
A Joyce Banda akuwonelera zisankho m’dziko la Nigeria
Mtsogoleri wakale wa dziko la Malawi a Joyce Banda ali m'dziko la Nigeria komwe akutsogolera nthumwi 40 zochokera maiko osiyana siyana padziko lonse kuwonelera zisankho zomwe zikuchitika m'dzikolo. Banda wauza Malawi24 kuti mabungwe a National… ...