Kumbukirani kupemphelera dziko lathu – Chakwera
Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera ati mpingo uli ndi gawo lalikulu kupemphelera dziko la Malawi ndi masomphenya ake. M'mawu awo pamene anakasonkhana nawo pa mwambo wa mapemphero ku mpingo wa Lingadzi CCAP mu… ...