Yemwe anapeka nyimbo zachikatolika Pankalasiyo Phiri wamwalira
Mkulu yemwe analembanawo nyimbo za buku lachikatolika otchedwa Pankalasiyo Pondani Phiko Phiri wamwalira m'mawa wa lero lachiwiri. A Phiri amwalira ku Nyumba kwawo ku Mua ndipo amachokera M'boma la Dedza. A Phiri ndi m'modzi mwa… ...