Apolisi adzudzulidwa pomanga a Namiwa mwankhanza
M’modzi mwa anthu omwe amayankhulapo pankhani zokhudza chitetezo cha mdziko a Sherrif Kaisi adzudzula apolisi kaamba komanga omenyera ufulu a Sylvester Namiwa mwankhanza. A Namiwa amangidwa Lachitatu pomwe amatsogolera zionetsero zomwe cholinga chaka chinali kufuna… ...