Munandilangizadi aMalawi koma ine kusava – walira Tay Grin
Pomwe Mutale Mwanza wanenetsa kuti sanakhalepo pa ubwenzi ndi Tay Grin yemwe akuti ndi khanda komaso samatha kukonda mkazi, “mfumu ya zinyawu-yi” yati ikunong'oneza bondo posavera malangizo omwe anthu ankayipatsa kuti isachite chibwezi ndi nkazi… ...