Dzizimba! Bambo wamangidwa atanyamula bokosi lamaliro usiku
Bambo wina m’boma la Neno wamangidwa pomwe mzake wathawa kamba kopezeka atasenza mabokosi a maliro usiku omwe akuti sing'anga wina anawauza kuti asandutsidwa magalimoto. Malingana ndi lipoti la polisi lomwe tawona, womangidwayu ndi Christopher Manyika,… ...