Boma lati layamba ntchito yogawa ufa ku maanja okhudzidwa ndi njala
Boma kudzera ku Nthambi Yoona za Ngozi Zogwa Mwadzidzidzi (DoDMA) tsopano layamba ntchito yogawa ufa ku maanja omwe akhudzidwa ndi njala m'dziko muno pansi pa ndondomeko ya Lean Season Response. Malingana ndi DoDMA, ntchitoyi yakhazikitsidwa… ...