Mzuzu residents have been warned to keep their daughters away as rapist General Kanene will visit the city next month.
Malawians made the warning on social media soon after Skeffa Chimoto posted on his Facebook page that the Zambian musician Clifford Dimba popularly known as General Kanene is coming to Malawi.
Skeffa said he will share the stage with the rapist when they will hold three shows in the Northern region. The two will perform at Mzuzu Hotel on 1st July, Planet Entertainment in Karonga on 2nd July, and Mzuzu Tourist Lodge on 3rd July this year.
Kanene’s visit to Malawi has sparked debate among people in the country as some have warned those in the Northern region to keep their eyes open as the rapist may sexually abuse their daughters.
Kanene was in 2014 convicted and sentenced to 18 years in prison after he raped a minor.
He was later pardoned by Zambian President Edgar Lungu after serving one year of his 18 year jail term.
Ena inu mwagwirirapo ana koma kusagwidwa musachuluke nzeru iya
Ena inu mwagwirirapo ana koma kusagwidwa musachuluke nzeru iya
dats true guyz be ware about kanene plz my people
Ndakhumudwa kwambiri, by caling sum 1 a rapest. Tangonganiza kuti ndiweyo being insot in such way as u did to him, ungave bwaaa? Kumanganiza kawili, katatu ndibwino..
Zandinyansa mwaonjenza a MW24 mwayamba bodza ngat mulibe nkhani kungokhala bwa
Mw 24! shupit
Zautsilu basi kusowa chokamba eti? Mxiiii
Did u see him? Malawi 24 you are so rude and could be sued for statements.
Iwe kwaku tatenga remote utchaye select kanyimbo ndikabwino… Kwatelera basi ku mzuzu
Kkkkkkkkkkkkkk koma
Akt General Kanene sangaimbe amene sangaimbe niuso check this outu
Makandi yako, shame on u chikala suzibakuti unyoza BA ambassador? Ata kupusa bati
Koma inu panyelo panu ndithu kosowa zolemba et agalu
Shame on you writing stupid articles like you are a cent. Bunch of idiots
Mentally bankruptcy in fact you need a brain donor ka Malawi 24
Idiots, if u don’t have something better to do then just go to the toilet and …….
Kanene is not a rapist
He was convicted for having an affair with a girl of under 18
So you 24s you are not worth to bear a national name
Because of your primitive and natnariv behaviour
Dzimvele mu mtolo!
Ona lero wapusa
Muenera kupepesa
Kapena kusintha dzina musakhalenso
Kodi kuno onxe amagwililidwa aja ndi General yemweyo amawagwilira? Tink twyc.
So what is the connection here?
you must be a professional fool
What kind of sheet are you malawi 24 why you are violating some one human right ngati mwasowa zolemba kungosiya bwanji
shame on u m24
A Malawi 24 ofunika alandile chimbama chakumatako
ndi former ambasada wathu kuno and i doubt if he z realy coming there coz pano tili bisy kapeni 11august a lungu niboma
Uslees pipo taking abaout others
welcom Kanene
go away whith that article
Mmmmh koma choncho sibwino wat the fuck is this? Why do u want to spoil this mans business grow up pls guys even if he did he paid for it who knows may be he learnt his a lesson. So let him be plsssss
Agalu!!
they want to be popular but i wonder why they decided to take this way,,shame malawi24!!
Mw 24 haters!! ur posting ma rubbish.
Idiot
Idiot
Malawi24,u must be vry stupid.how can u sit down and post this stupid news? learn to respect our nebas
Malawi24,u must be vry stupid.how can u sit down and post this stupid news? learn to respect our nebas
Iwe walemba nkhaniyi ndiwe chitsiru sindizakondanso nkhani zanu
Iwe walemba nkhaniyi ndiwe chitsiru sindizakondanso nkhani zanu
Zachamba et
As a Zambian, I say lock up kanene immediately you see him greet girls, especially children! He is a health hazard!
This is nonsense
Malawi24 yu are very stupid
Iwe malawi 42,umatibowa ndi nkhani zako za zii mufuna kumuonongela mbiri nzanu??shame on u
Thats true
Kusowa zolemba
bola iyeyu Amangogwilira,koma iweyo #Malawi24 nd Mabwanu ako Onse mumapha Anthu akakudzudzulani pozonyasazomwe Mumachita.We forget to forgive.Mind you,”
Zikugwiriza or its a joke?
Hmmmmmmmm,as a Zambian I feel so insulted.Hw dare u insult the General?Ndipo muzisanka zolemba musamalemba ngati mulibe evidence sha!!!!!
need to insult him coz he’s a rapist full stop
Za nziiiii!!imeneyi ndinkhani,osakambapo dzaphindu nthawi zina bwa?
or mungankhomelele bwanji i love this guy.kanene big up
Ndizoonadi ndinudi mbuzziii za atola nkhani
unlike pompo pompo
He is a registered sex offender people should be told how it is nothing wrong here hahaahaha
We all learn by mistake
These people are not professionals..ask skeffa chimoto on this number 0999 647 938..He will tell the real line up of artists on the poster. there is magigi, chimz kelly and skeffa NO kanene on the line up..mutichitisa manyazi a media fe mxiew
How about ur own deeds?Malawi media always after ppo…xul munapita kut?nosense
We waiting for ur apology idiot
Zaziiiii
Mmmmmm this is irresponsible journalism, ….does your publication even have an editor? .
what a stupid post! Who are your editors please? Aaaaah ndizochititsa manyazi izi nsaname. Don’t post things anyhow mutionongera mbiri yathu yabwino.
Mmmmmm Pali zotukwana anthu munakhala bwanji ku jaja anzanu Please don’t do that again
What kind of reporting is this, you seriously need refresher courses!!! Shame on you Malawi 24
Forsake malawi 24
someone remove me from this group, i cant take any more
Osatengera lamulo kumanja uzavutisa banja lako…..osatengera lamulo kumanja uzavutana na boma….love this song
Ka page ka anthu openga aka
This is so stupid!
kkkkkkki
Not good. Judge him not by his past. We all make mistakes.
General kanene walakwa chani kodi kukhala tidzingokhalira kuyipisilana mbili?kukhala satero kanene timpatse ulemu,Nayeso ndi muthu ngatiife tomwe bcoz ndizowawa kuyipitsilana mbili.
Mmmmmmm m media enawa if i was d 1 i cld sue u O:-):-
think twice before you post thats not good
This is a clear indication that you are not professional, you take Kanene as a dog which barks everyone
Stupid mother faker..way cn u say that 4 kanene,,,,
Stupid mother faker..way cn u say that 4 kanene,,,,
I don’t think its a malawian who posted this …. iam a malawian and I’m very sorry for the insult …. better him his a rapist but the one who posted this I’m sure his an albino killers bcz it has showed his a very stupid pig
Malawi 24 Ndiyautsiru Heavy.Imangolemba Nkhani Zopanda Phindu
Welcome to Malawi GK ali nachilonda ndiye amvela kuwawa big up, check this one out leketee
Bwino.. muvelevele abwera.
Inu talembani zanzeru sizopusazo iya
Inuyo achitsiru a Baxter pamenepa mukuti mwalemba nkhani worth reading?
The biggest stupidness you ever published is this. I think you are all drunkards fools ngati sukumufuna osangokhala bwanji amalawi tikhale ndi ulemu uja wakale please!!!!!!!!!
kumaona zolemba nanu inu he z comin here to perfom osat nyasi mukuthokazo ndipo amene walemba nkhaniyi alibe nzeru mkati mwako
Ndinkaona ngati a Malawi 24 ndinu maprofessionals koma sinnadziwe kuti kuli mbuzi zokhazokha. shame on you!
Kuweruza ndi kwake! !!!!
Welcome to MLW GENERAL KANENE & leave more of ur latest albums here. In ur schedule, remember also BLANTYRE. Never mind these simple minded so called journalists!
Kuchinda siwaletsa manje machindidwe.. …inu a Malawi 24 bola osachinda over.. Demeti zanu
Ife ma Zambians timakunyadirani kwambiri poti timadziwa kuti ndinu abale athu, ndipo maganizo a misampha mwaife mulibe, koma mukatitenga ngati anthu opanda nzeru ndiye kuti mukupempha kutsenza mphika wakupsya pa mutu panu..
kuyambira bwana wawo,atolankhani ndingoti onse ogwira ntchito kumeneku ndizitsiru,mbuzi,agalu,anyani to the maximum.zidebe zobooka zopanda nzeru olo pang’ono
But y can’t u just concentrate on your albino killing business and leave peaceful Zambians alone?
mwasowako zochita eti kugwilira ndi kuimba zigwilizana bwanji?? Makape okhaokha xool yaka munakaphunzira iti ………#Stupid
Fake reporters no trust on you now
As a Zambians we feel insulted Malawi 24 need to apologize. We have a lot of Malawians who stay and keep them as brothers and if can call us name? Do you want us to take a revenge on your citizens as they enter through mchinji boda every day?we know, we see them,
ndkumangisani.
un ethical
He rapes the beautiful ones, so there is nothing to worry for there is no any beautiful daughter in Mzuzu.
Mental retardiation, totally delapidated
That’s the problem of studying nutrition and you want to be a reporter. Leave these pages to journalists
Kkkkkkkkkkkkkk Malawi 24
News papers in MW never writes serious issue
Koma inu mulakwa nazo za ziii
Kkkkkkkk koma 24 aaaaah ndinu mbuzz
Kkkkk chosani post mulembe kena manyazi bwa mmm musamuipisile mbili muzanu mm
useless
Jickmented way of comm to the followers.
Try to find other means not that. u r proffessionally uncorrect!
Faq u
loading………..No! alrady. Man ngat mufuna kuntchuka mwalakwitsa nt this way…wi r 1 pipo
A Malawi Dzukani,osangoti zakunja, munvetse mbiri yake General Kaneneyo then put up your comment. Cool and smart. Other wise muzaombela mfiti mmanja.
Bwetete wamanu nonse aku malawi 24 ndiye zikugwilizana bwanji ndikuzapanga visit mzuzu ndisete zanu zimene mukuyankhula kukhuta eti
Foolishness at it’s best shameful reporting and primitive at it’s best
Idiots u think Zambians r rapist fuseki
Nkhanizi mumazitenga kut kodi???
ngati mulibe volemba z better mukope ng’ombe vimenyana na nkhumba pama blank pages kuchila kuti mzikamba G kanene sowonse wewalinamamimba ni kanene anawapasa dont b hearing fals romous about kanene he z a gud guy
A stupid title
Stupid post!
za ziiii……….kupusa bas
Malawi 24 where do you get your reporters? ?
Are they professionals and know their
responsibilities?
This is disgusting guys otherwise we readers are losing trust in the way you present your news!
Totally out of code of conduct! Do have evidence ?
Yoh shame on u
Ulekwatako amano chika………… waunfwa
Ya its now time to #unlike malawi24 because of #stupid reporting.ma page ena ngati malawi voice,malawi independence,ndidzaulula +ena ambiri ndidathana nawo kale.lero ndi tsiku lako malawi24.tidzaonana,byeeeeee!!!!!
yenda bwino
Is this what you call professional reporting?
Do u hve proof thdt he’s a rapist or u act on rumors,,,idiots,,,
Amalawi24 apatu ndemukuonetsa ukape wanu pa display Lol
Amalawi24 apatu ndemukuonetsa ukape wanu pa display
Kodi inu simunachimwepo why u like to publish nosense
Mapeto ake akakutukwanani muziti anthu ndi oipa pamene inu khalidwe mulibe
Malawi24,pliz stupid becoz u are out of business,apologise to the public of Malawi,I will nvr say to Zambians fans,nina bafana base zambia do nt say u feeding Malawians bt Peter family plz,nawe matyanda ghako,u strungle 20yrs nw u forgot
Its fine poti Genneral kanene adayimba kale (munthu salimuche) ndiye Adm naye ndi munthu kkkkk mbuli xophunzira ximenezi mukunyoxetsa dziko ndinu
Check this out!nawe iwe malawi24 suziwa kukamba manje suchita bwino ine sindikonda zamene uchita iwe…..kodi title inasowa mpaka kuika imeneyi?ndizakutchayani so
mukhale ndiulemu abale
Amalawi kupusa
Mwasowa nkhani eti inu a Mental24…sies
Manje chizungu muziwa kulemba koma m’mutu nzeru mulibe sure,why muchita ngati kuti mphamvu zamene asewezera anapeleka niwamalume wanu? nizake mphamvu! sizamu familynso ya amayi anu, araa! apa amalawi taziwa kuti inu a24 muli Dead minded sure.Aaa! Chake Dis Out!!
May someone have mercy on your …. soul, let’s emulate love among us to shame bad spirits.. leave negativity and concentrate on good one did.. proudly Zambiain in gods image we are all one..different colour one people.
Eeeeee man mwatani mpaka pamenepo???? Why??????
u no sense people aaaaa
Malawi 24 Pls go to Hell!!!
musamunyoze komaso kumuipitsira mbiri munthu bwanj osangonena kut kanene akhala ndi ma show osat kumakamba zopusazo
Walembawe Mac..che…nd..e…ako!!!!
Malawians,you guys should start behaving like pipo who are schooled.
mwamunamzla kt wavala nsapato yamwana
Malawi 24.com change
Machimo ali mma grade osiyana. Osamanena anzanu ngati kuti inu simudachimwepo. ZANU mwapanila…munene za Kanene…isaaaaaa!!!!!!Mxxxxxxxx
Tiueni tipasane ulemu.
I was in mchinji lelo… Yaba. Thats why Malawi cant develop with media like this one. Malembedwe ya Nyau Nyau…. Phwate
Sanje poti kanene akupita ku mzuzu nanga bwanji osalemba zoti a Dpp akumampha ma albinos mbuzi za anthu inu ziwanthu zopusa ngati cabbage
I have never seen a senseless article like this one.
kodi ku page ili timalembako nkhanizi nditi ana kapena akuluakulu ngati ndi akulu akulu nde nawoso ayi2 sakuziwa zoti angamalembe mwina ndi kwama jokes?
Stupid page, timanena ife kuti Malawi 24 ndi kagulu ka anthu openga, ozungulira mitu nanga tawonani zomwe akulembazi..shame on you.
Is like a damm………
Just on a lighter note side and not something to be taken seriously I suppose!
hahahahaaa sagwirira #General, amagwirizana kuti akapange zadamazo,,,inuyo ndi ana anuwo bachedwani paja iyetu #AlibePulobulemu
No sence
#FCUK****
mudziganiza bwino as human being pofuna kulemba nkhani zanuzo.Boma yamulola bwanji kubwela? Mwasowa zolemba eti?
lets call a spade a spade chilungamo chimawawa……
Malawi24 @…@…@Vizende Imwe
lets call a spade a spade
Malawi24 fans yake yonse inavaya School zakwachaa
This is total trash.
This is embarrassing, i never thought this page can do this, you have disgraced our nation. I wonder if you are really a Malawian.
Forgive him please our neighbour,
nosense,i thought ur educated enough to not destroy other people’s private lives, if we dig you up you might even have more crimes than what he did you morons calling yourselves malawi24,if his country’s court set him free,what rights do u have to destroy his image like that,find interesting news to write not this nosense,useless!!!!!!.
You are nothing but a fool
Stupid Malawi 24 reporter, if u ve nothing to write just sit and relax
Poverty stricken news media
U admin nyapanu wat wrong does kanene did 2 malaw am malawian bt dont talk dat thing it jst shows hw stupidity u r,, once again nyapanu,,,,,,
Bad & stupid kind of journalism, learn to report responsibly. I’ll ask Clifford’s lawyers to take legal action against u Malawi 24
kkkk kupusa….. kulibwino uzilemba khani Zako zomwe zija zot banja latha chifukwa cha missionary… than kuipitsa mbili ya ena
Hahaha.Abale,kodi Amapanga Choncho?Kkk.Tisaipise Mbiri Yabwino Yochuka Kuti Warm Heart Of Africa!Kanene !Welcome To Your Home Away From Home!We Are A Hospitable Nation.
Hahaha.Abale,kodi Amapanga Choncho?Kkk.Tisaipise Mbiri Yabwino Yochuka Kuti Warm Heart Of Africa!Kanene !Welcome To Your Home Away From Home!We Are A Hospitable Nation.
Nangasi walembawe sunachimwepo
Amunamidzila
Ngat mumasowa zolemba muzingosiya aaaaa nditukwane kapena paaa oky bas musiyen muthu za usilu bas
Amalawi 24, Ndinu Wakolwe
imwe amarawi 24 mwapurumuka chifukwa sindli ku malawiko ndkanakupangani zina nd zina,bcoz of ur stupd post
Ths Z A Nosense Post, Anagwilira M’bale Wako, U Hv To Serious Malwi 24 Otherwise We Will Lose Interest In U
Malawi24 koma mumanyanya anthu inu
amalawi 24 ndnu amisala khani zinatha kalekale, osamalemba khan zotukula dzko lathu bwanj
A 24 mwandikhumudwisa,it’s not fair.
Oimba wakulu pa zed wish you all the nest
I do regret likin this page. I believe this journalist is a chewa tribe, ur notority is jst de same as that ov a goat. pliz write smthing dat can give sense. stupid m24 with stupid journalist. have u seen zodiac saying nonsense like this?
Malawi 24 this is too bad u have to grow,i dont knw if the writer went to school,thats an insult
Malawi 24 this is too bad u have to grow,i dont knw if the writer went to school,thats an insult
Kkkkkkkkkkkkk amalawi sazamva
Messi wasiya kusewera mpira ku dziko lake after ataulusa mpira pa penalty imene anasewera. Mpira unakagwera kunja kwa stadium
You Jounalists,that’s not the way!
are u (the writer) better than him?
You would have searched for the better term to use than that word.
My folk man! take out ur silly post
I, being a Malawian, am much disappointed by the writer and the topic itself. Sorry for our neighbors
Am discourage with this fokolo called mw 24
am a zambian and am very disapointed with your remarks, malawian you are a disgrace to us.
Kanene sanagwilire,,, mfanayo ankamufila kanene,…………….nanga akanatani poti nayenso ndi munthu, chinali chibwenzitu
Admin ur brain need to be fixed
Very stupid indeed
Where Is Ambulance??? Iwant To Tek Our Admin To Zomba Mental Hospital Bcoz Wat U Hve Written Is Totally Insane!!,,, Makes Me To Call U “Asshole”!!
A malawi 24 mmmmmmm i think simunakwanile pa umunthu wot mutha kupatipasila nkhani
kkkkkkkkkk.u reporter i think u don’t know ethics of ur job. go back to xul
simuonekanso pa phone yanga oipa inu osakhululuka
This is bulshit M24 you have just proved that you are that kind of people who likes when others are in pain.you fools and nothing but fools.Everybody makes mistakes and they don’t pretend tobe good but try to figure out how they can restart new life as a changed people. get life guys and grow up. if you don’t know ur work I ll give u some tips. MIND UR OWN BUSINESS
He who has no Sin must be the first to cast the Stone. If U are really serious about ur Warning I guess U warn the Immigration Department not to allow Him inside the Country. If they allow Him then He is a Freeman. And I trust all the daughters and girls U are warning about are all virgins.
Kuopa kukawachita rape, mpiru,chinese
kikiki koma ndaseka
Aaaaa koma
muri vindere ba malawi 24 SHURT UP.
don’t think only malawian read your News,we zambians read it too.think of the impression u are creating.
makape24 akanena zoona ndizampira bas
Apa Nde Mwaonjeza Bwanji!!! Mwana Wa Mzanu Kumchezela Choncho?
Zawana chani……?ati Malawi24…..mmmh ok
By watching your children, stop tis man.
Koma
Worse article ever, u guys have no right to call the artist “the rapist”
NDICHO CHIKHALIDWE CHA AMALAWI CHIMENECHO INE NDIWADZIWA BWINO!
Nkhululukileni mtola nkhaniyu, amagwa chifufu.
Is he just raping any how, please write what can make interest to people to like your articles.
chikaona nzako chapita mawa chili pa iwe chikakhala kwa nzako umati chigwile nyanga!… pepani kwambiri!!!!!!!!!!…….
”Nsapato za ambwiyako!”
Manje mukulemba va bwanje inu a 24 thi z shit, plz just close this page
Machende yanu
Akapuku mwakhuta nkhwani uko mapazi anu
Thz same gals u re warning to stay away frm Kanene wil be throwing themselves & flocking at him lyk bees to scented flowers…….U can’t bit gals with fame guys
General Kanene was convicted and charged in a court of law and condemned to 18 years behind bars. After serving his sentence for 1 year he was pardoned by the highest authority in Zambia, H. E. Edgar Lungu, the president. Some of the reasons leading to that pardoning are good behaviour and remorsefullness.
It is therefore disgusting for Malawi24 to insinuate that General Kanene is coming to Malawi to rape our daughters. It is total disregard of respect and dignity to continuosly call Kanene a rapist when you don’t even know the truth behind his incarcelation. Reading between the lines of Skeffa Chimoto’s facebook it is clear that Kanene is a musician of high repute and is coming to Malawi to entertain and not otherwise.
Malawi24 should have been the first to desist from mudslinging. By doing what they have done Malawi24 has dented its own image as a source of information that can be relied upon. The most noble thing they can do is to offer unconditional apology to Kanene through the same channel.
Altermatively the author of this blasphemous article should be traced and be sued for character assassination so to send a message that mediocre reporting has no room in morden Malawi.
Lol
Does that make sense at all to write that, sometyms if u want other to respect u, u shud respect urself first.
ndani sanachimwepo ayambe kumgenda uyu,nsambi,
satana mphamvu zamene alinazo? ndizoletsa anthu kuthandizana!
Sikulankhula kwabwino kumeneku.
1 out of 18 years!!!!!? Am sure there wasn’t enough evidence to his conviction and he was rather just a suspect. This is not worthy a news
Malawi24 you are not matured jourmalist & you have nothing to offer malawians,shame on u poor educated journalist.
All we are bound to wake mistakes. but why dwelling in the past? thou shall not judge. he is a different person. he diddnt even rape. it was just a trap. you dont have stories to post? are you angeles? are you jealousy?
Iiiiiii Malawi 29 shame on u. You don’t hv any stories
Kulakwa uku Munthu akamangidwapo chikhale chifukwa?
Malawi24 Apa Ndiye Ndakhumudwa Nanu.
If he is a rapist then people should be told but not by saying he is coming to rape them….. Why was he pardoned? If he is a rapist then he should not be performing but people will still follow him and if he was wrongfully accused he needs public apology from malawi24
zachamba izi eti anagwiririlapo mchemwari wanu?.
Kusowa zolemba zikugwirizana bwanji? Akubwerera ku zayimba? Pena kuzagwirira tiatsikana mukambato, this is nonsense
Chabodza Ncha ? Isn’t He A Rapist ?
Jealousy Malawi 24 you writing rubbish! Is that how to famous people? Is he the first in a such crime? Nonsense!!!!!
Mwayamba kupusa manje, nanga imwe mumapha azanu na ati mwayamba kuyenda mbulanda si kupusa konse uku uchisulu vabwera mochedwa ivi vinthu musiyeni abwele tione ngati azagwirilira kamwama kanu.
Apa ndiye mwaika bola yeniyeni, manyazi bwa
Kumva zotelo, kutulukilatu page.
Ngati mumasowa zolemba kuli bwino mudzikalima kumadimba mwamva!!!AGALU.
Learn to forgive nd forget in life.read the bible everyday malawi 24
Amene alemba izi ndingoti ur ass
Malawian dis z yo behavior ua biz begging for food in chipata
Zziiiiiizzzz zaziiiii
kkkkkkk
Check this out!
Guys lets report ka media kompusa kwa mbiri
How can you say like had been its others are saying like that how can you feel!
Kod iwe malawi24 bas nkhan ikhale.imeneyo
Kulakwa tu kumeneko
Is kanene coming to Mzuzu looking for girls to rape? A24 inu tamalembani zomwe munthu akubwelera and be proffesional on your work.
Ths is Bullshit! hw dere’u? whats the point in fact? Kupusa kupose pamenepa? Mtopola2 umenewu. Mukunyoza Oimba ot athandizanako zochita ndi oimba athu. Admin thi is tatally insane!!!!
Chimizi wakwithu pala imwe luso mlije lakwinba, just zipp up yr dirty mounth and stay awae
What’s this Malawi 24? ???????
U ar vry stupid hw cn u say tht” kufuna kuononga mbiri zanzanu eti! Anakuuzani ndani kuti abwelera kuzagwilirira ana? Learn to respect other pipo oky! Silly
Kkkkkk
Chala sichiloza mwini
Evean if kanene rape he rape on his wil, there iz northing to do with u,,by the way he is coming to make money in ur coutry while u r busy gosip about him u ideot
another defamation case,ngati mulandu unatha he still remains a rapest?ngati sumvera mushe imwa!
So if people fail to go there will Malawi 24 refund his expenses?
Inu a malawi 24 u r very stupit,ngati mwasowa zolemba muzingo gona.pamataku pinu seeeee
Kkkkkkk wasweka kwali nawi
Vindeli ivii weeeee
Chomeni
Chomeni
Pala wasowa vakulemba basi kupanga za against.
Pala wasowa vakulemba basi kupanga za against.
Eti mbundeli
A Malawi24 news pakuti pinu mwapulika? Is this how you insult musicians?
Character assassination
zachibwana zokhazokha basi
regreat to like this stupid page
did he rape anyone before?
Stupid media practitioner,am a Malawian but this is very bad!Why can’t just mind your business.You are very stupid and you should apologise to the General.
Yes Indeed Malawi 24 Need To Aporogize To Gk
Malawi 24 panya panu ziphwisi za abambo ndi amanu! !!!!! Mwandikwana khala ngati inu muli oyera opanda banga? ???
kikikikik malawians will never seize to amaze us, the backwardness and primitivity is still rife even upto the level of a journalist, i thought by now you should be able to diffrentiate between rape case and child defilement, for your information the person did not go to jail for rape but sleeping with an under age girl, kupusa naku pwalala ndiye kwanu ambuzi imwe
kodi who owns Malawi24????…i’ll keep on urging the whole M24 to go bak to xul coz M24 has alot of characteristics of ignorance!!!!…journalism yanu a M24 munaphuzira kuzaire eti??..atolankhani anzanu ozindikira sapanga za usarvage mumapangazo!!..
Osafuna akhale ife tipita
Realy guys,trying 2 tarnish General Kanenes image,did he rape ur daughter or ur sister,live da guy alone,u cnt evn prove da accusation,rubish
Chimbutuma cha Mtulankhani….
Mkadakhala ine mkanachotsa post imeneyi pama comment onse 104 ndawerenga zaonetsa kuti olemba wa Mw24 walephera ntchito
Za Zii….
Dude ain’t got something to write eti? Mxm!!!!
Zanga waka nawe kanene tizayimbe kuno kumzuzu takupokelelera namawoko yawiri don’t litsen to this malawi 24 news
They must apologize,
Let’s love our neba country Malawi 24 wakeup
This is Rubish koma.
Kodi olemba zimenezi mnaphunzira school zotani??
Mbatata za anthu ndithu
Zaziiiii kamba ina osati zaugaluzi
what kind of reporting is this ?
Thats stupid malawi 24 leave GK alone i will never stop like his music
koma yah amalawi24 nde mwati titani? azanufe chizungu ndiapongozi.kkkkkkkkkkkkk
Matter of fact malawians are not foolish.it is this clarpy media publishin lame facts. watch ur dirty mounths before u typ in ur comments.and u stupid journalist how many time do we have to tell u about publishin dirty bull shit stories
Mpnews24 you must go to hell! If it’s jealousy then you’re a son of Satan, there’s no other way to introduce him nicely?? Do u understand that u can land in jail with such kind of insult? His case is over and he’s not a rapist!!!! You better go to hell
Munasowa Zolemba Eti?
Munasowa Zolemba Eti?
Comment loading
You admin must be some how sick upstairs, how can you say such thing? Is General Kanene coming to rape in Malawi? Stop smoking weed man!!!
Nilibe naye chifukwa
Welcome home GO we love u….
Why worry about an undiluted imbecile? This is bullsh**t…
do u mean to say that he is going to mzzu to rape girls? shame on u admn.
Nkhani Zina Izi
What kind of reporting is this
ma guys a Malawi 24 mumatinamiza hevy bwanj…..mumasowa chonga post chani….what kind of bullshit do you guyz post here
Mxiw!!! nxa!!! iwe ndigalu eti, uli ndivuto, masowa zolengeza aMalawi, zitsekeleni inuyo ndibanja lanu, WE VOTE FOR HIM KANENE
Joe gwaladi will also be there
Ka Imwe Wa Malawi 24 Mitiyinu Yikwenda Makola Pamalo Yanyake Ngati??????.Nthenvakuti Mungalembanga Ivi????.Muri Vabweka Bweka Chomene Sono.No Sense.
Malaw24 tazipangani Zau proffessional nde zichan zimenezi umbuli bwanji Kumangolemba #zopusa bax #zitsiru zosazindikira #agalu muuzane ngat mwatopa tsekan #nyasi zanuzo #stupit!
Kanene is agood musician than malawian ok
That’s an insult guys. If he has a rape crime it doesn’t mean he keep on raping each and every path he walks. This is not good reporting
If you got nothing to writer the just shut up ,stupit writer
Malawi 24 you are stupid ngati mulibe nkhani osamangogona bwa
Agogo pamulomo
Iwe chicco ndisamale kkk
Hahahahaha tikuope?
Ayi ungondisamara koma
Tiyeuko
Ndana sakuziwa kuti uli mwano ngati Malawi 24
Kkk choka
Iyaa uzindipasa ulemu
mbuzi za atola nkhani ngat izi sinazione,,,kodi mkumalemba nkhani mtalezera kapena chani??Nosense!!!
Ngati aMalawi24 mumalemba nkhani mopusa chonchi,sitizakukhulupiliraninso.
shame on you, u call ur self malawi24 but ur the 1 ukuyipitsa mbili ya amalawi kumaiko ena mukakhala mukusowa zolemba muzitenga manjawo nkumaseweletsa akatunduwo ok
That’s not good @ all, General Kanene ndi munthu ngati inu and mutati mufufuze bwino mupeza kuti nkhani yogwirirayo anangosema,tsikanayo anali wamkulu ndithu koma kamba kakuti ndi wotchuka anafuna kumuyipitsira mbiri,nsanje ndi yoyipa zedi khalani ndi ulemu,anananuwo akutenga pakati ali ndi 14/15 years onsewo anapanga izo ndi General kanene? Kusowa zolemba
Malawi44
wats o diz,why denting a bad image,kwa zanuu,mwalowa china…
mind ur own business&munsiye Kanene out of ur stupid stories,,,,,,,poti zanu zabisika nde muzikamba zaanzanu???????ngati ana anuwo ali mahule amaphweka okha!!!!osati muzilemba zoipa zamunthu wina ayi,,,,,,,,,,u idiots,,,,,Kanene uyo walemela kale inu ndimiseche yanuyo muzingosaukabe
go deeper!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!
kkkkkkkk sunagonebe nawe
nthaw zino ?
kkkkkk
iya kagone uko kkkk kwada2 uku mmawa ndikumunda2
kumunda kotan ? sindimatha2 kulima ine.
mmmmmmmm zaulesi basi kunamizira kusatha
iwe sindimathadtu ine koma amakwanisa kwambiri ndi ……………………………………………….
ndani????hahaha basi usatchule zina ndamdziwa
kkkkkkkkkkkkkkkk mwina siameneyo ukuganiayo?
ndiiyeyo Mmmm kulambalala apamanda pamusi paja wanziwa????
kkkkkkkkkkkkkkkkkk yah ndanziwa.
gud
kakaka
This is one of the nonsense post u hav ever posted,,,,be serious!
Aaah check this outu
Zot kanene anagwilila ndizopanda umboni, takambani zinthu zamzelu apa zoti zikuthandizeni osati zomangolimbana ndianthu oti zawo zinayela kale
Walemba izi ndi mbuzi
Malawi24 Always attacking Innocent Ppls..
kkkkkk….
A’ AAAAAAAAAAA!!!!!!!! AMALAWI 24 WHY? NGATI INU SIMUNAYAMBE MWACHIMWA, AKABWERA MUYAMBE NDINU KUMUPONYA MIYALA. ENANU MULI NDI MACHIMO KUPOSA CHIMO LIMENE ANAPALAMULA KOMA KWAKULA NKUSAGWIDWA.
Zausilu General kanene ndi munthu wankulu mpaseni ulemu
I am a fan of General Kanene. Whateva bad u say about him can’t move me an inch. Thanks.
Did this man rape someone and go to jail for rape? Why was he pardoned? If he did commit rape I bet you never thought he would do that so if he can rape once surely he can do it again…… But like many wrongfully accused people in Africa maybe he is innocent the is no harm in alerting people of what he went to jail for. Maybe his music is good but if he did rape someone no matter how good the music is surely you can’t still love him if so does that me your ok with people rapping others?
Rubish.if you don’t have something to Post just go to TOILET.maybe you can keep yourself busy.
Malawi24 are empty vessels!!! I’ve seen most of you’re stories, they luck substance, are you really ethical news publishers???
kkkkkkk No Comment
Kkkk chipongweee
Kekekeke, lock them up,,,
Kkkkkkkk uku ndi kuwashosha dala wa neb
Kkkkiest. Ndakomoka
Kodi news iyi ndi satanic?chani? Kanene angadzagwirire ana kuno?
Kkkk
nyo0o u idi0t malawian pp0
Eeee amalawi sazathekadi…kkkkkkkkk….
Kkkkkkkkk lool
khalidwe lavutapo apa!
Dont do like this we are 1 in christ
Ndy a2 ogwilira d u set dem free,,malawi24 pano ndy palib zmen mukulemb.
welenganiko Duncan Kaonga Patience Jaccobs
Shaaa anthu ngachipongwe pulizi kkkkkk…… tibisa ana onse #maule_Zingunde
hahhahahahahah ndipo inu kalembedwe kamakono
Atolankhan akuonjeza pena pake
ine zandikhuza
Sakhomelela chonchi!!… kulesa anthu kupita ku show kumeneko?
ife tipitabe #Tikavina
Olo akhomerere ana akuti atitetezefe tili konko…
koma ma comment ukuwawelenga koma
Ayi sinnawaone ima ndiweremgepo
Tanenedwa naotu apa .. ngat kut all journalists r lik dat
Akufunika mu class la Nyirenda awa
hahahaha Assiii ntheee
Vin anathoka2 kt M24 ndiyama students kkkkkkk
Kma apa ationjeza
kkkkkkkkkk Aixe ine kulilira ntundu wa Amalawi
Kkkkk koma anthu nde akuyankhula
Palibe wanena chabwino
Aziwapanga edit ma stories awo
Alibe Editor
Eeeeh mavuto nde alipo
Nkhan zoterezi akapusa nazo azawamanga nazo!…. amalemba zoonjeza
mesa akuti freedom of expression
Nde amat azipanga defame anthu?
Ma xul kusiyana
Section 34 -36 of the constitution kkkkkk
Duncan ndi yako yomweii
Ma xul kusiyana?? Muli ma geli angat a journa muno?.. vin ankat amakhala a btz compass ambiriwa
Kkkkkkk aziphuzitsi kusiyana
Ah we all knw journa ethics apa
sanafike that topic
Hahaha nde we assuming kut alembawanso?
kkkkkkkkkkkkkkkkkkk,,,,,
Nde wayamba kukwiyira ife#Nana
Ndakwiya nao awa… kkkkk ahhh Sozo
Ndangoona
Munthu musiyeni A 24 inu alibe puloblem vuto ndinu.mesa zinatha kukhoti akumangitsani zaziiii iyaaah!
otsamuonongera mbiri kanene big up will be dey
Inudi nkhani yakale kale ngati yadzulo asowa chokamba, apa ine ndimamkonda.
mmmmm u malawian munthu amasitha kd agwiririra ana anu
Walemba post -yi.Pofunika kumpatsa #MBUZI.Ndati ameneyuyu mbuzi.Eee! Walandira mbuzi bcoz of his poor headline.Ndati mbuziii!!!!!!
Malawi 24 is a joke
You guys are beyond stupid, I don’t knw hw we can call that, focus on your own business, leave the guy alone,,,, jealous, leave it to the zambians, who are u to judge people, idiots
Za ziiii don’t black mail him and telling people false information to he’ll with your artical bodza linakulowani osalemnba za nzeru bwanji
Malawi 24 does not know that prisons are reformatory place, they would love to see GK rot in jail: shame on u. No news to rpor?.
Kkkk oh
U are foolish is this how u insults our musicians? ? We welcome you people here nicely and have u forgotten that even maize u are getting here in Zambia??? Mwapya ba swine
kkkkkk ndi chibwi no plan awo amalenba..
Are we getting it for free? we are giving you money.
If a man who rapped a child or woman from Malawi was coming to make money in Zambia would you not want for fellow Zambians to know just to be safe?
It shows the kind of people U are…. it speaks volumes
Guys guys watch your tongue. manje mulankhula monyoza yawa abale athu aku Zambia, kumene kuli kupusa. zoonadi inu amalawi mulibe nzeru, zoona mungamasekelere zomwe alemba wa malawi24 ndithu, can’t u see this is no sense?? wanthu wenawa ndi ma imbwa (injaa)
Forsake. We have sent ZNS to block all maize movements to Malawi. We have enough cash. Muzafa na njala ba Nyau inu
u pple @ zambia u r stupit enough. why u follow malawi 24? r u malawian? stop & start to follow zambia 24 if u have foolish pple shame
Why follow a media house which has no physcal address?
wa malawi 24 nivipuwa kaili bizybizy mu yesha nawazanu kayili mu liveni chabe uyu kanene shaaaa wanthu wenangu wadabwisa
Iam a malawian please our zambian friends forgive and forger the page for posting such a stupid headline iam 100% sure they are just jealousy of him bcoz he has a talent that the man posted this will not have not evn in his next generation…forgive.
fuck u!!!!!! where is the conection btwm maize and kanene? foolish mxeeew!!!
Mwapya njala izakunyokolani….. infact what is in Malawi???
Enock Banda filekefye fo icons nyasaland fipuwa echo fyachulila, nachi president chabo ngachilelanda kwati tachakwata ameno kikkkkk Malawi 24 shameon you
Mercy Sinyangwe u have made me to smile big time
Mind you,you zambians ,you are the ones who turnished the image of Kaneni by speculating and arresting of him that he has defiled and today you are blaming the Malawians.who is to blame?
That’s why your president has told u to eat mbeba. …… am not surprised
kkkkk following
Kkkkkkkkkkkkkk people of the world
Walemba Ixi Ndi Mbuzi.
Childish page run by stupid idiots,so u don’t even know media ethics!Be professional
This page is out of order, only they know to post is lies and stupid things,
Exactly eish
Malawi 24, ngati mulibe nkhani ndibwino kungokhala
Therez no virgin in martenity ward, no innocent in jail,,, same as u admn of this page you are wicked,,, ulibe namzeru ndiwe chipuba,,nyandulee ubweza dziko pansi
chibwi no plan ….
Chimbwi no plan indeed,
Writers from Mozambique not malawi
Writers from Mozambique not malawi
Mwaonjeza guyz olembanu.
AMA MALAWI 24 PANU…PA MANU
kkkkkkkk…..koma eeeeeee
unfair,
Kkkkkkkkest Koma 24hrs!!!
Foolish admin
Malawi 24 do u really follow media ethics b4 u publish ur stories???…shame!
As if you are angels yourself munthu zinapita…….. After all you u dont even know the whole story of what really happened
This is total stupidity
Chabalakata
Malawians, you can really be very bad… Now I believe…. I think i will go flat out telling our Zambia artists to avoid Malawi as time goes. Lets see. Umfwiti mwauyu
this media source is unreliable & lacks substance in their reporting,just don’t be serious wth them,they just write anyhow…
Robbaa Twalibu, njala yachita…
Learn not to insult Robbaa Twalibu what have u benefitted from those insults
Nanunso ama news mukasowa zolemba kuli bwino muzingokhala chete… Mpaseni ulemu munthu wankulu general kanene… Sure iwe chocolate size 10 angakwane mu size one?
Check This Auto
No No No O O O O O Oooo!!!
This one guys sucks…….. Chotsani chonde
He is a gud guy! nimunyamata wabwino abale! Regards from Zambia
Kusowa cholemba eti?
Kkkk
Hahahahahaha..
Zandikhudza….
Mmmm Ma Guys A Mw 24 how do u write ur storie? Actually what angle,news values etc do u follow?
Sinnaonepo page ya bodza ngat iyi man aah….amatipaka bodza bwanj
Aaah these guyz amwene kaya utolankhan anakaphunzira kut
Aaah these guyz amwene kaya utolankhan anakaphunzira kut
apatu wamuphera nzako ufulu. ukumanya nthena??
This is too bad! Nkhani zinatha kalekale
pofuna kuipisa mbili yanga a malawi 24 alemba koma nikafuna kutchuka nitchuka nekha ala shatapu !! wajeno niwajeno ! akuti akanene niwarepist shatapu ! ife niwajeno tizaimba tinyimbo pamalawi kaya tizaona ka size 1 tizabaya ife niwajeno tifuna malawi muzaleko zaife wajeno
Does Kanene Rape Any Girl,anywhere & anyhow?
Ndekti chan
mucezeni bwino
Amwene mulibe natu
?
no nid to hid them akzapus azagwiridwe tchito
Umalakalaka utakhala jonournalist et?
Mmmm koma a MW 24 !!!! Kkkkkk
damage basi kkkk
Anzawo akupanga money kkkkkk
poti akazi akwathu kuno ndizomwe amafuna.
tiyeni waka uko Ku nanga mbiri zawanthu yayi ndimo mufwilenge nthena nthena wanyinu wakupanga ndalama
Wandiphuzitsa chitumbuka kkkkkkk zikomo
OKY,AZATIPEZA BASI
kklll tapulika