Bola kwa Farao: Afrobarometer yati a Malawi ochuluka atha kuvotela DPP
Ngati mu chipululu nthawi ya Mose, khamu la a Malawi likuti bola ku Aiguputo komkuja. Ulendo wa ku Kenani otsogoleledwa ndi Tonse uja ukuoneka waomba khoma. Tsogolo palibe. Utsogoleri wake ndi opatsa khambi. Kafukufuku amene… ...