Malawian soldier killed in ambush

Advertisement
Dyson Mayao
Dyson Mayao
Killed in ambush

A Malawi Defence Force (MDF) soldier has been killed in action in the Democratic Republic of Congo during a United Nations mission following attacks by an unknown armed group on Sunday.

MDF public information officer Paul Chiphwanya confirmed the development saying Dyson William Mayawo, 50, was working as a Motor Man in Elingeti during the time of the ambush.

He was shot in the abdomen and was rushed to a hospital where he died due to excessive bleeding. Mayawo was based at Chilumba Barracks and was working as a staff sergeant in the department of Motor Platoon.

According to Amnesty international, in October alone a hundred people lost their lives in DRC which show an increment of attacks on civilians, men , women and children by rebel groups.

Advertisement

302 Comments

 1. Angonditumizako ine ku D.R.C Ko ndikathana nawo ine ndekha cifukwa akafuna kundiombela ndi zikaxanduka tculu m’paka ndkathana nawo oxe

 2. but we shall on loosing soldiers till when?coz malawi is apeaceful country no fighting,bt our soldiers are stil dying.phindulake lilikt mose tiddayambira kuluza asirikali muja?

 3. May his soul rest in peace , tikusowa sleeping banana ndinthabwala zako

 4. We were together in ivory coast,he is very amicable person whom we could trust than anyone and he used to play Bawo as one of his favourite hobbies

 5. It was written that èvèry1 will face the death.so that death isn’t stranger to us.l thìnk we will meet there,lshaallah.

 6. Ambuye tetezani onse asilikali otsalawo kuti akwanilitse ntchito yawo,komanso landirani mzimu wa mmbale watbu mmanja mwanu,kwa abale ofedwa,limbani mtima monga mwa malemba oyera akunena..Mzimu wa Ssgt Muyao uuse mumtendere.

 7. Pepani ku banja losalaro! Kmabe ndim’mene zinakaenera kukhalira monga asilikali ankhondo mwachidziwikire aenera kufera kunkhondo mwamwai kunyumba ndio ntchito yao!!!!! Rip

 8. Ife tibwelako no worry,mmawa ndimwana Wako,osamakamba zopusa ndibwino kuseka pa kamwa than kukamba za ziii,guys mains awo ndi amene Ali pompowo mark them!

 9. RIP MR MAYAWO ndife okhuzika pa imfa imeneyo choncho tingompepha ambuye wathu yesu khristu afungatire kwa asilikali amene adakali kumeneko komanso akukonzekera kupita

 10. Masikwano zinalowa china basi.. Kale msilikali akamwalira ku nkhondo palibe amaziwa or akazi awo awomwalirawo mpaka asilikari enawo atazabwerako koma pano ndinu nomwe kuziwa..

 11. is vry sad 2 died in other countrs wthout ferwell 2 hz famly.and moreover mukamalumbirsa asitkali dnt say ndzafera dzko langa jst say i swear dat i w’ll die in other countries.GOD FORGIVE YOU 4 WAT U OZ DON.

 12. kuteleku mukamaona asilikaliwa ifa yawo ndimeneyo basi or ku training amakaphuzira kupha muthu….komaso ibelieve enawo anathawa zawoyu ……..mukudabwa inu koteteza ilingatiso khondo pawokha zingawenga zikatopa zimathothola wachitetezo iwe. thats y amaenda mifuti yontchera amaziwa kuti do or die………kumapeto God guide my bro there or anailembetsa ifao

 13. We Malawians we dont care about our fel Malawians why…??

 14. Pamenepo timati Malawi kumamvutika ndipachimake.km choti muziwe moyo sangula ndi ndalama #patache anayimba kaya ndikumvutika amalawi ndie titha

 15. rest in pc mmh kma akuluakulu ngat nkhan yake il imeney yomakaphesa aslikal kumeneko kul bwno amalawi tsgmapteko ayambana okha athanaso okha ash! amalaw tthele khondo ya en ake?

 16. Think b4 u post ur comment, nxt tym will be u/ 2ur family, then tizaoneso ka comment kanu inu anzelu zambili? #RNP brother

 17. RIP Bigman the Nation has lost a small part of something Big but if it’ll keep on loosing its small parts by the end it will get lost …. So Malawians watch out!!!!!! tizifa macongoliza mkumakhalapobe akuchita mtopola zadala dala.

 18. Anthu nose muli ndichifundo chifukwa ?awa aujeniwa afela zimene adalonje pamalamulo antchito ndidzafela dziko langa ndidzamenyela dziko langa nkhondo,mamuna mzako mpachulu ulinga utakwelapo ,kodi iyeyi wapha anthu angati ndipo wamenya angati kwawo kuno.Adalonjezana ndalama zankhaninkhani ndiboma ameneyu ndipo wapha anthu angati ku DRC kuti nayeso aphedwe wafela malonjezano ake ndi boma.akadalota sakadapita mwina chifundo tingapangile otsalawo komaso mkazi wake akwatiwa . Anthuwa anyanya kumenya anthu kumpila ndiye azifa kumene ena azilowako ntchito imeneyi

 19. Akungofuna kuphetsa asitkali amayiko ena nkhondo yanj yosatha?nanunso a boma mumangosayinra zilizonse ngat m’dziko muno muamamenyedwa nkhondo bwanj?taonan a stikali a2 akuthera mayko ena.lyf en money whch is great.

 20. bambo aga adali silikali wadziko ino akandifotokozera mene khondo imakhalira mayiko amosambiqur ndi luwanda amat zimakhala zopweteka gat waluza mzanu abuye abuye landilani mizimu ya asilikali owe anatisiya pa khondo komaso matenda awutse mutemdele amen

 21. Eeeee mulungu anati nayo mitima anakakhala amunanu,mai bambo kapena abale anu munakamva bwanji kumakuwuzani ma comment opusa amene ena mukupelekawa umuthu ndiwofunika. Rip akubanja simathero azonse chiyambi cha moyo wina watsopano limbani mtima

 22. we still wishng u,our bravity soldiers only the succes and all the best for the biggest job u’r doing there.But the soul of mr #Muyao rest in ertenal peace

 23. Painful, to say bye to your loved ones with a smile and later bring tears in their lives! REST IN PEACE SOLDIER…..

 24. Mmene Amkayamba Ntchito Amkadziwa Kut Anthu Ku Nkhondo Amakafako Or Mmene Amkapita Amkadziwa Zosez Nde Mukuopa Chani?? Wafa Basi Inuso Mudzafa Kaya Ngoz Or Kudwala Onani Za Moyo Wanu Lake Watseka,.

  1. Don’t make jokes with things of God! You may just attract a curse upon your life. Better just say your condolences, you can not mock men of God.

  2. Mr Steve, av u bn to the mental hosp with a problem of psychatric? Seems u r a bit crazy. Judge ur comments b4 posting. This is uttery nonsense

 25. kukhala msilikali kumafunika kulimba mtima makamaka mkazi chifukwa imfa imakhala pa mphuno pawo choncho mulungu adalitse ndi kulandira mzimu wawo amen.

 26. R. I. P Soldier Walimbana Nako Kulimbana Kwabwino.

 27. This is a loss to the nation…whether we like it or not..it takes a lot of money to train and keep these men and women in shape…..But we are not cowards…..we will fight for peace in DRC…palibe zoti azibwerako…thats betrayal to the peace of the region!!! May God guide all our soldiers in and outside the country for your bravery!!!!!!

 28. Ambuye landilan mzimu wa malemu Dyson Moyawo amene inu mwamukondetsetsa kut lero amve kuitana kwanu. We will ever miss you Chief Commanda

  1. Forget about the animal n enjoy the meat brother,wat I mean is to be a soldier it means you will kill or to be killed boy anyway keep your dream to become the truth.

  1. pang’ono pamenepo simuziwa kuti soka lawina ndi mwayi wawina ?pali a2 ena sanawatenge usilikali coz analibe ndalama ydishira ndiye akamatha amenewo osaukao azapeza mwayi wantchito pamenepo.

  1. mmm..nyamnyirenda it daznt min dat. somtymz 2 drop a comment,ukuwona kuchedwa xo u jst lyk n whn u lyk,u mek ur frnds to b aware kt kwachtka chna chake… wapulika?

 29. rest in peace mr mayawo we will miss u ku church being mkulu wa mpingo ku college my instructor ku ntchito my boss, till we meet again u have fought ur war,,,,,,,,,,,,,,,,,, rest in peace once again

 30. OH M.D.F KOMA NDIMENE ZIMAKHALIRA KU KHONDO ENA AMAFA
  KOMA CHIMAFUNIKA NDIKUKONZEKA BASI AMENE ALI SILIKALI WAZIWA CHOMWE NDIKUNENA

 31. ubwino wake anadyelatu sizakunozi matata amangothera kupitila kumsika akazi aasilikali ukutu anzanu #tata 1wik yatheratu imagwira ntchito yake yeniyeni sizakuno tata kustadium Za zii

Comments are closed.