Ndimatchaja K34 miliyoni – Zani Challe watutumutsa anthu
…akuti samapanga chibwezi ndi azibambo obowoka mthumba Pomwe amayi oyendayenda ena akumatchaja ma K1000 komanso ma K2000 m’makwalalamu, oyimba wankazi otchuka m’dziko muno Zani Michelle Chiumia yemwe amatchuka ndi dzina loti Zani Challe, watutumutsa abambo… ...