Mtumiki wati Jetu watenga njira yachitayiko, asiye kuyimba
“Mama Jetu siyani njira ya kuchitayiko yomwe mwayiyamba, its too late for that. Dziko la pansi limapeleka sapoti pa zinthu zoyipa zakuchionongeko.” Awa ndi mawu omwe mtumiki wina akuti watumidwa ndi Mulungu kupita kwa woyimba… ...