Dziko lino lili pa chiopsezo cholandiraso namondwe
Nthambi yowona za nyengo yati pali kuthekera koti namondwe yemwe akuyembekezeka kubadwa mnyanja ya m'chere ya India, akhoza kudzafika kapena kuyandikira kum'mwera kwa dziko lino. Malinga ndi nthambiyi, Namondweyu sanabadwe koma akuyembekezeka kubadwa mu Nyanja… ...