A Phungu ena a MCP amagawa soya pieces ndi ndalama pa malo olembetsera – Mkandawire
M'modzi mwa akuluakulu a gulu la Chisankho Watch omwe amayang’anira ntchito za chisankho m'dziko muno, wauza atolankhani mu mzinda wa Lilongwe kuti kalembera wa gawo la chitatu unakumananso ndi mavuto akulu monga ziphuphu. Iwo anati… ...