There will be a new face surely in the 2016/17 super league season and that is of Japanese midfielder Genki Nakamura who has penned a one year deal with Mighty Be Forward Wanderers.
The Japanese has been under scrutiny at the club ever since he came in months ago.
He has been centre of attraction lately and the technical panel has maintained that they have been impressed with him and remain upbeat he will be of great help in the campaigns this year.
Among other top signings, the 2015 Carlsberg Cup champions have made include roping in Azam Tigers goalie, Nenai Juwaya, rivals Nyasa Big Bullets ace, Jafali Chande and Peter Wadabwa from Silver Strikers.
Nakamura who has been involved in a number of friendly matches at the Lali Lubani side lately was reportedly chipped into the teams by their sponsors, a Japanese second car dealer-Be Forward.
Kikikikikikiki hahahahaha
Let hm battle n judge later!
Nakamura,wadabwa,zakazaka&derez rumourz thatN
Amakasewera socials ku Nsanama.
All the way from Japan kumazasewera mpila mmunda?
Nebayutu Osadandaula Nae Lakula Ndi Nsanje, Koma Mungandiuze Ngati Nebayu Anayamba Wapezapo Player Wakunja Pa Ulele? Kapena Nyerele Ndi Timu Yokondedwa Ndimaiko Ambiritu Eti, Nankha Mpaka Ku Japan !! Kwa Ine Ndingoti God Bless Manoma
Ndi Noma yokha imene imakwanisa kukhala ndi ma player akunja bas osat za a Neba kkkkkkkk kma Ground lakero nde eeeeee
No surprise the more we have them alover the country the more they got that chance. Welcome them……
Abale koma ground lo ayi uku ndi ku Malawi di.
alubinoyu siokudyanjokauyu beba ukaipezakuti sato kayatikuonerani,
mukufela kuyela muziwa BULLETS chakachino
Kodi kampopi ikuti chani?munayesera kulowa Khafu kaya mumati mkhafu.sanakakuwumbuzeni mwamanyazi uko?ku Malawi mpira kulibe.palibe kusekana apa.national team ndi yomweija mwaiwona ija.pa home mkumasewera ngati Thyolo police eaglez. VIVA ma Bankaz.timangosapotera kusowa chochita ma Weekend wa.
Pajatu inu a bb kwanu ndi kunyoza basi musiyeni tili ndi tecnical director amuona kuti agwira ntchito
Koma akanapita ku fodya bullets ndiye akanakhala mbambande sinchoncho?koma anyungwi inu simudzatheka basi. JERASI BASI NOMA MOTO KUTI BUUUUUU
Ok
He’s a nic player, welcome
Akabweranso Maplayer Aku Nigeria Aja Amaka Nebayu Koma.
Kodi inu aneba simukuvesa kwanu ndikuderera basi ija 6 munatipasa simukutipasa urem kkkkkkkkkkkkk ife kwathu ndikuthokoza bas
Pamupira zilibwino, muzamuwona kuipa akalowelela zandale.
Kodi nakamura wabwera kom mpwepwa zinazi abale
Kujapaniko amamenya wa m’makwalala uyu kuno team yake tingayelekeze ndi chikwawa medicuse kkkkkkkj
Napweri wa mmangochi uyu simungamve dzinalo kkkkkkkkkkkkk koma neba uphedwa chaka chino ndinapweri wanuyu kkkkkkkkkkk ziliko chaka chino
Koma ground lakero shamme
Season ndi ya2 iyiii
Hahahahahaha Japanese kwa neba kkkkkkk koma kwavuta.Player wabwino sangabwele kumalawi aaaaa izi ndinkhoko.
Ma China osauka kkkkk nanga ten amalandila anyamatawa iyeyu adzilandila yomwe?
Ma China osauka kkkkk nanga ten amalandila anyamatawa iyeyu adzilandila yomwe?
Kodi paja mjapanese amakhalanso mchina?
Shaolin soccer ndi mabaki ndi majudo aziloredwa nxt season kutentha..
Shaolin soccer ndi mabaki ndi majudo aziloredwa nxt season kutentha..
Enanu njiru. Tisamangoti m’malawi wagudwa kunja, nafenso tidziwagula olo zikhake mphwepwa kwaoko. Nanga a Malawi abwinowo ali kwaani? Angotinyidwa ati ndi ma professional players. Zausiru? Manoma ndakunyadirani
Enanu njiru. Tisamangoti m’malawi wagudwa kunja, nafenso tidziwagula olo zikhake mphwepwa kwaoko. Nanga a Malawi abwinowo ali kwaani? Angotinyidwa ati ndi ma professional players. Zausiru? Manoma ndakunyadirani
Kod Nakamurayo Adzasewera Nd Myendo 4 kapena Iwiri Yomweyo Nanga Chomumuopera Nchiyan?
Kkkkkk nsanje ndinapweliyu
Kkkkkk nsanje ndinapweliyu
Akapsa ndi zuwa uyo ku chikwawa
Akapsa ndi zuwa uyo ku chikwawa
kongomva kuti ndiwa ku japan bas akanakhala kuti ndi dolo pa chikopa ithink kuno sakanabwela komabe wachita bwino timuphunzisa
kongomva kuti ndiwa ku japan bas akanakhala kuti ndi dolo pa chikopa ithink kuno sakanabwela komabe wachita bwino timuphunzisa
Sighning fee ndi zıngati?
Sighning fee ndi zıngati?
payekha amati ndi proffy kkkkk hung ching
payekha amati ndi proffy kkkkk hung ching
changa ndi chisoni ku Noma chaka chino ulendo wa ku division basi Maulee more Fireeeeeeeeee
changa ndi chisoni ku Noma chaka chino ulendo wa ku division basi Maulee more Fireeeeeeeeee
mapesi akuJapan ndi Chimanga ku Malawi. Lets welcome this guys as Japan hasn’t seen any portetial in him. jst imagine, you know that he came at free data.
Zapatu basi
I lyk him.amatha koma kungoti anoma mumakonda wa phuphuphu.All the Genk.
I reserve my comment, but this Japanese name sounds lomwe-lomwe so!!! kkkkkkkkkk anyway permisssion granted
Super
akanakhala wabwino akana saina zaka 3
Chaka chino muzioma ngatimumapatsidwa mpatandizaka zwirizi koma chaka chino bb irimadzi wina arira malemu wanuunja mumati fodya uja aziona.
Machine anoma kkkkk muva kuwawa aneba
Kkkk bola asabwerese shouring socer
Shouring socer?????
neba wathu ndiwatsanje kwambiri inunso mutha kutenga ma player akunja amakuletsani ndi ndani,tsanje bas muzasiya lit tsanje zanudzo kod,mlibe manyazi takukanilani ife toto,azasova ndi defender wanu uyo opepera uyo kaya mumat fodya aziona chaka chake ndi chino kkkkkkk
Madolo Athu Akukamenya Ku Jon Ndi Mozamb Iye Akubwela Kuno NdiKape Uyu
Zaziiii
Zaziiii
CHAKA,CHINOMUZIONA.
CHAKA,CHINOMUZIONA.
Paja malawi 24 ndiyanoma eti…?
Ngat a Malawi sakutha,a bwere nakamulayo,olonso atapanga coach flames
Itwillnotchangenothing,tothefamilyofnyerere.nebourife.c.jelaskomauziona.
All the best manoma koma akazangoti mutu ukundipweteka chonde mukamukweze ndege mwamsanga maliro kudula
Paja mbwelera zanuzo zimathawa first round# 1year sikumukaikira kumeneko kkkkk
Ngati analephela kugolesa ku Nsanama ku machinga ndie azachinyaso kt???? spy ameneyi wa JICA malawi immigration wake up,Army Inteligent findout more about ths guy
ZAUCHITSILU BASI!
zitizo iwe?
Neba kkk
Neba kkk
You retarded?
akunena zopanda pakeo ndi adani athu ife eni tili pheeee! manoma basi
akunena zopanda pakeo ndi adani athu ife eni tili pheeee! manoma basi mpunga mpunga
football iyi sizafilimutu izi maspy nde kt chani?
football iyi sizafilimutu izi maspy nde kt chani?
football iyi sizafilimutu izi maspy nde kt chani?
uziona
Munthuyu atha kunena zoona inu,ameneyo watumidwa ndithu,player aliyese amafunitsitsa azikasewela ku spain,england,germany,italy etc ndakumvetsa mwina uspy wamapokonyole awo
One yr to train noma players Huu waah! Punch , kick kick more flying and scisors kicks the coming season
Ameneyo ndi mbola. Akutali sangathane ndi a Malawi abweleranso kwao within 1st round muonaso
Is this a football pitch or grazing ground for cattle?
What an April fools!
Machine bamboo
speed yakeyo akati vuuu honda mwana! Achina fodya ukwecheukweche season ino! Manoma4lyf.com
Kamadzi uyu
Machine bamboo
NEBA amakamira za ziii! Atsu anawakanika, nanji uyu mu hagh Huh, kkkkk
koma noma ine kundimvetsa kukoma
Palibe atakupatse uitenga wekha minyama yakoyo
Iyitu ndi Noma wakulu
Nakamula nakamula nakamula kkkkkkkkkkkkkkkk koma abale musandipase minyama ndi nakamula wanuyo
Neba kansanje kameneko
Neba kansanje kameneko
kkkkkkkk timuwonera maneu lino dziko lake