NRB yatsimikizira aMalawi kuti ikugwira ntchito yake mwa ukadaulo
Bungwe loyendetsa kalembera m’dziko muno la National Registration Bureau (NRB) lati ilo likupitilira kugwira ntchito yake mwaukadaulo ngakhale pali madandaulo kuchokera kwa mzika zina zokhudzidwa kuti kalemberayi sakuyenda bwino. Izi zadza pamene gulu la mzika… ...