Odwala korona ku Chikwawa apempha chilungamo kuchokera ku Boma
Wachinyamata waku Chikwawa amene boma lidalengeza kuti wapezeka ndimatenda a Covid-19 wapempha boma kuti limuwuze zowona ngatidi alindi nthendayi chifukwa iye akukhulupilira kuti adanamizidwa za matendawa. Wachinyamatayu Ismael Maluwa yemwe amakhala kwa Ngabu ndipo amayankhula… ...