Season ndi kumadzulo ndithu. Kuyamba bwino sikuphelezela ku kumaliza bwino.
Atathibulidwa pachiweru ndi Siliva, manoma aonanso malodza lero mu mzinda wa Mzuzu asilikali atawanyenyanyenya ndi jombo.
Pa masewelo amene anachitikila pa bwalo la Mzuzu, anali mnyamata wa Moyale Timothy Nyirenda amene anaonetsa mbwadza a nyerere lero ndi kuwapangitsa kubuula ngati nkhumba yobayidwa mu nthiti ndi mkondo wa msilikali.
Iye anamwetsa chigoli pa mphindi 15 zokha kuti adzetse mdima ku banja la nyerere, sipanathe nthawi yochuluka kuti amwetsenso china kuti adetse malingaliro onse opitilila mu chikho cha FISD.
232 thoughts on “Ayigwebanso, aifafantha, aithyola nsagwada noma ija”
Comments are closed.
iwe adm ndiwe nyapapi wamva basi ukuona nagti ife mpira sitimautsata, hhaha Noma forever axe ndiponso iwe ndi sapota wa kabwafu, mukasowa chochita muzingozikanda apa osati kunamiza anthu zausilu basi
kkkkkk kumamveranako chisoni amzanu akulira
NOMA 0MKACHIYANI KWA BANKERS ALIBE KALIKONSE 2017. NGATI ANKANAMA LAST YR INO NDI 2017 UMODZIUMODZI LOOK 4WRD
Hahahahaha ziliko cha chino
4 Days Magameatatu Olomutakhalainu Timu Iliyose Imakhalandi Fest 11yodalika Komaso Ma Big Game Okhaokha
uku ndiye kulemba mopusa uku..fokofu!!
Idakakhala yaludza ndi bullets panalibe khan apa
Ulemu pa ujeni Pako
Mmmmmmm mwaxwa zokamba eti team yayamba kuluza & noma
But how can Malawi 24 report about the match like this? These are jokes we crack in whatsapp group chats not a professional page like Malawi 24. It’s a shame, to say the least.
Yenda bwino neba,uyembekezerenso next year kkkkk
admin saonesa mbali, grow up and have some manners.
Kkkkkkkkk Admin sakuziwa kathu uuuuuuuuu 47 points no one come closer kkkkkkkkkk admin uyoooooooooo wagwera kuminga uuuuuuuuuuu
You have 10 boyfriends ,Yet when you pray you say “God bless my relationship” my sister, which relationship? Just say”God bless my Team”
yaluza yaluza bas akadawina bwez akut iwo ndimadolo ng’oooooooo akusinjani bas
Kodi zili choncho?
moyale balaks fc ikuchita kubeba kumastand
Congrats to mtopijo and the entire club
Wanyelele vomeleza skuti upusa
Iwe admin sumazitsata wamva, ndi bwino kungokhara osamalemba nkhani, osati uzilemba mbwerera zakozi apa, maso anoma ali pa league, ngati sukudziwa, ndipo pomwe ndaonera ubulutu wako ukuphatikiza kuyamba bwino kwa mu league ndi ma cup
Nde kuichotsa manotu kkkkkkkkk
Lack of proffesionalism among our reporters triggers the violences sometimes
Koma ikusogolera TNM super league .Noma woyeeeeeeeeeeeeeeeeee!
Poor mood of reporting
umapezeka kut uli mu group/page yomwe admin analekeza standard3 kkkkkkkkk fisd tiribe nayo ganyu koma super league
Kodi ndye kut inuyo a nyerere mumangofuna daily muziwina pa moyale? Kkkkkk
hello everyone am happy sharing this with you, am not suppose to be doing this but i can’t hold back my joy so i have to share with you, you too can be help just as i was helped by Dr Odudu who cured me the HIV virus after suffering from it for some years and CD4 count was very low i was depressed, i was desperately in need of getting rid of it, but the ARVs were not helping so i was eager to contact Dr Odudu who gave me his herbal medicine, today as am posting this i am HIV negative, don’t hide your sickness or else your sickness will hide you, contact Dr Odudu today so that you see a reason to back through the years of your depression and smile to yourself, you can call or whatsap him with his number (+2349067902914)or email [email protected] , pardon me i offend you with this post, but i must share this good news
sindikuonapo chanzeru kumachta post zinthu zopusa ngat zimenez it just show dat u got weak mind!
Kkkkkkkk pamene simukumvetsetsa ndiye pati? Mwafa basi musachulutsepo ma excuse apa..! Munakakhala kuti mwawina bwenzi mukudandaula kuti chani? Team dzina lake player Black mamba, chonchi mungawine? Kkkkkkkk ukhwirii, Chiichi? Airtel Top 8, Carlsberg Kananji Cup, Fisd Challenge Cup.. izipsya mtima..! Chaka chino mwati wina samenya mpira ulele?
INUNSO MUMAYIOPA? Nyerere NDI more
makape musapye mtima kwambili
nkhani ndiyakuti ayithudzura basi
Makape
huhuhu madzi achita katondo ku lali luban road neba Ahmed Nkwanda Grey
Ife achiyao timat Noma jila ajikasile soni, ajipomwele,, ajididiukwile,ajiliwete,ajikasile
Iwe umalemba za Malawi24..
Mbolo ya mako nyini ya mdala wako wamva eti
Mukamuoña #Timothy_Ñyireñda
Akagwele ameneyu
INU TAKHALAN CHETEEEE
Umbuli kwathu suzatha how can someone so called journalist write article in a poor way like this especially openly show his side, this is stupid
Eti kuwina noma osalemba ma status ake opusawa ayi koma kungoluza nde eeeh
Malembedwe osonyeza kuti olembayo ndi mdani wa Nomayo
Aichita bwino amayelekedwa kwabasi
Amuthidzimura neba
Zoonadi kuyamba bwino sikumaliza bwino
“SEASON NDI KUMADZULO” NDE KUTI CHANI
ZOTI IYI NDI FISD CUP SI LEGEA SIMUKUZIWA?
APA ZAONETSELATU KUTI MPIRA SIMUWUTSATA BWINO SO DO MORE RESEARCH BEFORE POSTING TRASH LIKE THIS ONE
“ANY WAY THE TEAM HAS LOST THE GAME,WE ARE OUT FROM THE CUP
ITS TIME NOW TO CONCENTRATE MUCH ON THE LEGEA,ADD MORE EFFORT SO THAT THIS YEAR WE MUST TO GRAB THE LEGEA TITLE”
Ntolakhani opusa iwe, unaphunzira kuti uzilemba like this. Get lost ndi bb yakoyo
Mukumawerenga bwanji nkhanizi? Wat am getting is What happened? The owner of this website (malawi24.com) has banned the autonomous system number (ASN) your IP address is in (21837) from accessing this website. Error 1005 Ray ID: 3abed724081129dd • 2017-10-11 03:47:51 UTC Access denied Cloudflare Ray ID: 3abed724081129dd Your IP: 107.167.112.4 Performance & security by Cloudflare
Iwe admin wa Malawi 24, ndiwe galu kwambiri, ukuonetseratu mbaliyako. Ukuona ngati ituluka yokha Noma mu fisd cup? Kape weniweni iwe!
Kudandaula za ma game atatu in 4 days ngati munasaina ma player 11 bwanji? Munasaina over 30 good players. You could rest some players for other games, especially the league game of Eagles because you are already in the comfort zone
Nde ilipo team yomwe imapita ku ground ndi ma player 30 .or 20 ?
Rotation Sir
Mmmmmm,sory angakhale zili choncho kuti team imakhala ndi maplayer 30 ,koma team inailiyonse imakhala ndi maplayer owadalira, mpila wa ku malawi sidzatheka,
Awa nd madeyadi ndthu.
Thanks Mr Hendrix Chanza
This is not a good point, kusewera MA game mondondozana chonchi it’s an insult to Noma
Sorry Gentlemen
Even if teams can regester 100 players, they can never all be in good shape
Iiiiii…..!
Kumamuthizimula Neba kut azipsa Ntima kkkkkk
all the nomard funz lets just accept the result ,we can not change yestaday bt we can change tomorow .lets plan well tomorow how we can beat moyale coz here we can use obseen language to the jernalist who has posted the story bt it wont change anything . u can complain in whatever way bt they wil be NO changes people wil be just louphing at you. It raining now to nomards, next time it wil be to our neba! PEPANI AKUBANJA PEPANI!
ZACHAMBA ET!
Kkkkkkk admin yu amakoka chingambwe,champweteka ndithu coz iyi ndi fisd .Noma imatha zofuna za FAm zakwanilitsidwa koma tionetsanq ku League
kkkk…angadandaule zoti Noma yamenya ma game ambiri in just few days koma dziwani kuti mpira ndi proffession that requires training now ngati amenya ma game ambiri ndiye zabwinozo chifukwa miyendo imakhala kuti sinazizile koma akakhalitsa miyendo imaluza skill, OK.. mukudandaula kuti mwaluza chifukwa cha kuchuluka ka ma game omwe mwamenya motsatana but my question is what if you made it? would you still be complaining about the number of games?
kkkkk mtola nkhani uyu ndi wa ganyu sindikaika
When it comes to schedule yama games, I don’t like it here in Malawi how can we improve and play better .. for example a team playing three games in four days, I believe ndikumalawi kokha kumene timapanga zimenezo..
Just so you know,this is so cuz of umphawi wama team akumalawi.its a financial challenge 4 our teams to travel to the central,north and south just to play with one team and come back again several times to play with the others that’s why for example when nomads goes to the north it will play with all the teams that side so that they dont have to come again,same for chitipa united,it will play all its fixtures vs south teams in one go.
Uhmm what happens with the gates money? I believe Amapanga makwacha ambiri
ayitosa mmaso
ATi ma game akutari okhaokha kkkkk amayenda wapasi? Aisosora afafantha aikudzura aithyora akutha aigaza neba umayenda mbari…..
Moyaleeee moto kuti buuuuuuu!!!!!!!! #Neba uzipsa mtima.
Kkkkkk,player ntchito yake ndiyosewera mpira even akumakhala ndi game dairy ndi ntchito yake,musanamizire kutopa akugwedanibe
Noma kkkkkkkkkkkkkkkkkk
Ndalankhula mwano apa ine? Ndangosekatu. Kkkkkk
kkkkkk ife maule kumva sekeseke
Kkkk! Ayikhwekhweleza
Unprofessional reporting,am not a noma fan, koma this reporting leaves a lot to be desired.which school of journalism did you go to???
sinkhan yomfusa xambil iwe kape et
Amuzazada nde wapsa mtima.
he did ask gud question umbuli ndi umene ukukupangisani kusaona mistake ya walemba nkhaniyi
kkkk….. mistake yamzanu mwaiona chifukwa choti walemba zomveka akanakhala kut sanalembe zomveka simukanaona mistake ndie whatever chomwe tikuxiwa ndichot Noma yafa basi
Game kaya ndi ya league kaya ndi cup ndi mpira basi, kuvomereza kuluza ndikovuta, but the fact is Noma ayifafantha yatuluka mu Fisd 2 kwa tetete.
pa ize noma ndi more
Bayikhwengweneska palibwe kkkkkkkkkk
Ma bulutu a FAM fixture yopusa
Next week mukipitaso Ku Mzuzu, mukodzedwatu
Ayifwenthulaso! Kkkkkk
Noma yango-booka ngat ndowa yotethetsela madzi… Kkkkkkkkk
Ayiponda ,ayidula Mkosi Ma Cup Ndiamene alibho Kusiyanaso Ndilingi Caka Cokolola Maule Cakacino Simucinukha Cikho Olo Cimodz
hahahaha ndakomoka,thileni madzi ine….!!!
Tikuthira chill
Sinali league mukanayamba mwafunsa kukhala ngati ozindikila koma muli mbuli pa mpira Admin Noma imasewera Fisd not league komanso it was tricky fixture anthu kusewera mpira loweluka Sunday kupuma Monday lokhaTuesday kusewelanso that’s not fair.
ine sindimadabwa ndikaona ma nkhani zonyozazi zikuchuluka kuposa zoyamika adani ndi ambiri paja ntchentche zimakonda zinthu zoola
ine sindimadabwa ndikaona nkhani zonyoza noma zikuchuluka kuposa zoyamika adani ndi ambiri paja ntchentche zimakonda zinthu zoola
Musanamizire kuchuluka magame bro. ~ mwangonya nayo basi ~ nanga silver inakuphwisitsani ija munalinso ndimagame motsatizana ~ mukunamiza mwanaaaaa chani…ZAMANYAZI BWANJI? ~ nde nkumati chaka chino nchokolola ~ koma muziti chaka cholanditsa katundu wamunyumba..END OF THE CODE
Shame on you
Nkhani..yake..it..
ungoonesa uchitsilu wako ndi masapota anzako,iwedi ndiogwila mu estate ya illovo eti,,,your coment show that u are indeed a savage,,think before droping a coment #myson_ntayamanja
Kkkkkkkkkkkk ku commenta kut neba azipsa mtima
Kodi mwati ayitemera kosathwaa???
Mukusangalala chani nanu inu? Ma cup onse akudutsani chopenyako ndiye APA mulimba?
mwama team atchldwawo panalibe team yomwe inali ndi mwayi opuma nonse zifkwa zinali zofanana bwanji dandaulo lachoka ku team ya noma yokha ? ma team enawo panalbe yoluza ? a moyale akanalza dandauloli likanamveka ? kutopa kunali kwanonse , kuynda kwanonse , team yili yonse inali ndi magame zachitika vomelezani
Moyale sinayende inali pakwao atopa bwanji?
kb inayenda ndikuwinaso team yomwe yakuchotsan mamba lero pakwawo pompo. neba akugagada
OOH My blue s
Mpira uwu siwa league Mr admin, it’s Fisd Challenge cup, nde mukukamba za season sizikugwirizana. Ife tili phee ndi 47 points, inuyo sizokayikitsa, tikudziwa team yanu hence chimtima kuwawa noma ikayiphula and kusangalala ikaluza. Komanso what type of fixture was this, 3 games in 4 days, nooooo!
admin ndiogulitsa ma memory card anyimbo kale sangazidziwe izi
Aaa, osadzudzula fixture yo bwanji. Olo kunjako , they can’t do that
Kkkkkk lero limenelo
Eti amafuna anyamata athu atani ma game akenso akutali kokhakokha anatopa anyamata athu tawamvetsa ndithu. Fisd yo takusiilani tengani ndinu
Sanatikonde apa
Kkkk koma akonda Moyare Barracks? I guess thats where you were heading to Mr S Jere.
Aaa man, atipweteka koma , Saturday game. Sunday game , Monday ulendo waku Mzuzu and today game, matimu Ake akuluakulunso. They are not made of iron. They are prone to fatigue boss
Kunoso ndikunja bwana. Mwamva sugar, three cups gone so far
I know taluza koma the fixture was so tight, ndichomwe tikudandaula. Silver inatimenya, tinamvetsa koma apa nchifukwa choti ma players anatopa man.
Hw many players dd u sign mukat maplayer anatopa? Infact mesa munkat munasigner cream yokhayokhA ndecmunalowetse enawo bwaa.. Mmm learn tu accept thngs
Ayifwafwanthabeeeeee ng’o
Ayaya Simunawa Lipire Ndiye Eeee Akwiya.
Mmene munaluza game yanu yoyamba ndi Silver munali mutatopa ?
Zavutapo apa Noma siyindisangalasepo chibadwire ine
Sam, ndiye bwanji simunawine ya Silver yo? Poti munali a fresh? Kkkkkkkkk
we accept defeat,not w@ ppo used 2 say,ok!!
Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk dont 4get last tym your rivals had also combinasions of the same issue 4 game in 1 week. During the funeral of Douglas Chilambo bullets forced to play game tikulila. (#DouglasChilambo mzimu wake uwuse m’tendere). Chilikwazako osamati tachigwile nyanga. U miss 3 cups woooooo!!! ;(;(;(;(
Ma Cup ku Noma kulibeko, ayamba kumamwera madzi mmbale. 3 cups gone kkkkk
apse mtima zeni-zeni—bola adatenga –Esau kanyenda ,Lucky malata nd Chester .apsemtimawo
Zatukusila
Oluza Ali phee aganyu akutilamkhulira kuziwa kut njobvu zikamamenyana umavutika ndi udzu. Chitimu chimene chimawa psyesa anthu mtima pa Malawi pano mchimenechi. That’s why tikuti be forward, backward never kkk
Kkkkkkkkkkk pamene simukumvetsetsa ndiye pati? Mwafa basi musachulutsepo ma excuse apa! Sam Jere ndi azinzakowo.. kudana ndikuudzidwa chilungamo kumeneko? Munakakhala kuti mwawina bwenzi mukudandaula kuti chani? Team dzina lake ? player Black mamba.. chonchi mungawine?kkkkkkkk ukhwirii, Chiichi? Airtel Top 8, Carlsberg Kananji Cup, Fisd Challenge Cup.. ? izipya mtima..! Admin, Chaka chino mwati wina samenya mpira ulele?
Kkkkk …iwe ndikapedi et season imakhala ya league bas
zinthu zavuta
Ngakhalee inee for lyf nomaaa
Ayimeta mpala opanda madzi kkkkkkkk
Lose or win is a football
Eeeeeeee koma admin iweyo ndewu sumaiopayi nde wati Neba amutani?????.I could be greatful if you would write in Capital laters edit pls!!!
kkkkkkk neba mpaka kulira just bcoz aMW 22% apanga post pa air mmnnm sry mpira ndi choncho siingamawine team imodzi alwez
Indeee mulimonsemo koma ndiya2 basi
Banja Lonse Kulira After Kugonja 2 kwa chilowere
Masiku sakoma onse
Pepa noma usovenge
Neba ndatopa kukupepesa alah.Kutha zankamwa iwe zikawagwela anzako.24 tiye nawo amazolowela fusek
Kkkkk NEBA AAAA AYAMBA KUWOCHA MACARA
Napepe
asanamizire kuchuluka kwa ma game ndi ntchito ya ma player imeneyo that’s why ma team amakhala ndi ma player ambiri,
Iwe olo yako team ungamenye silver, blue eagles moyale pa masiku anai, ganyu adzakupha , mtendere si nsima tu
Za chamba nde tikunenazo mzimenezi
Take it easy Neba there is chances of replay hahahaaaaa
Tamuuzani ameneyoo massahpusiii,akeee
Season ino Neba wangotipelekeza palibe kuwina any cup or spoon season ino wait Luso tv abwelenso ndi wheelbarrow ina next yr
Aaaaah…masapota a PP awa. Amayi anakuthawani, mukulephera kupeza mtsogoleri mpaka pano.
Hahahaha Koma abwana mwandizutsa bwino kwabasi.
Kkkkkk another pesticides for killing ant is called moyale
kkkkkk
Nkhani za mpira zimakoma koma malembedwe awa ngaziwanda.
mmmmmh uthenga ngati uwu ndiwofunikila kwabasi plz tawusungani pa bwino
Asova
Malawi 24 go back to xool, atola nkhan osasamba inu nthawi yonsey munali kut mwadziwa lelo kut noma inali ndimasewero?
Page iyi ndi ya anthu a bullets ihope
osadanda Neba
Hahahahha neba sindikudanda ine aaaa
zachitika kkkkkkkk
Kikkkkkk olo siife oyamba
Ikawina simulemba zanuzo zonyogodola Malawi 24 shatapu zanu
ulendo uno isewela yabuli chifukwa super league ndi ya Bullets kapena Silver Nyau fc
Kkkkkkkk inu Manoma samatha mpira inu !!!!!
Wayikama Yachitamanyaz Yapepela Mwaonekelatu Anamikodzo Fc (noma)
Takhalani amzeru nanu a24 news..Team yisewer bwanji maGame atatu mosatizana..nonsense..!!!
Mmene mumaluza ndi silver munali mutamenya yakuti popeza inali game yoyamba muli fresh kkkkkkkkkkkkkkk?
Mukumva nyu nyu nyu
Kkkkk akulira ?????
Tieni nayo TNM..5points gap..kkkkk
Nzokoma nyerere zake zikuchita kudyeka bwino kuposa ngumbi.
Hahahahaaaaaaaaa you nailed it bra yooooooo this is comment of the yr!
I can feel the beat, kuli nye nye nye, kuli nyerere ku manoma!
Hahahaaaaaaa hey buddy you make me crazy laughing alone at this hour pls stop it!.
amugwebabe kkkkkk koma ine ndimadabwa tu kut lero simulembaso kut aigweba
Mtola nkhani wa masewera ayenera kudzudzula ndondomeko za masewera… osamaima kumbuyo kwa team kamba koti matimu alipo ambiri. A noma simunawakonde, Silver -Eagles ndi Moyale sungasewere nawo mnyengo ya masiku atatu kuphatikiza mtunda wa Blantyre >Lilongwe >Mzuzu…. mwamva akulu….????
Man KB inasewera ndi Bullets, kenako ndikumenya ndi BT United osapuma ulendo ku Mzuzu ndikukang’amba Moyale
Dandaulo lanu lamveka ndipo FAM yasitha masewero anu mubwelezanano tsiku lomwe mungakonde ????
kikikikkkkk
Awuzeni man, atolankhani wosazitsata
Edwin, ngati ayenda wapansi kubwera kuno Ku Lilongwe komaso Ku Mzuzu? Muli ndi zima player zambiri nanga mmazisungiranji? OK pempho lamveka ma game onse atatu tikuwabwereza komwe kwanuko, 1 game per fortnight kuti mukonzekere kkkkkkk kkkkkkk kkkkkkk
Kuonetsa ngati anthu ozindikila koma Ali mbuli
Im writing this for tomorrow…. we dont have to wait for a white man to give us a lesson…. where is the football body standing concerning this issue…??? Mm?? Do we have the nomands only in this war…? Give out sound topics osati kuima kuseri kwa team mapeto ake matimu ena sangachite bwino…. wamva iwe fisd…. kaya titi fisidi…. kkkkkk mtolankhani…kkkk
Za mpira izi…kkkkk….. ena masapota oziwa kuvina… ena kugenda.. ena kutsata malamulo… sungawamvetse….kkk
Ya biba noma
vomelezani kuti mwagwila mpita.Komaso moyale munkati ndi akazi anu….Shame!!!!!!
hahahah paja team imasainitsa ma player angat.,? Mwat osewa amasewera mmh kayaa. usovenge neba
Kkkkkkk hahaha
kkkkkkkkk kutuluka cha mutu pepa
Sunday munalikuti inu,yikawina simulankhula bwanji,believe me mupezeka muli nonkha pano,ine am out dislikin your page,useless, Palibe chanzelu munalembapo.
Ife we still lyking the page ikubhebha
Kkkkkkkkk mene ikubhebhera ukanaziwa iwe? Eishhh!
Ana achepa
Zachamba eti , iwe mpira umaudziwa? Pali team yomwe siyinaluzeko? Brazil inaluza 7-1 world cup kwawo komwe iwe unali kuti? Loose or win Noma for life
Tamangoliran nanu mwafa apa will
Ilipo, Noma
Vuto siyiweyo koma kochokera@Harrid
kkkkkk malawi24 hahaha ndakomoka…mwati aitani nyerere
Vuto la anthu ndi limenelo, #Noma ayikuzula, ayithesemula mpomwe iwe ukusangalala..
Anyway inenso ndili mgulu la anthu ambili omwe akusangalalawo. Kkkkkkkk
kkkkkkk ayifafantha…kuigwritsa magobo
Ayiphwetsemula 2 – 0 kkk
kkkkk okodzera pagolo anaxowa
Eshii
Eeeee…..komaso nde ayitu. Kkkkkk
Breaking news
kkkkkk what a fantastic story
iwe pa thokomela pako spayenda bwino
Munasewerapo mpira inu…? Ma game ngati awa ndi mitunda yomwe amzanuwo ayenda, nyengo mukuziona…? Mmalo mozuzula mpata wa masiku mukutero…? Palitu matimu ena zimafunika kuwamenyera ufulu…. munthu adzipuma… kukonzeka…. nanga mawa akadzakhala awo mudzatani…
Zako izo neba
Palibe excuse ifeyo mpira timamenya 3 games per day ukakamba zamasiku vomerezan
Tisatengere zoti timakwera timu iti…. osewera timafuna kupuma,,, kukonzekera mosiyana ndi timu inayo.. tizikonza bwino ndondomeko tisadikire mzungu….
Nzeru mulibe mukulimbana ndi Noma , Noma yayenda kuchokera Ku Blantyre kupita Lilongwe kukasewera 2days kupuma Monday Tuesday kusewera mpira Moyale mukuikambayo sinayende inali pakwao
Kkkkkkkkkkkkk Patricia, ngati mulibe zolankhula osangokhala pheee bwanji? Munamenyapo mpira inu?
Kmatu mudakawina sibwezi mukudadaula zoti simunapume kkkk just accept de defeat
Nyerere zatikitidwa ndi combat boots
Makhwala atsopano a NYERERE ,amene alowa m’malo mwa DD7 akuti ndi Mathews Sibale ndi Timothy Nyilenda.M’chigawo chapakati makhwalawa akupezeka ku area 47,kumpoto ali kukaning’ina.
Kkkkkkkkkkkk fon # piliz
Zoremba zake zimenezi mkunama kut MALAWI 24 imapezeka mu AGMA HOUSE,atorankhani opanda ma ID,NO EDITORS & even laptop yake amaBena mu ndix ya m’bare wao waku Johns mkupanga kapage
ndimaopa kunena izi ndimayesa ndikuzidziwa ndekha
Tangovomerani kuluza osalimbana ndi atolankhani kkkkkkk
Atorankhani m’nga ZODIAK & Times basi osati Malawi24 ndimakape
Hahahahaha!Nkhani imeneyi ikundisangalatsa bwanji!
Wanoma pompo kukomoka kkk
kkkkkk
auzeni anvesese
Koma ma reporter inu 24 muli ndi mavuto ambili
Azifwafwantha
Malawi24 ndi number 1,ndemwati azitani nyererezo???