Ogwira ntchito ku khonsolo ya Balaka akwiya ndi kuchedwa kwa malipiro
Ogwira ntchito mu nthambi zosiyanasiyana za boma ku khonsolo ya Balaka mam'mawa uno akhamukira ku ofesi za Khonsolo ya bomali ati kamba ka kusakondwa ndi kuchedwa kwa malipiro a mwezi wa May. Ogwira ntchitowa ati… ...