Ayigwebanso, aifafantha, aithyola nsagwada noma ija
Season ndi kumadzulo ndithu. Kuyamba bwino sikuphelezela ku kumaliza bwino. Atathibulidwa pachiweru ndi Siliva, manoma aonanso malodza lero mu mzinda wa Mzuzu asilikali atawanyenyanyenya ndi jombo. Pa masewelo amene anachitikila pa bwalo la Mzuzu, anali… ...