A Malawi Defence Force (MDF) soldier has been killed in action in the Democratic Republic of Congo during a United Nations mission following attacks by an unknown armed group on Sunday.
MDF public information officer Paul Chiphwanya confirmed the development saying Dyson William Mayawo, 50, was working as a Motor Man in Elingeti during the time of the ambush.
He was shot in the abdomen and was rushed to a hospital where he died due to excessive bleeding. Mayawo was based at Chilumba Barracks and was working as a staff sergeant in the department of Motor Platoon.
According to Amnesty international, in October alone a hundred people lost their lives in DRC which show an increment of attacks on civilians, men , women and children by rebel groups.
So Sad,R.I.P Sad.
Angonditumizako ine ku D.R.C Ko ndikathana nawo ine ndekha cifukwa akafuna kundiombela ndi zikaxanduka tculu m’paka ndkathana nawo oxe
but we shall on loosing soldiers till when?coz malawi is apeaceful country no fighting,bt our soldiers are stil dying.phindulake lilikt mose tiddayambira kuluza asirikali muja?
Abwino sakhalisa padziko. R I P
May his soul rest in peace , tikusowa sleeping banana ndinthabwala zako
U die a heros death we are proud of u by keeping piece in African continets shows hw serius u was with citizen protection RIP
Rip.
So u think its funny……??
R I P Ambuye odziwa kutonthoza atonthoze onse ofedwa.Once again R I P.
Ambuye asogoleleni azibale athuwo chifukwa tikudalira omwewo ndikupempha mzimu wanu uwafungatire amen R I p .
Rest In Peace my soldier. Will miss you. My condolences to the lost family….
Rest in peace!
We were together in ivory coast,he is very amicable person whom we could trust than anyone and he used to play Bawo as one of his favourite hobbies
May his soul rest in peace.
R I P mr Mayawo
It was written that èvèry1 will face the death.so that death isn’t stranger to us.l thìnk we will meet there,lshaallah.
Rnp
We need men like him, no retreat bt die hard,may his soul rest in peace.
Mzimu wanu uwuse mumtendele
Sidzikuyenela kukhala choncho,Ambuye atetezeleni ena otsala.May his soul rest in peace!
Died on duty!May his soul rest in peace!and God is going to take over his family for sure!
mmm! Nyengo zowawa kwa ife pamene zinthu sizili bwino ku MALWI, eish!
Rest in ertanal peace Mr mayao tikusowani kuthupi kuuzimu tilinanu limodzi
R l p
REST IN PEACE MR MAYAO
Puma bwino msilikali wathu
133 likes, what is it that you like?
Ukadziwa zikuthandiza cha??
Palibepo nkhani apa nde zakunkhondo ka mwasowa zokamba
Zopweteketsa Kwambiri, Koma Boma Litiganizire Anthu Akupanga Ma Retirement Koma Osapanga Reclute Bwanji? Ife Anyamata Tizingokha Mpakana Tiyambe Kuba?
Ambuye tetezani onse asilikali otsalawo kuti akwanilitse ntchito yawo,komanso landirani mzimu wa mmbale watbu mmanja mwanu,kwa abale ofedwa,limbani mtima monga mwa malemba oyera akunena..Mzimu wa Ssgt Muyao uuse mumtendere.
died on line of duty RIP
Shit happens good solder die in the bush Rip
Zot msilikali wafa kucongo wina mkumapanga like, zmenez mzokusangalatsani? R I P
His Soul Rest In Peace Amen.
Pepani ku banja losalaro! Kmabe ndim’mene zinakaenera kukhalira monga asilikali ankhondo mwachidziwikire aenera kufera kunkhondo mwamwai kunyumba ndio ntchito yao!!!!! Rip
Ife tibwelako no worry,mmawa ndimwana Wako,osamakamba zopusa ndibwino kuseka pa kamwa than kukamba za ziii,guys mains awo ndi amene Ali pompowo mark them!
Rip Dyson Mayao
RIP you died saving people
RIP
RIP MR MAYAWO ndife okhuzika pa imfa imeneyo choncho tingompepha ambuye wathu yesu khristu afungatire kwa asilikali amene adakali kumeneko komanso akukonzekera kupita
RIP my soldier salute
thats the risk they all take when they go there.
Masikwano zinalowa china basi.. Kale msilikali akamwalira ku nkhondo palibe amaziwa or akazi awo awomwalirawo mpaka asilikari enawo atazabwerako koma pano ndinu nomwe kuziwa..
is vry sad 2 died in other countrs wthout ferwell 2 hz famly.and moreover mukamalumbirsa asitkali dnt say ndzafera dzko langa jst say i swear dat i w’ll die in other countries.GOD FORGIVE YOU 4 WAT U OZ DON.
ambuye tetezan anthu anu
Oh God protect the Malawian solders that are there (R.I.P)
Ndizondikhudza kwambiri ngat m’malawi ! mulungu asunge otsala ndikuang’anira mzimu wa malemuwa!
kuteleku mukamaona asilikaliwa ifa yawo ndimeneyo basi or ku training amakaphuzira kupha muthu….komaso ibelieve enawo anathawa zawoyu ……..mukudabwa inu koteteza ilingatiso khondo pawokha zingawenga zikatopa zimathothola wachitetezo iwe. thats y amaenda mifuti yontchera amaziwa kuti do or die………kumapeto God guide my bro there or anailembetsa ifao
R I P a SSGT
We Malawians we dont care about our fel Malawians why…??
R.I.P
Ndalama idapha yesu,
may his soul rest in peace!!
And hv shocked with this the camp my young cc huby z my lord protect all malawias
RIP
..
Rip mr Mayao
RIP our soldier
Rip
Pamenepo timati Malawi kumamvutika ndipachimake.km choti muziwe moyo sangula ndi ndalama #patache anayimba kaya ndikumvutika amalawi ndie titha
may his soul rest in peace!
Rest in peace comrade
rest in pc mmh kma akuluakulu ngat nkhan yake il imeney yomakaphesa aslikal kumeneko kul bwno amalawi tsgmapteko ayambana okha athanaso okha ash! amalaw tthele khondo ya en ake?
Nde tikhalatu osauka, akabweratu akmagula magalimoto
Rest in peace Mr Mayao, our soldier
Kuli Boko haram?
part of their job
rest in peace,, yooo I’m shocked
Amen
Rip my bro
Think b4 u post ur comment, nxt tym will be u/ 2ur family, then tizaoneso ka comment kanu inu anzelu zambili? #RNP brother
Mulungu sataya wake keep on working hard mzomu wa sgn muyao uwuse muntendele
Abisalomu wafelanji…?
sorry
R.I.P zimachika
Kod nanu aboma mukutumiza ananu kutali bwanji osatumiza ma gwarada aku mocambiqu wo bwanj
Amene mukulemba zopusanu mulekeletu tatiyen tikhudzidwe tonse ngati amalawi (R I P)
May his soul rest in peace
Basi anavomera kufera dziko. Osati mulungu. Iyeso wanaphaposo ake
RIP Bigman the Nation has lost a small part of something Big but if it’ll keep on loosing its small parts by the end it will get lost …. So Malawians watch out!!!!!! tizifa macongoliza mkumakhalapobe akuchita mtopola zadala dala.
Soory Mhsrp
Anthu nose muli ndichifundo chifukwa ?awa aujeniwa afela zimene adalonje pamalamulo antchito ndidzafela dziko langa ndidzamenyela dziko langa nkhondo,mamuna mzako mpachulu ulinga utakwelapo ,kodi iyeyi wapha anthu angati ndipo wamenya angati kwawo kuno.Adalonjezana ndalama zankhaninkhani ndiboma ameneyu ndipo wapha anthu angati ku DRC kuti nayeso aphedwe wafela malonjezano ake ndi boma.akadalota sakadapita mwina chifundo tingapangile otsalawo komaso mkazi wake akwatiwa . Anthuwa anyanya kumenya anthu kumpila ndiye azifa kumene ena azilowako ntchito imeneyi
Rest in peace papa
Zibwerani amalawi kwathu kuno kulibe nkhondo.RIP.
Sheee! So sad
Akungofuna kuphetsa asitkali amayiko ena nkhondo yanj yosatha?nanunso a boma mumangosayinra zilizonse ngat m’dziko muno muamamenyedwa nkhondo bwanj?taonan a stikali a2 akuthera mayko ena.lyf en money whch is great.
R I P sir
R I P sir
Odya ndalamazo ali pheee! Nyambo mkukhala anthu achete. R I P
Ambuye Khalani Mbali Yawo Asilikaliwa Ife Tikudalila Omwewa Mzimu Wake Uuse Mutendele
Very Painfull,
Ause Ndi Eternal Peace
otsalawo angobwerako adzateteze nyanja yanthu kuno angayambe kulanda ena
Very Painful,,
Rest In Peace.
Vry concerned, may his soul rest in peace
Very sad guyz
Malawian soldiers r not strong
Very sad guyz
Rest In Peace Soldier tikabweza chipongwe chimenechi
speachless and concerned
R.I.P.
You have paid a soldiers dedt Mr Mayao!!! Oh you have gone so young. Rest In Peace!!!!
Very,very sorry.
napepe
bambo aga adali silikali wadziko ino akandifotokozera mene khondo imakhalira mayiko amosambiqur ndi luwanda amat zimakhala zopweteka gat waluza mzanu abuye abuye landilani mizimu ya asilikali owe anatisiya pa khondo komaso matenda awutse mutemdele amen
R. I. P
He is a hero,a hero dies at war.
Rest in peace sir
RIP MAYAWO
vry sad to we malawians.
Very sad news.
Eeeee mulungu anati nayo mitima anakakhala amunanu,mai bambo kapena abale anu munakamva bwanji kumakuwuzani ma comment opusa amene ena mukupelekawa umuthu ndiwofunika. Rip akubanja simathero azonse chiyambi cha moyo wina watsopano limbani mtima
Not gd at all.
sad, you’ll always bè rembered as a hero! Brevo malawian!!
we still wishng u,our bravity soldiers only the succes and all the best for the biggest job u’r doing there.But the soul of mr #Muyao rest in ertenal peace
GOD creating solder in DRC
RIP hero
Painful, to say bye to your loved ones with a smile and later bring tears in their lives! REST IN PEACE SOLDIER…..
Awalawi tiyeni tikhetse misozi,
Rest in peace
This is not a development, why cant you say “confirmed in an interview” MHSRIP
washosha yolakwika tibwela mwa revenge!
Better to die in war fighting for the peace of others than to die coz of sin for the lust of our body, (R.I.P)
Mmene Amkayamba Ntchito Amkadziwa Kut Anthu Ku Nkhondo Amakafako Or Mmene Amkapita Amkadziwa Zosez Nde Mukuopa Chani?? Wafa Basi Inuso Mudzafa Kaya Ngoz Or Kudwala Onani Za Moyo Wanu Lake Watseka,.
bwareraniko mungathe!ambuye randirani munthu wanuyo pepani aku banja.
Anthu anji okondandalama ifakuchta kuitsata.muthanose.
mmmmmm boss you have proved your ignorance!!!!…..
Ngatizakuwawa ukwele pamsana patchetche brow
wayiwala unaba ndalama pa74km kunjanji yamota ntchito mkusiya pomwepo simphavu yokonda ndalamayokhayokhayo?
Kkkkk!wandimaliza pokhapo brow.
Woyenda ndilupanga.azafanso ndilupanga.
kkk umadziwa ndati ndikukumbeso nawe
Ofalelo safamawa kond@mwawela waitha.
sured ndaku3la ixe
Kufa msilikali modzi pa ambush ndie kuti mwayesesa guys ndimene ndimaidziwila ambush-mo keep on fighting
R I P..the lord might be with your spirit..
Sad MHSRP
Soldier never die he jst go to heaven and regroup… R I P
God have mercy
my God bless our country.
Very Sad to all the malawians.
Very Sad us all.
Angati anali ochimwa ambuye awakhululukire bcz afa pofuna kuteteza anthu amene akuvutika(rest in peace)
Kill the ENEMY B4 he kills u. He may b 4got own principles.
HOW SURE R WE THAT THE SOULS REALLY REST IN PEACE AS WE SUGGEST?
Iwo analonjeza kuzamwalirira dziko lawo nanga bwanji akumwalirira ku drc rip
ziri bwino kwambiri ndiye ntchito imeneyo! wakhala ndi iwe.
Lord have mercy.
Lord have mercy.
u guys r f***kin insane,a soldier gets killed thats his job..this aint no f**kin nuz@all its bullshit!
RIP sir
He died in the line of duty, ndiye usilikaliwo
I lost my brother the moment he joined the Military, for obvious reasons! So,do we need to cry over this?
kumatchaja foni mwachangu ndibwino
Bushiri amadzutsatu anthu akufa, jst make some arrangements to set prayers.
Don’t make jokes with things of God! You may just attract a curse upon your life. Better just say your condolences, you can not mock men of God.
Unagwerapo mchimbuzi chokumba anapita kukuvuulaaa eti @ stevie
achimwene mzeru mulibe
Why ur saying thic
Aah musamdandaule wabwera dzulo ku chipatala I thnk sidathe misala yakeyo!
There is nothn wrong with steve!
Bushiri wake wabozayo… Kape weniwen
Mr Steve, av u bn to the mental hosp with a problem of psychatric? Seems u r a bit crazy. Judge ur comments b4 posting. This is uttery nonsense
kukhala msilikali kumafunika kulimba mtima makamaka mkazi chifukwa imfa imakhala pa mphuno pawo choncho mulungu adalitse ndi kulandira mzimu wawo amen.
ndi ntchito yao ameneo! Zimachitika R.I.P
R. I. P Soldier Walimbana Nako Kulimbana Kwabwino.
This is a loss to the nation…whether we like it or not..it takes a lot of money to train and keep these men and women in shape…..But we are not cowards…..we will fight for peace in DRC…palibe zoti azibwerako…thats betrayal to the peace of the region!!! May God guide all our soldiers in and outside the country for your bravery!!!!!!
Sad news
Mmmmm so painful RIP
Rest in peace buffalo
Ambuye landilan mzimu wa malemu Dyson Moyawo amene inu mwamukondetsetsa kut lero amve kuitana kwanu. We will ever miss you Chief Commanda
Rest in peace mdf
RIP Ssgt Mayawo we will miss you a lot
RIP OUR DEAR SOLDIER
Bola inu mwalembako zomveka anzanu nkhani yomweyi alemba kuti mudered kusiyana lusotu kumeneku
Deeply concerned
bring our soldier back home aziztimenya ku mpira osati ku d r c bi4 they all died pliz #boma
Only america is allowed to say briNg back our troops, not malawi. There is no reason for malawi to not help in drc
Rip soldier
death is an expectation to a soldier! RIP
R.R.P
Rest in peace mr Dyson
So Bad RIP
sory rest n peace
weak men die at home bt strong men die fightin on battlefield…R.I.P
well said
ngamo
Shame
Mwalowerera admin
Rest in peace. zopweteka kwambiri kwa ife achichepere wth a goal 2 be soldiers loosing u sir.
Forget about the animal n enjoy the meat brother,wat I mean is to be a soldier it means you will kill or to be killed boy anyway keep your dream to become the truth.
True bg.
peace keepin mission shaaaaaaaa
Sad achimwene
so sory to the family may his soul rest in peace
rip soldier man
BAD NEWS.
x0 xad indeed
ambuye atetezelen amalawi ali ku DRC Rest in peace mr Dyson mayao
afako angati? ndizomwe amapitira amenewo osadanda iyayi asilikali akamachepa ena azilembedwa ntchito mwina ulova utha.
dont say lyk dat. some1. z cryn has lost ha dad …dats nt lyf mi fynd
pang’ono pamenepo simuziwa kuti soka lawina ndi mwayi wawina ?pali a2 ena sanawatenge usilikali coz analibe ndalama ydishira ndiye akamatha amenewo osaukao azapeza mwayi wantchito pamenepo.
Machende ako wamva!!
????????????????
Ine zandiwawa kwambiri pamenepo R I P Commander
I heard that he was busy poking punani. RIP
Xo xad!!! Lip.
Zimachitika
Zosezo ndi peter wantarika
Zikugwirizana bwanji pamenepa?
hahaha ineso ndikudabwa koma abale
Enanu mkumalemba zopusa apa kamba koti kulibe abale anu.ife kuli azibale athu kumeneko,mulungu akusogoleleni inu muli ndi moyo.R.I.P
may god 4gv hz ppo!!
I can see many likes i dont know if they also feel sad or not………
Like ma bra sizithandauka kuti wachikonda only udziwe lero
like ndiye kuti wachikonda, wachita like yo nde wakonda imfayo, koma sibwino kupanga like death
upgrade ur vocabulary
mmm..nyamnyirenda it daznt min dat. somtymz 2 drop a comment,ukuwona kuchedwa xo u jst lyk n whn u lyk,u mek ur frnds to b aware kt kwachtka chna chake… wapulika?
Like can also be expressed as thanking the one who has posted the message to the public u moron
so sad…MAY HIS SOUL REST IN PEACE
rest in peace soldier boy! link up in the next episode!…….
Tipaseni nkhani ina asilikali amayenela kufa ku khondo kumene palibepo news pamenepa.
ulindizer koma?
Zomvesa chisoni
Eya zonvesadi chisoni
Am very sorry indeed
rest in peace mr mayawo we will miss u ku church being mkulu wa mpingo ku college my instructor ku ntchito my boss, till we meet again u have fought ur war,,,,,,,,,,,,,,,,,, rest in peace once again
Too bad, RIP
OH M.D.F KOMA NDIMENE ZIMAKHALIRA KU KHONDO ENA AMAFA
KOMA CHIMAFUNIKA NDIKUKONZEKA BASI AMENE ALI SILIKALI WAZIWA CHOMWE NDIKUNENA
he has created a chance for somebody,the consequences of this duty z to loss lyf
Stupid leaders are to blame 4 all these wars that never end. all they want is doing away with term limits.
R.i.p
R.I.P
Ndye wina kumtivuta kut mamuna wako ali ku DRC abwera nd 4m ngat samafako osaphweketsa ma sodier ndi zimenezi zilozanani kut akutumizeni
Sad!
RlP
thats what war is all about. tipatseni nkhani za muno mmalawi
iz this international?
Some people are heartless
Mulungu akukhululukire
You my friend. Have a backwards mindset
amakaimirira ndani?
we are all heartless
nawenso akukhululukire
Just as it is the case with your mindset
So sad.
nde recrutment ikuchedwatu,sibwenzi titapitako kumeneko….zandiwawa bwanji?
Amwene i’m so happy with your chewa slang.Mike seke katete zambia.
umakwana yamie
Thank U
Yamie Uli Bo.
thank u sir
uximvele chison mwana wang,ono wt ur nonsense coment.panganga ako plus
RIP
Kma ku DRC nkhondo idzathako,asrikali athuwo azbwerako angayambe kutmalizra tkudaliro omwewot ife kut nyanja yathu isalandidwe,,muuse mumtendere khobaa
Zopweteka kuti taluza m’bale,ndinali okhudzidwa pomva kuti ndiwa m’mudzi mwathu mweni-mweni. May his soul R.I.P
Shame.
Ndichifukwa chake mbali ya motor ndinkakana munthu udzigwila mfuti kunkhondo.R.I.P
thats do or die ndizomwe anasankha
Mayineeeeeee amuna anga
stupid joke
tchembere wankulu ngati iwe kupanda manyazi
Ankhale amuna ako ukanakhala ndi mphamvu mzolembela pa fb
Komanso ndamufufuza pa wall pake ndi single hule munthu mkulux2
i feel pitty for u unlucky gal,u just wish to have somebody and call him amunako?pray hard then mzotheka than kuyaluka chonchi
R.I.P de soldier
R I P
Ndizomwe analembesa kuti azafela anthu.RIP
Mhsrip
ubwino wake anadyelatu sizakunozi matata amangothera kupitila kumsika akazi aasilikali ukutu anzanu #tata 1wik yatheratu imagwira ntchito yake yeniyeni sizakuno tata kustadium Za zii
Mumayenda m’mbali asilikali aku Malawi… Mwazolowera kumatimenya ku mowa ndiku mpira..ntchito yanu ndi imeneyo..muyisova
Man Mwayankhula Muwonjeza Akanakhala Mbalewako Bwanji? Tose sitingakhale Ma Accountants Wamva Iwe?
Siukunama anthu oipa amenewa mpaka ndikumowa kumene eti man amawonjeza2
Samala chilipo chikukusata mwana wa njoka iwe udya batt!!
Tamvakale Iz Dzulo
Very sad inded
R.I.P
so sad to national
so sad
Dziko lapansi ndilovuta kwambiri, mizuyao ikautse muntendele .
R.l.p
sad indeed
May his soul rest in peace as his was keeping it.
Nanuso zolengeza zimenezi? Ndiwo usilikari umenewo
sad news
http://malawi24.Com/2015/11/13/escom-promises-more-blackouts/
bad news
So bad
Winaso or wadzulo uja?
Ndiwadzulo yemwe uja aunt
Kuteleku a mw 24 adziwa kumene oh.Ndmaona ngati wina kaya
Bola Asakhale Dzukulu Wangatu
R.I.P
Concerned
Mbola
Rip
R i p
Anasainira ameneyo.
So sad,,,rip
basi adzibwerako enawo nkhondo yanji yosatha ku congoko
R I P
so sad
So sorry,may his soul rest in internal peace