
Boma lapereka chimanga ndi ndalama kwa omwe adakhudzidwa ndi Namondwe wa Freddy
Kutsatira mavuto omwe alipo kamba ka namondwe wa Freddy yemwe adaononga mbewu ndikuyika a Malawi ochuluka munjala yadzaoneni, tsopano boma layamba kugawa chimanga komanso ndalama m’madera omwe adakhudzidwa. Ntchito yopereka thandizoli yayambira mu mzinda wa… ...