Njatani onse onena kuti Chilima anaphedwa – yatelo Komishoni
Bungwe la padera lomwe linakhazikitsidwa kuti lifufuze za ngozi yomwe idapha wachiwiri wakale kwa mtsogoleri wa dziko lino yapempha apolisi kuti athane ndi onse ofalitsa nkhani zomwe ati ndi zabodza pa masamba a mchezo. Mu… ...