Shammah Vocals wati mipingo ikhale patsogolo yolimbikitsa achinyamata zatsogolo labwino
M’modzi mwa anthu oyimba mdziko muno Shammah Vocals wapempha mipingo kuti ikhale patsogolo yochititsa misonkhano ya achinyamata kuti idziwalimbikitsa zatsogolo labwino la moyo wao. Shammah Vocals yemwe dzina lake leni leni ndi Shammah Sitola wayankhula… ...