Nakamura signs for Nomads


Nakamura
Nakamura
Nakamura safe at Nomads.

There will be a new face surely in the 2016/17 super league season and that is of Japanese midfielder Genki Nakamura who has penned a one year deal with Mighty Be Forward Wanderers.

The Japanese has been under scrutiny at the club ever since he came in months ago.

He has been centre of attraction lately and the technical panel has maintained that they have been impressed with him and remain upbeat he will be of great help in the campaigns this year.

Among other top signings, the 2015 Carlsberg Cup champions have made include roping in Azam Tigers goalie, Nenai Juwaya, rivals Nyasa Big Bullets ace, Jafali Chande and Peter Wadabwa from Silver Strikers.

Nakamura who has been involved in a number of friendly matches at the Lali Lubani side lately  was reportedly chipped into the teams by their sponsors, a Japanese second car dealer-Be Forward.

96 thoughts on “Nakamura signs for Nomads

 1. Nebayutu Osadandaula Nae Lakula Ndi Nsanje, Koma Mungandiuze Ngati Nebayu Anayamba Wapezapo Player Wakunja Pa Ulele? Kapena Nyerele Ndi Timu Yokondedwa Ndimaiko Ambiritu Eti, Nankha Mpaka Ku Japan !! Kwa Ine Ndingoti God Bless Manoma

 2. Ndi Noma yokha imene imakwanisa kukhala ndi ma player akunja bas osat za a Neba kkkkkkkk kma Ground lakero nde eeeeee

 3. Kodi kampopi ikuti chani?munayesera kulowa Khafu kaya mumati mkhafu.sanakakuwumbuzeni mwamanyazi uko?ku Malawi mpira kulibe.palibe kusekana apa.national team ndi yomweija mwaiwona ija.pa home mkumasewera ngati Thyolo police eaglez. VIVA ma Bankaz.timangosapotera kusowa chochita ma Weekend wa.

 4. Koma akanapita ku fodya bullets ndiye akanakhala mbambande sinchoncho?koma anyungwi inu simudzatheka basi. JERASI BASI NOMA MOTO KUTI BUUUUUU

 5. Akabweranso Maplayer Aku Nigeria Aja Amaka Nebayu Koma.

 6. Kodi inu aneba simukuvesa kwanu ndikuderera basi ija 6 munatipasa simukutipasa urem kkkkkkkkkkkkk ife kwathu ndikuthokoza bas

 7. Napweri wa mmangochi uyu simungamve dzinalo kkkkkkkkkkkkk koma neba uphedwa chaka chino ndinapweri wanuyu kkkkkkkkkkk ziliko chaka chino

 8. Enanu njiru. Tisamangoti m’malawi wagudwa kunja, nafenso tidziwagula olo zikhake mphwepwa kwaoko. Nanga a Malawi abwinowo ali kwaani? Angotinyidwa ati ndi ma professional players. Zausiru? Manoma ndakunyadirani

 9. Enanu njiru. Tisamangoti m’malawi wagudwa kunja, nafenso tidziwagula olo zikhake mphwepwa kwaoko. Nanga a Malawi abwinowo ali kwaani? Angotinyidwa ati ndi ma professional players. Zausiru? Manoma ndakunyadirani

 10. Kod Nakamurayo Adzasewera Nd Myendo 4 kapena Iwiri Yomweyo Nanga Chomumuopera Nchiyan?

 11. kongomva kuti ndiwa ku japan bas akanakhala kuti ndi dolo pa chikopa ithink kuno sakanabwela komabe wachita bwino timuphunzisa

 12. kongomva kuti ndiwa ku japan bas akanakhala kuti ndi dolo pa chikopa ithink kuno sakanabwela komabe wachita bwino timuphunzisa

 13. mapesi akuJapan ndi Chimanga ku Malawi. Lets welcome this guys as Japan hasn’t seen any portetial in him. jst imagine, you know that he came at free data.

 14. Chaka chino muzioma ngatimumapatsidwa mpatandizaka zwirizi koma chaka chino bb irimadzi wina arira malemu wanuunja mumati fodya uja aziona.

 15. neba wathu ndiwatsanje kwambiri inunso mutha kutenga ma player akunja amakuletsani ndi ndani,tsanje bas muzasiya lit tsanje zanudzo kod,mlibe manyazi takukanilani ife toto,azasova ndi defender wanu uyo opepera uyo kaya mumat fodya aziona chaka chake ndi chino kkkkkkk

 16. Ngati analephela kugolesa ku Nsanama ku machinga ndie azachinyaso kt???? spy ameneyi wa JICA malawi immigration wake up,Army Inteligent findout more about ths guy

  1. Munthuyu atha kunena zoona inu,ameneyo watumidwa ndithu,player aliyese amafunitsitsa azikasewela ku spain,england,germany,italy etc ndakumvetsa mwina uspy wamapokonyole awo

Comments are closed.