Auzeni atulutsiretu manyaka a nyimbo zawo chifukwa ndikudza mwaukali – Onesimus
Katswiri oyimba nyimbo za uzimu Onesimus wachechenjeza oyimba anzake kuti atulutsiretu nyimbo zawo zolumpha moto zo, iyeyo asadadze ndiukali. Bambo Onesimus anena izi pamene amadziwisa mtundu wa Amalawi kuti atulutsa nyimbo yomwe itagwedeze dzikoli. “Auzeni… ...