Ogwira ntchito pakalembera wa umzika apanga m’bindikiro
Anthu omwe anagwira ntchito pa kalembera wa chiphaso cha umzika mchaka cha 2017, ati apanga m'bindikilo sabata yamawa pofuna kukakamiza akuluakulu a bungwe la UNDP komaso boma kuwapatsa ndalama zawo zina. Izi ndimalingana ndi wachiwiri… ...