Chipwilikiti chidabuka kunyumba yachisoni ku Zomba
Chipwilikiti chidabuka kunyumba yachisoni pachipatala chachikulu cha Zomba pomwe achibale amatenga thupi la dalaiva yemwe adawomberedwa Lamulungu ndi apolisi ku 4 miles mu mzindawu. Ma dalaiva komanso anzake amalemuyi adatseka nsewu opita ku Blantyre pafupi… ...