Malawian Man jailed for injuring adulterous wife

Prison

PrisonLilongwe first grade magistrate court has sentenced Julius Dalasoni, 42, to 14 years imprisonment for beating his wife.

Dalasoni found his wife, Selina Julias, 34, with another man in his house at Biwi in the capital city of Lilongwe.

After he caught the wife, Dalasoni severely beat her to the extent that she was failing to do anything.

In court, Lilongwe first grade magistrate sentenced Dalasoni to 14 years  imprisonment with hard labour for committing an act intended to cause grievous harm, contrary to section 23 (A) of penal code.

The convict hails from Zidana village, Traditional Authority Phambala in Ntcheu.

Advertisement

55 Comments

 1. Dziko lapasi linatembenuka guys, chabwino chnasanduka choipa pomwe choipa chinasanduka chabwino . satana ali paliwilo nafe tchejere nd mauufuluwa nd mawu ot democracy akumasusana nd mawu amulungu tsamale kwambri.

 2. Thats unfair court bwanji osaona zifukwa zomwe zayambitsa kuti mkazi amenyedwe komanpaka atengere mamuna wina nyumba nwake mkaziyo anaonjeza its you court mukulimbikitsa azimayi kuti adzitichitira mwano mabanjamu

 3. Thats unfair court bwanji osaona zifukwa zomwe zayambitsa kuti mkazi amenyedwe komanpaka atengere mamuna wina nyumba nwake mkaziyo anaonjeza its you court mukulimbikitsa azimayi kuti adzitichitira mwano mabanjamu

 4. Amabungwe muli kuti please nkhaniyi muilowerere komanso amalamulo konzanipo pa milando yachigololo monga iyi kuti mabanja akhale aku Malawi akhale atanthauzo pa palibe chilungamo soka kwaiwe mkazi wachigololo wamangisa mwamuna wako zikuyendere

 5. Banja lililonse limakhazikisa lamulo pakati pa uwiriwao palibe chifukwa chokwanira kumumaga mzibamboyu ingomusiyani akapitilize kusamala ana ake pamozi ndi banjalakelo

 6. Banja lililonse limakhazikisa lamulo pakati pa uwiriwao palibe chifukwa chokwanira kumumaga mzibamboyu ingomusiyani akapitilize kusamala ana ake pamozi ndi banjalakelo

 7. Akusowa chopanga aboma wa akulephera kugwira mbava zoba ndi futi komano akuchiona chompheka kumuyika mamuna nzawo ku ndende chonsecho mavuto awo am’banja sakuwadziwa angomvetsedwa zomwe zachitika panthawiyo,mamuna amakhala paukapolo wadzawoneni kuyesetsa kuti mkazi awoneke bwino,adye,avale so ndintchito yayikulu,ngati mkaziyo walakwa akuyenera chilango komwe anafusilanako abomanu kunalibe.

 8. Kodi abambowo alakwisa kumumenya nkazi wawoyo?
  Iwe nkazi kumene uliko ukumva bwanji pamene wamangitsa amuna ako?
  Nanga inu akumipandonu chilango mwaperekachi Kodi chikugwirizana ndi mulanduwu?
  Mukanenera konko anyapala inu…

 9. Ezi singathe if u keep on arresting men who beat their unsatisfied wives.

 10. Love is blood akuziwana anthuwo & its a family not a coutship.komanso amuna ife timamenyedwa ndi azimayi koma simumapangapo kanthu pena timakokedwanso maliseche.aaah mpaka zaka 14,ndiye muzimudyesatu ndinu mkaziyo.

 11. ai apolice nuso penapake mmalenga misala fukwa mkazi ngat wagwidwa cigololocho akuenela kukunthidwa kmanxo kumupacilisa katunduwake nde inu mukumanga munthu olokwilidwa chifukwa chani is dat fair?

 12. Chidule mukapeza mkazi wanu akuchita chigololo thawanimo kakhaleni kwanokha ukwati mwauthetsa mukatero. Azimayiwa ndi ankhaza zoopsa

 13. Amenewo amawerudza mlandowu anali pachibwenzi ndi nkaziyo ndiye akufuna kuti ankwatire mkaziyo.chifukwa mkaonesetsa pamenepo munthu ali ndi zaka 42 ndiye akakhala mu prison zaka 14 azampeza mkaziyo.azakhala ali ndi moyo munthuyo akudikira mwamuna wake.

 14. Zakazosezo khani yake imenei, malamulo opusa awa akufunakut azimayi azipanga dara tikawamenya timangidwe iye zinamunyasa ndinkadzi wake anaenera kumuthira makofi kumene,

 15. Mukumagamulila mantha or kut azimawo akukondeni? Inusotu ciweluzo cikukudikilani cigamulondinkhaniyi sizumatchana plz chaonanzako capita ukundiye kulowetsa umphawi mudziko nanga mukansunga zakazonsezi citukuko ciliponso pamenepa?

 16. if u dont know women r being empowered there is bias we men have lost our position given by God Himself those who worship devil has come to make us wives wives wl be men thats why they are trying to scare us na me aaa akagwere with there rights

 17. Zopusa zitha liti kodi, 2 yrs wamafupa, 14yrs wolandidwa mkazi? Ma judge aku malawi siyani kuvala khonje wa curl kit kumutu mitu yanu itseguke.

  Ma hule nonse, ma lawyer ndi ma judge akafuna katundu wanu charge from 1 million kuposera apo, akalephera myalutseni.

Comments are closed.