
Boma liyimitse kaye kusamutsa aphunzitsi otsogolera ziwonetselo – Kamlepo
Kamlepo Kalua phungu wa dera la Rumphi East wafunsa mtsogoleri wa zokambirana mnyumba ya malamulo yemwenso ndi nduna ya maboma aang'ono, Richard Chimwendo Banda kuti ataganizira kuthandizirapo kuyimitsa kusamutsidwa kwa ogwira ntchito m'boma omwe ankatsogolera… ...