![Malawi24.com](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2016/10/Malawi-24-235x176.png)
Ayaya amwalira atadwala nsana
M'modzi mwa madokotala azitsamba odziwika bwino mdziko muno, mai Bwanali am’boma la Neno omwe amadziwika ndi dzina loti Ayaya amwalira. Malingana ndi khansala wa dera la Lisungwi m’boma la Neno a Mark Ngwangwa, mai Bwanali… ...