Abida Mia akapikisana nawo pampando wa wachiwiri kwa wachiwiri kwa mtsogoleri wachipani cha MCP
Phungu wa ku nyumba ya malamulo m'dera la Chikwawa Nkombezi, Abida Mia, abwera poyera kuti akapikisana nawo pa mpando wa wachiwiri kwa wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipani cha Malawi Congress (MCP) pansonkhano waukulu wachipani omwe… ...