![](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2023/09/Mkulu-wina-mboma-la-Mulanje-waona-mbonawona-atakanilira-panyumba-yomwe-anapita-kuti-akabe-katundu-mbandakucha-walero-235x176.jpg)
Bambo wakanilira atapita kokaba
Mkulu wina m’boma la Mulanje waona mbonawona atakanilira panyumba yomwe anapita kuti akabe katundu m’bandakucha walero. Izi ndi malingana ndi kanema yemwe anthu akugawana m’masamba anchezo yemwe akuonetsa mkuluyu atavala kabudula wankati yekha atakanilira pa… ...