Achenjezeni a Mutharika, JB akubwela kuzayima pa zisankho za 2019
A PP kodi mulipo? Pitani ku maofesi a chipani chanu chifukwa Mtsogoleri wanu ati akubwera ndipo 2019 akhala akupikisana nawo pa chisankho. Malinga ndi malipoti a olemba nkhani, Mayi Banda alengeza zoti azapikisana nawo pa… ...