaveni amangobwera ndi ya umodzi,,,,,bulangete lolandira,,, bed yolandira nsapato yolandira polish olandira,,,,kapu jagala yolandira nkumamulipiranso kma kulephera kugula zibag ziwiri mbalame za anthu,,,

 18. Ndiyawuza a silikali a renalmo mozambiq kut athane nanu 1 sordier amapha almost 3 full tatas nde akabwela tata nde kut ndi nonse samalani .

 19. Asilikali akumalawi tukuwadziwa ndi ankhanza kwa ma citizens…amadzinva u silikali hvy
  ..kulakwa kumeneku..tizkondana

 20. There is book haramu in Nigeria why don’t they go there to stabilize the situation, lack of education, considering that most of these guys are Jc holders am not surprised

 21. i never see hw stupid malawian soldiers are takamenyan tanzania ainso eish

 22. anva ndipo mabwana awo amanva chicewachi.dzikuchikadi wina kuvala unifon ku ganyu yokakwenya ngongole.malamu mulibe ganyuyu koma nkhaza wina yose kuvalira kuchibuku.kodi mabwana anthu oterewa tinganenere kuti ? mbiri yanu isaore ndi mmodzi.

 23. Hw cn u compare Malawi Army n South African Army?? U dnt kno kut ku SA Army they hv all resources 4 their sojaz?? All sojaz r accomodeted within nyc barracks??? Well paid? Kwanu kuno ndinu amphawi u cnt manage welfair ya asilikali [email protected] y u see them in rents, dairly bzneses in local twnz u associate wit them in dairly lyf… Its true ku SA sungaone nsilikali wamba AND u fail 2 identify the reason basi nkumati kuno sitiona asilikali kkkk inu mutaniko uko?? Uchitsilu!!

 24. Malawian soldiers stop this barbaric actions on civilians some african countries needs your help fight against rebels there

 25. Ngati kuli chitsiru cha usilikali mdiye ndi kumalawi,chimadziwa iwo ndikumenya anthu awo umene uli uchitsiru plus usaveji,

 26. Kkkkkk akati akulemba ma soja apa kumazaza ngat kuli mpila wa bullets ndi moyale koma apa kutukwana…. Mmati angomuyang’ana??? [email protected] soldiering usilikali ndi team wrk and nsilikali si John Rambo nsilikali sakhala modzi gyz…. Soka ilo mulungu ntchito yomwe akuidziwa ndi yausilikali basi olo analemba baibulo ndi asilikali kumwamba kulibe wapolice gyz kkkkk asilikali ndiodalisika mwamva inu kodi vacancy ya MDF ituluka liti tikalowe ife?? Lero pamalawi pano dhili ndiusilikali join army 2 kno the wrld kkkkk munthu nkumasilila kukhala kapokola zaka izi?? Kkkkkkk asilikali amatumikila team spirit u wl nva leav buddy behind in a battle field BRAVO MW SOLDIERS mumakwana……… And ur bzy talking abt TZ do u kno kut nkhondo pakati pa dziko lina ndi lina sichitika chisawawa mene mukuganizilamo?? And do u kno kut nkhondo amavutika ndima civilianz?? Tamaonelani zochitika kumaiko omwe kuli nkhondo and see kut amavutika ndindani?? U thnk asilikali amavutika nthawi yankhondo?? Kkkkkk innocent civilianz women n chldren r nw targets during war tym nt sojaz ena muganiza mwaumbuli apa

 27. Asilikali awa, mmh osatinso asilikali koma astikali. Astikali awa akutengela nkhaza za Mutharika. Nkhaza sikumenya kokhatu

 28. mukungotha ma Arvs basi ma complications akakuvutani kumenya munthu, asilikali thupi lyk toothpeak zopusa eti, jce or msce ndi kachaniso at this tym, eti leutenant, commander only at beating civilians and in most cases amakhalanso azimayi, rubbish, stop this shit immediately, ngati ndinu mashasha akanatiimitsa kutsekulira port mwachipongwe chomwe chija? koma inuuuuuuu musanilalatise mwava

 29. Ndigwirizane ndiamnzanga amene akunena za asilikari aku RSA,ndizoona kuno Ku SA siungaone asirikali a army chisawawa ayi,amakhara amwambo pamodzi ndi apolice,Zimene amapanga aMDF penapake ndiumbiri zimatha kuthandinzira anthu okhara mdzikomo osakhara ndimantha ndi Iwo,ntchito izingokhara kumenya anthu,kuwawopsyeza za ziii,mukaziona enanu mukadzapita Ku DRC,APA mumangodya ndarama zaboma popanda phindu,

 30. Ma soilder sadziwa kuti pamenepa amaonetsa umbuli wawo onse,Cas munthu wam’bulayo ndi Mmodzi,Muoona ikubwera TaTa yokhoma bwino like akupita kunkhondo,Kuonetsera2 Mantha cas anthu odzaza TaTa kukamenya munthu Mmodzi ndekuti zimaonetsera2 kuti asilikali akumalawi ndi Panja peni peni,

 31. Kkkkkk,koma ndye mungawanyoze a silikali argues,mmmmh,pot ndi pa social media’pa,kkkkkkkk,inutu simungayankhule manyi mukunenawa face to face with a soldier,dzabwereni ku monkey-bay mudzapeza a silikali a decent,openers,a magalimoto awo,otchena,koma ukawayamba!!!!,udzawaona ngatii savage’di,kkkkkkk,respect them please!!!!!

 32. Ndizoonadi palakwika penapake koma tisachulutse kunyoza atsilikaliwa koma tingozuzulapo chabe mu njira ina pokumbukira kuti iwowanso ndi anthu omwe angathenso kulakwitsa m’machitidwe awo,kwa ine ndingoti “plz achitetezo lemekezani anthu amene mukuwateteza poonetsa chikondi pa iwo pokumbukira kuti inu mwatchedwa kuti atsilikali kamba ka iwo.”

 33. Kkkkkkkkkkk its true guyz asilikali achiMalawi ndi achikape ngati ineyo kuno ku Durban sindinawone nsilikali olo wapolisi kupezeka kumowa ali mu unifolomu ndipo ndizosowa ukawona apolisi ali m’phabu ndite kuti akusa anthu amene aba penapake ndiponso polowapo amakhala atapemph a mwini bar

 34. Bunji osangopita ku mwazambiki kukaphunzila nkhono . Kuzolowela kumangodya beef basi.

 35. ife tikukwera ma minibus ndi masoldier mmaikomu malo akatha kuimilira ife tili pa mpando osat ma soldier athuwa matama nthoo nngat anapanga ndi interview yomwe chonsecho anangowatenga ankolo awo

 36. Lol ndalama zamisonkho yathu kusewela nazo kumeneko. Antcorruption ifufuze ndalama amaseweretsazo zachoka kuti?

 37. come to S.A u can’t see solders everwhere like beggers they r well organised bt if u go to mw mmmm so shame drinking wine with sevilian while they r on duty.I hate them like my shit.kumangowaloza basi asamajaile

 38. Kodi inu asilikali musatisowese mtendere ayi dziko lino ndilathu tisakhale ngati ndife mafolena ayi komanso usilikali ndi uniform yako tsiku lina uzapezananaye zako nayo wotopa azakukwaphula uli muniform yakoyo

 39. Ukakhala kuti uli Ku Joni sungadziwe kuti ndikucheza nayeyu ndi msikali pokhapokha udzamuone ali mu uniform. Asikali kapena asilikali amayenera kukhala osunga mwambo osati omenya anthu omwe amayenera kuwateteza.

 40. Mbuli zawathu izi ndipo amafuna kumapatsidwa ulemu ngat ntchito yawoyo analowera masters kkklkkkkkk zaumbuli bas ,, ngati muli madolo kaishoshe Tz tione

 41. Akhuta nyemba amenewo asiyeni njala ikawa kwapulaso akadye anthu otani amenewo akamvula unifolomo ndimunthu wamba amafuna azisowetsa mtendele basi cholinga aziti ndi asilikali aliowadza khuni kumakampu.

 42. Even GPS asilikari amakanika kuipanga follow…!
  Map reading yake it imene munawerenga?..Zopusa basi, asiyeni Amalawi asakhale akapoli’mdziko lawo..
  Ntchito kugulitsa zipolopolo kwa anthu akuba ndi Osaka ma Albino?

 43. Kkkkkkk a pmf bolatu amatetezako ko agaluwa angooletsa zida basis mantha!! Osapita kutanzanoyako bwanji kimenyela nkhundo nyanjayi chamba eti?

 44. Asilikali wa akugwira ntchito ngati kuti akuchita kukakamizidwa!,mangawa omwe ali nawo kamba kochepa kwa malipiro akuthera kwa anthu maka akakhala kuti asiya kopanda ufa kunyumba akumalusa kwambiri,kodi bwanji osangosiya basayo ngati mukuona kuti sizikukuthandizani?Ftsek!!!!!!!!

 45. Nthawi zambiri amakhalanso mabongwe ku baracks ko akatuluka amafuna kukhala ma shasha mbuzi zawanthu mmatukwanitsa ena osalakws

 46. A civilian is more dangerous than a soldier even a police man,,,when civilians come together they are not izy to deal with,we don’t need to face that experience in malawi plz our soldiers respect yourselves,,do u know what’s going on in USA,turkey and France all around the world,civilians when are tired of horriable behaviour becomes more dangerous than u our soldiers,,,

  1. choka mlonda wachabechabe kaya uti ndiwe penaciah u do dat rubbish bcoz of ignorant. work hard so dat u teach yo children not to live savage life like that of urs.

 47. The most interesting thing with such issues ndi zoti u wont find a Cadet doing such uncivilized acts. i think mwina requirement inakhala Degree for one to be a soldier rhere would be descpline.

 48. They are savages!!! Total savages!!! That is why you see them putting on a uniform even when they are on leave. Savages!!!!!!

  1. Kodi tikamati dzikoli liri m’manja mwa agalu mukuona ngati a galu ake timanena ndani?
   Kunali anthu a Xool achina Njoloma koma chifukwa cha nsanje munawapha…!
   Tapitani Ku Mozambique mukalande area yathu yomwe ma Portuguese anatilanda thawi ya ma British.
   Komaso talimbanani ndi mataifa kti tione kti ndinudi well trained!

 49. Lazy bones…!
  Kodi imeneyiso ndi ntchito?.. Pajatu zikavuta aliyense amatha kukhala Soldier bola kumvetsa kti mfuti imatani…!
  Musazuze a Malawi osalakwa pliz!

  1. amatero kulimbana ndi anthu wamba ndikulanda makala komatu nyanja paja adatenga aTZ , ma truck amafuta ndi aja adatenthedwa ku MZQ pepani pepani

  2. Phindu la malawi army sindinalionepo chibadwire changa,instead of protecting their country koma nkhanza zokhazokha,akapita ku DRC kophikira asilikali ammaiko ena zopusa basi.training ndi training koma kulanda makala dziko muli njala ili angoyang’ana bola asilikAli a zaka za mbuyomu achina,matewere,yohane ,chigawa amazuzula boma.

 50. mbuzi zawanthu zimenezi zimandibowa kwabasi.mbuli zolowera ntchito primary school leaving certificate. amazitenga ngati ndani kaya? ofunika ku kumana nawo mma Tarven mu kumangowapha agalu amenewa

  1. usilikali sintchito yonjoyasa . anthu aliku usilikali mbuli za anthu. amazitenga ngati kuti ngophuzila chosecho ndi mbuli. ikakhala mduti njosavuta kugwira ena ndi zina chabe kuti usilikali koma angotolela zikwama.

  2. Bola Mwamva Agaru Nomsenu, Mudzangoyerekeza Kushosha Mmodz Mwa Ife Mudzawone Kaya Ndikudzimva Kuphunzira, Komabe Muli Pans Mafana Muzipereka Ulemu Osamaphweketsa Ndipo Ine Sindinalowe Ntchitoi Chifukwa Ca Jc

  3. Hey u idiot stop talking shit. Usilikali sikuti ndiwe chitsulo. I have power than u. A real soldier has manners. its for lazy thinking pple. Ngongole mumahawkers pwa. What are u talkn. Akunyetsa ukatengera mawala.

 51. Kodi mukudziwa zomwe ma citizens akuwapanga a silikali ku turkey…. zomango khalira kumva kuti wina wamenyedwa ndi a silikali ✋zitheretu zimenzo otherwise muzawuwona mkiyo wa umodzi wa anthu

Comments are closed.