Anthu a mipingo ndi ena onse amene akudana ndi lamulo loti amayi aziloledwa kuchotsa pakati asayese Mafumu ali mbali yawo. Malingana ndi Mfumu Yaikulu Lukwa ya a Chewa, Mafumu akugwilizana ndi lamulo loti amayi aziloledwa… ...
Articles By Mwayi Mkandawire
The Malawi Energy Regulatory Authority (Mera) board has fired Chief Executive Officer (CEO) Ralph Kamoto and finance director Elias Hausi over allegations of corruption. The two are alleged to have diverted K2.964 billion from the… ...
Inu nonse okonda kutsuka mkamwa ndi mau aululu, samalani tsopano. Lamulo likuchitani tintini. Bambo wina wa zaka makumi atatu ndi mphambu zisanu ndi imodzi (36) wagamulidwa ndi bwalo la majisitireti mu boma la Machinga kuti… ...
Apolisi ku Mangochi agwila Bambo wina wa zaka 40 kamba kogwilila ndi kupeleka mimba kwa mwana wake. Malinga ndi onenela a Polisi mu boma la Mangochi, a Amina Daudi, Bambo amene watsekeledwayu kwawo ndi ku… ...
About 13 primary school teachers from 7 schools in Chikwawa district have been fired for absconding work. Chikwawa District Education Manager,Mrs Chrissie Chimsale,has confirmed the development when speaking with Malawi24 in an interview. According to… ...
Celebrated musician Dan Lu has been roughed up by minibus drivers in Chilobwe Township, Blantyre after a disagreement over the space he parked his car, Malawi24 has learnt. It is said that Dan Lu was… ...
Ngakhale chilango cha munthu ogwililira chili moyo onse kundende kapena kunyongedwa kumene, Bambo wina wangogamulidwa miyezi yochepa chabe ngakhale anachita chipongwe gogo. Malinga ndi ma umboni mu Khoti, Bambo Biwi Ephraim a zaka 54 anagwililira… ...