Apolisi ku Machinga akhazikitsa makomiti owona zachitetezo cha m’madera
Apolisi m'boma la Machinga akhazikitsa makomiti owona zachitetezo cha m'madera a kumidzi m'bomalo pofuna kuchepetsa umbava ndi umbanda munyengo ino yachikondwelero cha khirisimasi komanso chaka chatsopano. Poyankhula pamwambo omwe amakhadzikitsa komiti yowoona zachitetedzo chamadera akumudzi… ...