Lilongwe first grade magistrate court has sentenced Julius Dalasoni, 42, to 14 years imprisonment for beating his wife.
Dalasoni found his wife, Selina Julias, 34, with another man in his house at Biwi in the capital city of Lilongwe.
After he caught the wife, Dalasoni severely beat her to the extent that she was failing to do anything.
In court, Lilongwe first grade magistrate sentenced Dalasoni to 14 years imprisonment with hard labour for committing an act intended to cause grievous harm, contrary to section 23 (A) of penal code.
The convict hails from Zidana village, Traditional Authority Phambala in Ntcheu.
Dziko lapasi linatembenuka guys, chabwino chnasanduka choipa pomwe choipa chinasanduka chabwino . satana ali paliwilo nafe tchejere nd mauufuluwa nd mawu ot democracy akumasusana nd mawu amulungu tsamale kwambri.
Mmalo mopanga za kwacha kumangomanga anthu ndi zinthu zoszmveka zopusa
moyo ngokondera pena
kupweteka mkaziwako mpaka 14yrs koma wokupha albino nde 4yrz zazii zenzen
Thats unfair court bwanji osaona zifukwa zomwe zayambitsa kuti mkazi amenyedwe komanpaka atengere mamuna wina nyumba nwake mkaziyo anaonjeza its you court mukulimbikitsa azimayi kuti adzitichitira mwano mabanjamu
Thats unfair court bwanji osaona zifukwa zomwe zayambitsa kuti mkazi amenyedwe komanpaka atengere mamuna wina nyumba nwake mkaziyo anaonjeza its you court mukulimbikitsa azimayi kuti adzitichitira mwano mabanjamu
sono inu a Boma zaka14 kaziyo muzimusamala ana ake muwalipilila schools fe
ngati akuluwa mwawa pasa 14yrs naga wa murder mumpasa zingati?
judge ameneyu ndiwa chipani cha DPP
14 years kumenyatu uuu apa mwawonjeza kwabasi ala
Ndende ndizaosauka bax
Amabungwe muli kuti please nkhaniyi muilowerere komanso amalamulo konzanipo pa milando yachigololo monga iyi kuti mabanja akhale aku Malawi akhale atanthauzo pa palibe chilungamo soka kwaiwe mkazi wachigololo wamangisa mwamuna wako zikuyendere
Banja lililonse limakhazikisa lamulo pakati pa uwiriwao palibe chifukwa chokwanira kumumaga mzibamboyu ingomusiyani akapitilize kusamala ana ake pamozi ndi banjalakelo
Banja lililonse limakhazikisa lamulo pakati pa uwiriwao palibe chifukwa chokwanira kumumaga mzibamboyu ingomusiyani akapitilize kusamala ana ake pamozi ndi banjalakelo
Akusowa chopanga aboma wa akulephera kugwira mbava zoba ndi futi komano akuchiona chompheka kumuyika mamuna nzawo ku ndende chonsecho mavuto awo am’banja sakuwadziwa angomvetsedwa zomwe zachitika panthawiyo,mamuna amakhala paukapolo wadzawoneni kuyesetsa kuti mkazi awoneke bwino,adye,avale so ndintchito yayikulu,ngati mkaziyo walakwa akuyenera chilango komwe anafusilanako abomanu kunalibe.
Ndiye mkaziyo amusamala ndan,kapena banja lathela pompo,14 yrs is 2much
Kodi abambowo alakwisa kumumenya nkazi wawoyo?
Iwe nkazi kumene uliko ukumva bwanji pamene wamangitsa amuna ako?
Nanga inu akumipandonu chilango mwaperekachi Kodi chikugwirizana ndi mulanduwu?
Mukanenera konko anyapala inu…
Ndi amene mmanyenga akazi aweni akawamenya muwamange eet. Zopanda pake mzafa nditu ufit ukadali.
Ndi amene mmanyenga akazi aweni akawamenya muwamange eet. Zopanda pake mzafa nditu ufit ukadali.
pamalo paja ndipofunika kumaonapo wekha I would also have done the same beating
Zaka zonsezo zopusa
14 years? But cashgaters are sentenced to 9 years.I hope gov gonna feed the wife and children
Ezi singathe if u keep on arresting men who beat their unsatisfied wives.
A lot of women out there ready for serious relationships. Now she will enjoy herself for the next 14 years. eeesh.
Love is blood akuziwana anthuwo & its a family not a coutship.komanso amuna ife timamenyedwa ndi azimayi koma simumapangapo kanthu pena timakokedwanso maliseche.aaah mpaka zaka 14,ndiye muzimudyesatu ndinu mkaziyo.
ai apolice nuso penapake mmalenga misala fukwa mkazi ngat wagwidwa cigololocho akuenela kukunthidwa kmanxo kumupacilisa katunduwake nde inu mukumanga munthu olokwilidwa chifukwa chani is dat fair?
So tell us more what should we do if we found our wife’s with another man?I hope you can’t say we should just loughing,kkkkkk
zovuta
Mulungu wafundo mzimayi ameneyo awona zina
Chidule mukapeza mkazi wanu akuchita chigololo thawanimo kakhaleni kwanokha ukwati mwauthetsa mukatero. Azimayiwa ndi ankhaza zoopsa
Amenewo amawerudza mlandowu anali pachibwenzi ndi nkaziyo ndiye akufuna kuti ankwatire mkaziyo.chifukwa mkaonesetsa pamenepo munthu ali ndi zaka 42 ndiye akakhala mu prison zaka 14 azampeza mkaziyo.azakhala ali ndi moyo munthuyo akudikira mwamuna wake.
Zakazosezo khani yake imenei, malamulo opusa awa akufunakut azimayi azipanga dara tikawamenya timangidwe iye zinamunyasa ndinkadzi wake anaenera kumuthira makofi kumene,
Mukumagamulila mantha or kut azimawo akukondeni? Inusotu ciweluzo cikukudikilani cigamulondinkhaniyi sizumatchana plz chaonanzako capita ukundiye kulowetsa umphawi mudziko nanga mukansunga zakazonsezi citukuko ciliponso pamenepa?
Basi, kuluza zonse nzanu. Komanso ma lamulo penapake
Basi, kuluza zonse nzanu. Komanso ma lamulo penapake
Zopusa azibambo ena naonso akumatimbidwa koma azimayi samangidwa chifukwa chiyani
Zopusa azibambo ena naonso akumatimbidwa koma azimayi samangidwa chifukwa chiyani
Koma zakazo zachuluka,,
Koma zakazo zachuluka,,
Dziko limakondela azimayi.
Kodi nanga zaka zonsezi bomboyo sanasiyeko ana kunyumbako?
all those years???? only beating???? pali nkhani ina yake.
if u dont know women r being empowered there is bias we men have lost our position given by God Himself those who worship devil has come to make us wives wives wl be men thats why they are trying to scare us na me aaa akagwere with there rights
This is very unfair anthu akuba ndi mfuti nkumapha anthuwa 1 year eee dziko lokondera ili
Tidzawona Masiku Omaliza
Pa nkhaniyi samayenera chilango chimenechi
But if it was a woman who hurts her husband,she couldnt spend even a single night in custody..
akhalira yomweyo yokondeledwayo,I was born to love a woman not to hurt her
ine ndamenyedwa makofi ndi mkaz wanga ngati mwana kuti nditulutse mawu ine manyaz kuti aneba angave…bwanji osamangako wangayi mkaz pliz …
Kkkkkkkk koma iwe usandisekese
nkhanza kwa Mayi
eee kumawaumbudza wena akujaila ngati mchimwene wako imya
Wina Owombera Anzake Ndi Mfut ali phee paufulu
Zopusa zitha liti kodi, 2 yrs wamafupa, 14yrs wolandidwa mkazi? Ma judge aku malawi siyani kuvala khonje wa curl kit kumutu mitu yanu itseguke.
Ma hule nonse, ma lawyer ndi ma judge akafuna katundu wanu charge from 1 million kuposera apo, akalephera myalutseni.
Zachamba munthu wogwilira 5 years womenya hule mpaka 14?