Mzuni itsekulira pa 19 m’malo mwapa 12 February
Sukulu ya ukachenjede ya Mzuzu yalengeza kuti ophunzira omwe akupitiliza maphunzilo pasukuluyi adzayamba maphunzilo awo amchigawo choyamba lolemba pa 19 February 2024 m'malo mwa pa 12 February. Kudzera mchikalata chomwe Malawi24 yaona, sukuluyi ikudziwitsa anthu… ...