
Mfumu Mwanyanja yaphedwa poiganizira kuti ndi mfiti
Apolisi m'boma la Chitipa akhazikitsa ntchito yosakasaka amaliwongo osadziwika omwe apha mfumu Mwanyanja, m'dera la mfumu yaikulu Nthalire m'bomalo. Gladwell Msimwaka, Mneneri wa apolisi ku Chitipa ndiye watsimikiza za nkhaniyi ponena kuti mfumu Mwanyanja, yomwe… ...