Mtsikana wa zaka 17 apha mwana pofuna kukwanilitsa chizimba
Malodza! Mtsikana wa zaka 17 ali m’manja mwa apolisi ku Lilongwe pomuganizira kuti wapha mwana wa zaka 10 pofuna kukwanilitsa chizimba chomwe anauzidwa ndi chibwenzi chake pa masamba anchezo. Wofalitsa nkhani pa polisi ya Lingadzi… ...