Ayigwebanso, aifafantha, aithyola nsagwada noma ija

Advertisement

Season ndi kumadzulo ndithu. Kuyamba bwino sikuphelezela ku kumaliza bwino.

Atathibulidwa pachiweru ndi Siliva, manoma aonanso malodza lero mu mzinda wa Mzuzu asilikali atawanyenyanyenya ndi jombo.

Yakanthidwa Noma

Pa masewelo amene anachitikila pa bwalo la Mzuzu, anali mnyamata wa Moyale Timothy Nyirenda amene anaonetsa mbwadza a nyerere lero ndi kuwapangitsa kubuula ngati nkhumba yobayidwa mu nthiti ndi mkondo wa msilikali.

Iye anamwetsa chigoli pa mphindi 15 zokha kuti adzetse mdima ku banja la nyerere, sipanathe nthawi yochuluka kuti amwetsenso china kuti adetse malingaliro onse opitilila mu chikho cha FISD.

Advertisement

232 Comments

 1. iwe adm ndiwe nyapapi wamva basi ukuona nagti ife mpira sitimautsata, hhaha Noma forever axe ndiponso iwe ndi sapota wa kabwafu, mukasowa chochita muzingozikanda apa osati kunamiza anthu zausilu basi

 2. But how can Malawi 24 report about the match like this? These are jokes we crack in whatsapp group chats not a professional page like Malawi 24. It’s a shame, to say the least.

 3. Iwe admin sumazitsata wamva, ndi bwino kungokhara osamalemba nkhani, osati uzilemba mbwerera zakozi apa, maso anoma ali pa league, ngati sukudziwa, ndipo pomwe ndaonera ubulutu wako ukuphatikiza kuyamba bwino kwa mu league ndi ma cup

 4. hello everyone am happy sharing this with you, am not suppose to be doing this but i can’t hold back my joy so i have to share with you, you too can be help just as i was helped by Dr Odudu who cured me the HIV virus after suffering from it for some years and CD4 count was very low i was depressed, i was desperately in need of getting rid of it, but the ARVs were not helping so i was eager to contact Dr Odudu who gave me his herbal medicine, today as am posting this i am HIV negative, don’t hide your sickness or else your sickness will hide you, contact Dr Odudu today so that you see a reason to back through the years of your depression and smile to yourself, you can call or whatsap him with his number (+2349067902914)or email [email protected] , pardon me i offend you with this post, but i must share this good news

 5. Kkkkkkkk pamene simukumvetsetsa ndiye pati? Mwafa basi musachulutsepo ma excuse apa..! Munakakhala kuti mwawina bwenzi mukudandaula kuti chani? Team dzina lake player Black mamba, chonchi mungawine? Kkkkkkkk ukhwirii, Chiichi? Airtel Top 8, Carlsberg Kananji Cup, Fisd Challenge Cup.. izipsya mtima..! Chaka chino mwati wina samenya mpira ulele?

 6. “SEASON NDI KUMADZULO” NDE KUTI CHANI
  ZOTI IYI NDI FISD CUP SI LEGEA SIMUKUZIWA?
  APA ZAONETSELATU KUTI MPIRA SIMUWUTSATA BWINO SO DO MORE RESEARCH BEFORE POSTING TRASH LIKE THIS ONE
  “ANY WAY THE TEAM HAS LOST THE GAME,WE ARE OUT FROM THE CUP
  ITS TIME NOW TO CONCENTRATE MUCH ON THE LEGEA,ADD MORE EFFORT SO THAT THIS YEAR WE MUST TO GRAB THE LEGEA TITLE”

 7. Mukumawerenga bwanji nkhanizi? Wat am getting is What happened? The owner of this website (malawi24.com) has banned the autonomous system number (ASN) your IP address is in (21837) from accessing this website. Error 1005 Ray ID: 3abed724081129dd • 2017-10-11 03:47:51 UTC Access denied Cloudflare Ray ID: 3abed724081129dd Your IP: 107.167.112.4 Performance & security by Cloudflare

 8. Iwe admin wa Malawi 24, ndiwe galu kwambiri, ukuonetseratu mbaliyako. Ukuona ngati ituluka yokha Noma mu fisd cup? Kape weniweni iwe!

 9. Kudandaula za ma game atatu in 4 days ngati munasaina ma player 11 bwanji? Munasaina over 30 good players. You could rest some players for other games, especially the league game of Eagles because you are already in the comfort zone

  1. Mmmmmm,sory angakhale zili choncho kuti team imakhala ndi maplayer 30 ,koma team inailiyonse imakhala ndi maplayer owadalira, mpila wa ku malawi sidzatheka,

 10. all the nomard funz lets just accept the result ,we can not change yestaday bt we can change tomorow .lets plan well tomorow how we can beat moyale coz here we can use obseen language to the jernalist who has posted the story bt it wont change anything . u can complain in whatever way bt they wil be NO changes people wil be just louphing at you. It raining now to nomards, next time it wil be to our neba! PEPANI AKUBANJA PEPANI!

 11. Kkkkkkk admin yu amakoka chingambwe,champweteka ndithu coz iyi ndi fisd .Noma imatha zofuna za FAm zakwanilitsidwa koma tionetsanq ku League

 12. kkkk…angadandaule zoti Noma yamenya ma game ambiri in just few days koma dziwani kuti mpira ndi proffession that requires training now ngati amenya ma game ambiri ndiye zabwinozo chifukwa miyendo imakhala kuti sinazizile koma akakhalitsa miyendo imaluza skill, OK.. mukudandaula kuti mwaluza chifukwa cha kuchuluka ka ma game omwe mwamenya motsatana but my question is what if you made it? would you still be complaining about the number of games?

 13. When it comes to schedule yama games, I don’t like it here in Malawi how can we improve and play better .. for example a team playing three games in four days, I believe ndikumalawi kokha kumene timapanga zimenezo..

  1. Just so you know,this is so cuz of umphawi wama team akumalawi.its a financial challenge 4 our teams to travel to the central,north and south just to play with one team and come back again several times to play with the others that’s why for example when nomads goes to the north it will play with all the teams that side so that they dont have to come again,same for chitipa united,it will play all its fixtures vs south teams in one go.

 14. Unprofessional reporting,am not a noma fan, koma this reporting leaves a lot to be desired.which school of journalism did you go to???

  1. kkkk….. mistake yamzanu mwaiona chifukwa choti walemba zomveka akanakhala kut sanalembe zomveka simukanaona mistake ndie whatever chomwe tikuxiwa ndichot Noma yafa basi

 15. Game kaya ndi ya league kaya ndi cup ndi mpira basi, kuvomereza kuluza ndikovuta, but the fact is Noma ayifafantha yatuluka mu Fisd 2 kwa tetete.

 16. Ayiponda ,ayidula Mkosi Ma Cup Ndiamene alibho Kusiyanaso Ndilingi Caka Cokolola Maule Cakacino Simucinukha Cikho Olo Cimodz

 17. Sinali league mukanayamba mwafunsa kukhala ngati ozindikila koma muli mbuli pa mpira Admin Noma imasewera Fisd not league komanso it was tricky fixture anthu kusewera mpira loweluka Sunday kupuma Monday lokhaTuesday kusewelanso that’s not fair.

 18. ine sindimadabwa ndikaona ma nkhani zonyozazi zikuchuluka kuposa zoyamika adani ndi ambiri paja ntchentche zimakonda zinthu zoola

 19. ine sindimadabwa ndikaona nkhani zonyoza noma zikuchuluka kuposa zoyamika adani ndi ambiri paja ntchentche zimakonda zinthu zoola

 20. Musanamizire kuchuluka magame bro. ~ mwangonya nayo basi ~ nanga silver inakuphwisitsani ija munalinso ndimagame motsatizana ~ mukunamiza mwanaaaaa chani…ZAMANYAZI BWANJI? ~ nde nkumati chaka chino nchokolola ~ koma muziti chaka cholanditsa katundu wamunyumba..END OF THE CODE

  1. ungoonesa uchitsilu wako ndi masapota anzako,iwedi ndiogwila mu estate ya illovo eti,,,your coment show that u are indeed a savage,,think before droping a coment #myson_ntayamanja

 21. mwama team atchldwawo panalibe team yomwe inali ndi mwayi opuma nonse zifkwa zinali zofanana bwanji dandaulo lachoka ku team ya noma yokha ? ma team enawo panalbe yoluza ? a moyale akanalza dandauloli likanamveka ? kutopa kunali kwanonse , kuynda kwanonse , team yili yonse inali ndi magame zachitika vomelezani

 22. Mpira uwu siwa league Mr admin, it’s Fisd Challenge cup, nde mukukamba za season sizikugwirizana. Ife tili phee ndi 47 points, inuyo sizokayikitsa, tikudziwa team yanu hence chimtima kuwawa noma ikayiphula and kusangalala ikaluza. Komanso what type of fixture was this, 3 games in 4 days, nooooo!

  1. Eti amafuna anyamata athu atani ma game akenso akutali kokhakokha anatopa anyamata athu tawamvetsa ndithu. Fisd yo takusiilani tengani ndinu

  2. Aaa man, atipweteka koma , Saturday game. Sunday game , Monday ulendo waku Mzuzu and today game, matimu Ake akuluakulunso. They are not made of iron. They are prone to fatigue boss

  3. I know taluza koma the fixture was so tight, ndichomwe tikudandaula. Silver inatimenya, tinamvetsa koma apa nchifukwa choti ma players anatopa man.

  4. Hw many players dd u sign mukat maplayer anatopa? Infact mesa munkat munasigner cream yokhayokhA ndecmunalowetse enawo bwaa.. Mmm learn tu accept thngs

  5. Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk dont 4get last tym your rivals had also combinasions of the same issue 4 game in 1 week. During the funeral of Douglas Chilambo bullets forced to play game tikulila. (#DouglasChilambo mzimu wake uwuse m’tendere). Chilikwazako osamati tachigwile nyanga. U miss 3 cups woooooo!!! ;(;(;(;(

  6. Oluza Ali phee aganyu akutilamkhulira kuziwa kut njobvu zikamamenyana umavutika ndi udzu. Chitimu chimene chimawa psyesa anthu mtima pa Malawi pano mchimenechi. That’s why tikuti be forward, backward never kkk

  7. Kkkkkkkkkkk pamene simukumvetsetsa ndiye pati? Mwafa basi musachulutsepo ma excuse apa! Sam Jere ndi azinzakowo.. kudana ndikuudzidwa chilungamo kumeneko? Munakakhala kuti mwawina bwenzi mukudandaula kuti chani? Team dzina lake ? player Black mamba.. chonchi mungawine?kkkkkkkk ukhwirii, Chiichi? Airtel Top 8, Carlsberg Kananji Cup, Fisd Challenge Cup.. ? izipya mtima..! Admin, Chaka chino mwati wina samenya mpira ulele?

 23. Eeeeeeee koma admin iweyo ndewu sumaiopayi nde wati Neba amutani?????.I could be greatful if you would write in Capital laters edit pls!!!

 24. kkkkkkk neba mpaka kulira just bcoz aMW 22% apanga post pa air mmnnm sry mpira ndi choncho siingamawine team imodzi alwez

 25. Season ino Neba wangotipelekeza palibe kuwina any cup or spoon season ino wait Luso tv abwelenso ndi wheelbarrow ina next yr

 26. Mtola nkhani wa masewera ayenera kudzudzula ndondomeko za masewera… osamaima kumbuyo kwa team kamba koti matimu alipo ambiri. A noma simunawakonde, Silver -Eagles ndi Moyale sungasewere nawo mnyengo ya masiku atatu kuphatikiza mtunda wa Blantyre >Lilongwe >Mzuzu…. mwamva akulu….????

  1. Edwin, ngati ayenda wapansi kubwera kuno Ku Lilongwe komaso Ku Mzuzu? Muli ndi zima player zambiri nanga mmazisungiranji? OK pempho lamveka ma game onse atatu tikuwabwereza komwe kwanuko, 1 game per fortnight kuti mukonzekere kkkkkkk kkkkkkk kkkkkkk

  2. Im writing this for tomorrow…. we dont have to wait for a white man to give us a lesson…. where is the football body standing concerning this issue…??? Mm?? Do we have the nomands only in this war…? Give out sound topics osati kuima kuseri kwa team mapeto ake matimu ena sangachite bwino…. wamva iwe fisd…. kaya titi fisidi…. kkkkkk mtolankhani…kkkk

 27. Sunday munalikuti inu,yikawina simulankhula bwanji,believe me mupezeka muli nonkha pano,ine am out dislikin your page,useless, Palibe chanzelu munalembapo.

 28. Zachamba eti , iwe mpira umaudziwa? Pali team yomwe siyinaluzeko? Brazil inaluza 7-1 world cup kwawo komwe iwe unali kuti? Loose or win Noma for life

  1. Vuto la anthu ndi limenelo, #Noma ayikuzula, ayithesemula mpomwe iwe ukusangalala..
   Anyway inenso ndili mgulu la anthu ambili omwe akusangalalawo. Kkkkkkkk

 29. Munasewerapo mpira inu…? Ma game ngati awa ndi mitunda yomwe amzanuwo ayenda, nyengo mukuziona…? Mmalo mozuzula mpata wa masiku mukutero…? Palitu matimu ena zimafunika kuwamenyera ufulu…. munthu adzipuma… kukonzeka…. nanga mawa akadzakhala awo mudzatani…

  1. Tisatengere zoti timakwera timu iti…. osewera timafuna kupuma,,, kukonzekera mosiyana ndi timu inayo.. tizikonza bwino ndondomeko tisadikire mzungu….

  2. Nzeru mulibe mukulimbana ndi Noma , Noma yayenda kuchokera Ku Blantyre kupita Lilongwe kukasewera 2days kupuma Monday Tuesday kusewera mpira Moyale mukuikambayo sinayende inali pakwao

 30. Makhwala atsopano a NYERERE ,amene alowa m’malo mwa DD7 akuti ndi Mathews Sibale ndi Timothy Nyilenda.M’chigawo chapakati makhwalawa akupezeka ku area 47,kumpoto ali kukaning’ina.

 31. Zoremba zake zimenezi mkunama kut MALAWI 24 imapezeka mu AGMA HOUSE,atorankhani opanda ma ID,NO EDITORS & even laptop yake amaBena mu ndix ya m’bare wao waku Johns mkupanga kapage

Comments are closed.