Dan Lu beaten in Chilobwe

Dan Lu
Dan Lu
Dan Lu (In black circle) shot in the course of the brawl.

Celebrated musician Dan Lu has been roughed up by minibus drivers in Chilobwe Township, Blantyre after a disagreement over the space he parked his car, Malawi24 has learnt.

It is said that Dan Lu was heading towards a hair dressing saloon owned by his wife Emmie-whose photos of pregnancy he leaked recently in Chilobwe when the incident happened.

‘’He had parked his car near the saloon but one of the minibus drivers hit the car a little bit. It was after this that they started exchanging words. The other drivers joined the row before they were seen roughing him up saying he was being rude’’ an eye witness wrote Malawi24 on Monday afternoon.

The drivers argued with him that he had parked the vehicle at a wrong space.

A circulating audio clip which was apparently recorded by one of the passengers of the minibuses reveals how the brawl might have been serious.

‘’Iyeyo amazitenga ngat ndani kodi? Ku Chilobwe kuno amazitenga ngati celeb iyeyo chifukwa chani?’’ (So he thinks he can come here in Chilobwe and boast about being a celebrity, hell no)’’ one of the drivers was recorded saying.

This comes days after he posted on Facebook a photo of him and his wife in which he lays his hands on her half-bare belly.

He was slammed on the social media but he was quoted by a local paper as having said ‘It is my business’.

Advertisement

502 Comments

 1. IF we all have jah love no ,jelousy,hateless cud exist,jah guide us long live mr dan

 2. Guys please let’s not mix stories here.. Za mimba ya nkazi wa Dan lu zikugwilizana chani ndi ngozi ya galimoto??? Anthu amene mukupanga ma comment osanveka ambilinu apa mu live galimoto or ntengo wa galimoto even insurance simukuwudziwa… Ama mini bus sayenda bwino pa nsewu.. Kungoti anthu akuda nsanje nde inakuchulukilani kwambilili ndi chifukwa chake zimavuta kulemela…. Dan nthawi yake inakwana kuti akhale ndi Ndalama, munthu wa dziko lapansi amasangala akamamuona nzake akuvutika nanuso pangani zanu ndalama mwina ife tinga dzakambeko za inu.. Munthu aka khala kuti akusakidwa China chili chonse chomwe munthu angapange zimakhala zolakwika.. A ma mini bus munali kale ndi chifukwa ndi Dan.. Ngati akazi anu simuwa nyadila zanu zimenezo nde kuti ana badwa ngati phongo… Let Dan enjoy his money mukumuzunzilanji munthu ndi thukuta lake???

 3. vuto ndiloti oyimbanu mukangotchuka mudziko mumafuna mudzilitenga dziko ngati ndilambuyanu doing whatever u want. ambuye mutengeni dan lufani yu mutibwezele evison matafale plz plz takupasani waulele uyu.

 4. Eyaa! very good minibus drivers, ndipo nonse amene mukubakila dn mbuzi. Inu zimene akuchita ameneyu simukuwona?, kapena simukumva?. as we Malawias we dont like behavier like that, ndiye poti ananenakale kuti iye siwakumalawi, komabe asayiware(chakwanu leka), akadananazo kuntheni. Amalawi chifukwa chani kuyikira kumbuyo zopusa?. Enanu mukuti tipite tikawone kunja zimene azathu akupanga, eee…!, amenewo akupanga zakwawo, sopanoifeso tisiye zathu tizipanga zawozo, nsopano zathu atipangira ndani?. Kwa ine ndikuyamikira anyamata amene amupanga zinandizina dn, pitirizani ndipo malawimuno mukanakhala anthu ochuluka oganizabwino ngati inu sibwezi tilindianthu opanda khalidwe ngati dn, very good ngakhare kumakuntha daily.

 5. a #Dan_Lu! mavuto ena ndiosavuta kupewa…. kubadwa kwa inu makolo anu amayenda mimba pa m’tunda? iyitu ndiye nkhani yeni yeni akupandilani anthuwa…. ku tchuka musamakuphatikize ndi kunyumba tayesani kukhala oimba wa chitsanzo chabwino…..

 6. Mmmmm my fellow Malawians, let’s concentrate on our problems & get solutions 2 dem oky!!! Dats y w r nt developing instead w r married to stagnation!!!!! Very sympathetic

 7. Kodi Tizingomva Mbiri Zoipa Zaiyeyu Basi?Nanunso Amalawi 24 Mumulonderanji Munthuyi.Tizi Wolakwa Ndiyekha Dzikoli?Mwatikwana Musiyeni.Kenako Tizamva Danilu Wazibibira Chifukwa Chosegula Mmimba.Musiyeni Nyamata Awonetse Nthawi Ya Chinyamata Yake Inu Mwakalamba.

 8. Wina amvekere Dan Lu ndiwamatama! Oooh! Umafuna ukhale celeb ndiwe? Nde uztipangira matama ife? Kod utakhala kut ndiwe wamenyedwa akanaziwa ndani. Mumafuna muziwoneka ngat abwino bt ur dark side is rubbish only that no one cares abt ur existence. Mnthu wozindikira wil nt care abt celeb personal life.

 9. Fight for a good fight for your own benefit, he’s progressing and have vision, talented! Discover your purpose in life! Time is money!

 10. What I know about minibus drivers,,they smoke chamba 2 much,,so the best way to avoid their donkey behaviour,z only to stay away from them!

 11. Paja amalawi, munthu asasambe, asayendetse galimoto mumampezela zifukwa, nsanje basi parking inatani? Ndikulodzani nonse mwatenga gawo pomumenya Dan Lu

 12. Malawi 24 remove the headline called…. Has bean beaten!!….. They were exchanging words ndawelenga katatu nkhaniyi koma sindikupeza pamene amamenyana mpaka wina kumenyedwa….. Dan-lu inde we are not proud of him pa zimene akuchita but! Izizi mwangomufalisira za bodza

 13. Koma a Dan lu ndiye mwatchukatu,PA nzana timava za ma picture owonesa mimba,lero akuti akumenyani ma celeb azanu a maminu bus kkkkkkkkkkk.

 14. Anthu akaza ndalama atsamangimu nyela manyi Malawi chifukwa ndi otsauka ayi ukakhala ubwanawo mudzikawa onetsa anthu aku mangochi otsati pachilibwe panoyi

 15. Mmmmmm ndukhulupilira kuti a ma minbus wo amumenyela zifukwa zina not wrong parking,taona anthu ife akupanga ma wrong parking koma osamenya.kungot ma minibus driver umbuli umakusowetsani mtendele ndichifukwanso mumayamba kugwila ntchito musanasambe uku mukungonunkha fodya ndi masachet shame on you ma min bus driver.nanunso a Dan Lu ku saloon kwa akazi anu mumakataniko ?,malo oti amadzadza ndi azimayi okha okha,nkazi kumachez naye kunyumba man.

 16. Amuchita bwino coz amayankha mwano panthawi imene amamuuza kuti asunthe galimoto yake! Kodi amene mukumuikira kumbuyo inu, tangoganizani inuyo mukukanika kudutsa coz winawake wakutchingilani ndiye mukumupempha kuti mudutse ndie akuyankhen chipongwe. Mungamve bwanji muntima?

  1. Am telling you Malawi we are full of jealous, when ur poor r talking about u, and when ur rich is satanic, i don’t understand, now they want all malawians to b celebrities which is impossible, sometimes i hate to be a malawian.

   1. Unfortunately your a Malawian and nothing will change that

 17. koma anthu alibe chisoni,kumumenya mzawo nkhani yake imeneyi…..zoti mkazi wake ali ndi mimba koma anthuwo akudziwa?KKKKKKKKKKKKK

 18. No wonder minibus drivers… Africa, jealous too much. Mix usaveji. Amnzathu amanyadira ma cerebu adziko lawo. Munakatha kumuuza iye ndikumversa koma osamumenya… No wonder Luck Dube was killed by own fellow citizens. Thus African standard kind of reasoning…. it happens.

  1. Kkkkk bro mwati kunyadira celeb??? Ma celeb ambiri amankhara ozikonda ndiye iwe nkumawanyadira like really..if they need to be respected the best way they must just keep themselves away from mini bus drivers..

 19. Hmmmmmm amalawi bodza silizakutherani ndichifukwa chake simmatukuka coz u gat na tym 4 work bt gosp ….. Car pack yake yakut imene Dan lu anapanga pack yo .? T ws a cetain accedent n a ws there thers na quarel pon de residence . A malawi amalawi nsanje basi……..

 20. The ignorant idiots. Mukulimbana ndi Dan Lu wathu bwanj. Ngat amakubowani shut up ur proboscis. After all we dont need u. Amene timamufira tinakwana kale. U are just a drop in a lake. Amalaw umbuli basi. Osamapita ku sukulu zakwacha bwanj.

 21. Heyi pangani zanu naye Dan alindiufulu opangachilichonse ngati mmalawiso asazuzike ndiinu akapolo amphawi, pangani zanu osamulonda chonchi shit za manyasa

 22. Dan lu ,pepani amalawi mpaka ambuye adzabwela umbuli thoo anu wake amati mashasha mubwele kuno Ku jonz tidzakuthyoleni mano or a police mmalo mokalima kumangomwela kachaso anthu akuti agwile bwino ntchito munamuona munthu kuti omwa kachaso amaganiza zaukape akapolo onunkha dzuwa ,Dan lu ndimufunsa bwinobwino makape nonse ndizakushutani ndinfuti or a police auzidwe ndilibe nawo ntchito akapolo onunkha dzuwa amuthalika ,uzowela namasimba futseki, Dan lu ngati ukundiva anthu amenewo undiuza kuti ndikhululuke ndi iweyo ,I don’t any one about Malawi too small imutwana auzaniphaphela

 23. Amutapa,amutsukuluza,amufafantha,amutidzimula,amukanyanga,amuchotsa chimbenene,amutsukuluza awa ndi eni town amugwilagwirawa,bt why?

 24. Maliwians what r u doing mwafasako ereeeeeti wrong parking inu mumazparker motani amaminibus nsanje mutuwa dimunati uko nkuyamba

 25. Inu nde mukulimbana nayetu osapanga zanu bwanji .kupanda nzelutu kumeneku.malo molemba za chimanga chinabedwachi muli kakaka kunyozetsa nzanu shame on you purpet reporter

 26. Mukafuna kutchuka ndikumenya simungatchuke njira ya bho ndikuyenda maliseche pachinantindi/#Pagulu la anthu mazanamazana. AMA OUT BHEKANI IZINDABA ZENU MUYENZANINA SINJALO JE KANTI INI. IWOLAMASIMBA ABANTU AMNYAMA UMUNTU UYAZIYENZELA IZINTO ZAKE. AKASAFUNE SCELA ABANGANA BENU. NOMAYENA UTHATHA I PREGINANT YA FANZI WAKE KUKHOMBA PHAMBI KWA ABANTU THAT MEAN……. BAMUTHANDA KAKHULU

 27. Angotopa nawe anthu ndinkhani ya mimba ija, ena zinawakomela ena zinawanyasa ,ndimene ukuonela pa ma commentwa sorryrio mr shupie..

 28. Mmmmmm koma ku Malawi!!!! Si njira yothetsera vuto imeneyo just imagine anthu amenye muthu is right?? Aaaasaaa Dan kip it up umakwana!!!

 29. Kumalawi omenya anathadi Et? Mungamati Dan Lu waphikidwa yet or magazi sanatuluke mkomwe? Pachikhalidwe chathu munthu akat wamenyedwa akuenera kut atuluke magazi apo ai atcholedwe khosi ena amatiso kutapidwa nkhwiko or mano anyamulidwe mu sosala. Nde ndisamveso wina akuti mfwii mfwii Eeee Dan Lu wopereka mimba uja wamenyedwa ndimuswa.Dan Lu ndakumana nae madzulo omwewa kunsika wanjala patsidyapo atagula chi Obama ndi Thobwa lache akumwa uku akufotokoza umo zinaliri

 30. no he wasn’t… fanz inangimulusira cfukwa amakana kusuntha galimoto yake bas..#Malawi24 check thoroughly b4 posting mukuonjezano pple will be doubting ur authenticity

 31. If you are saying,respect a fool to avoid noise.A fool is Dan Lu and not drivers.Look what he did.Totally contrally to our tradition.The one appreciating that simply shows he is not a Malawian.We were born to respect our culture just as our freinds are doing.Why showing this strange tradition?He has got his young brothers and sisters who maybe are just growing.What image is he planting on them.Very bad.To be beaten its food for thought to him.Dont sympathise him.

  1. #dan, u r right. dan lu ndi yemwe ali opusa apa. achita bwino amuponda. ine ndi madana ndi anthu opanga zopusa.

  2. Za mimba ya nkazi wake zikugwilizana chani ndi ku mugundila galimoto????do u even know how much a car cost??? Cars are expensive and minibuses drivers always drive recklessly… Anthu okuda tili ndi vuto nsanje kwambilili ndi chi fukwa chake zimativuta kulemela.. And munthu muka khala kuti mukumusaka mumamupezela zifukwa zambili mbili.. Thawi yake yakwana Kaya Ina afune Kaya as afune Dan lu Ali ndi dolaa… Pangani zanu ndalama nwina nafeso tingakambeko za inu…

  3. Za mimba ya nkazi wake zikugwilizana chani ndi ku mugundila galimoto????do u even know how much a car cost??? Cars are expensive and minibuses drivers always drive recklessly… Anthu okuda tili ndi vuto nsanje kwambilili ndi chi fukwa chake zimativuta kulemela.. And munthu muka khala kuti mukumusaka mumamupezela zifukwa zambili mbili.. Thawi yake yakwana Kaya Ina afune Kaya as afune Dan lu Ali ndi dolaa… Pangani zanu ndalama nwina nafeso tingakambeko za inu…

  4. Za mimba ya nkazi wake zikugwilizana chani ndi ku mugundila galimoto????do u even know how much a car cost??? Cars are expensive and minibuses drivers always drive recklessly… Anthu okuda tili ndi vuto nsanje kwambilili ndi chi fukwa chake zimativuta kulemela.. And munthu muka khala kuti mukumusaka mumamupezela zifukwa zambili mbili.. Thawi yake yakwana Kaya Ina afune Kaya as afune Dan lu Ali ndi dolaa… Pangani zanu ndalama nwina nafeso tingakambeko za inu…

 32. kodi bac amalawi tilindi chi mzimu chomamenya ma cerebrity bac? ayi koma nkhani yake? chifukwa choti anayimba ndi kcee????

   1. Mini bus drivers a pa malawi ndi ma savage. sanakamfunsa kuti asunthe. Iwo aja amayima bwanji

  1. nde zonyadila zimenezozo? Ndani samawadziwa ma mini bus drivers a pa malawi kuti ndi ma savage. Sakanadutsayi? Iwo aja amayima mkati mwa msewu nkumapakila ma passengers ife titangoyima.

 33. #1;nsanje yakula apa nanga olo nkumamumuti amazitenga ngati celeb?moti simunaziwebe kuti Dan Lu ndi celeb?malawi sazathekadi kkk

 34. Fana Dan lufani ikakuona lisiro sikata ndipo ukumana ndizambiri malingana ndi chibwana unapanga pakati paja poonesa mimba ya mkazi wako ku mtundu wa malawi ndipo zambiri zikubwera kwa iwe uziwa minyama fana

 35. Kkkkkkk anthu ena ndinu odabwisa.mukuchita kufunsa chifukwa chomenyedwera?????? Kkkkkkk chifukwa ndi choonesa chi mimba#musova;!

 36. There is a say, which says respect a fool to avoid noise, Sorry Dan Lu ngakhale akutero ine ndimakufilabe. Indeed malawi nsanje 3 much.

  1. #max, Ukupepesa munthu opusa. iye amapanga zonse (kuyanika mimba + wrong parking ) just for fame. achita bwino amukwapula, ifenso timatha kupeleka mimba nde iyeyo ndindani ? ma rubbish basi ndipo ndkadakhala kut nddalikomweko ndkanamusinja nawo. chithokozo kwa onse omwe apangisa kut munthu opanda umunthuyu amenyewe.

 37. Stop this nonsense you so called adim, who is dan lufani by the way? If you don’t have anything to say then shut your mouth, don’t you have anything Godly?

 38. GyZ amene akudziwa kuti ine ndamumenya dan lu chisilu cha muthu ndipo saganiza galu wachabe wamuthu ndife gulu la anyamata omwe timamufunila zabwino mr dan lu kuti mulungu azipitilila kufunila zabwino pa luso lake alinalo lomwe likufikisa pomwe sakayembekezela angafikepo pa chiyambi chake nde monga boma lakumalawi ngati ife mtundu wanu wakumalawi omwe timakusakhani kuti mutisongolele dziko lathu lamalawi athu ameneo mwafufuze kwagwila alandileso chilango mr dan lu siolakwa koma phanvu ya satana yakwela kwambili athu majelasi ndine mwana omwe ndili mu south afrieca koma ndi zika za dziko lamalawi zisilu zawathu zomwe zamenya oyimba wa dziko lakwathu munga malawi makape athy akumudzi

 39. Honestly its better to stay away from such type people…anthu a ma minibus sayaluka .koma iweyo ngati celeb umayaluka and you cant beat them since they are in numbers…ma celeb akwathu try some kind of private life zomazionesazi ndiye aiiii ..malawi ali ndi nsanje kwambiri..

 40. The tax driver is wrong as I read through the news ,he just bump his car and the car was parked in front of his saloon.it just show that their just taking advantage of his fame .Dan Hire bodyguard and kick their ass their should learn a lesson a tax driver or sue them so that their should pay the damage

 41. Cereb waine nd sir Patrick’s,mwanache komanso slyce plus Lucius banda osat mphale yamatama yamenyedwayi.sindngampangire nsanje chifukwa sindmadya pakhomo pake Dan lu wanuyo

 42. ndinali popo..magalimoto anagundana n amadikila police kuti izalembe lipoti..ndy ma minbus drivers amaona kuchedwa..then there was disagrmnt #inu malawi 24 kumafufuza kaye kuti mupeleke khan yonveka bwino..sizaumbuli mumapangazi

  1. amadikila police..ndy ma driver amamuza kuti asuthe galimoto yake coz inaseka nsewu..mpaka ine ndnangosika kuyenda wapasi panali pa malingamoyo..anthu amangomutukwana

 43. laughing mood activate…simesa ati anapack pakati pa mnseu..ma celeb opanda zochta..monday ngati lero mesa ndi active business day??mh..kaya koma nde zosabwino…

 44. MALAWI. Uthengau ukupita kwa Mtsogoleri wa dziko la Malawi. Olemekezeka Bwana Prasident komwe muliko. Imvani mtundu wa malawi kulira. Bwana ife ndi anthu omweaja tinakuvotelani tilibe nanu mangawa koma lathu ndi pempho chabe. Malonjezo anu sitinaiwale maka munati muzapitiliza bwino pomwe akulu anu anasiyira. Ife amalawi sitifuna zambiri bwana monga mukudziwa ife ndi anthu olimbikira muzintchito ndipo sitidalira kuti muzitipatsa ndalama pa mwedzi kapena mudzitimangila manyumba ayi. Koma nkhani ndadza nayo pano ndiyoti Ife amalawi tili ndi umphawi wadzaoneni pamene ndi anthu omwe anakuvotelani. Mwina mungathe kufunsa kuti simukufuna ndalama ndi manyumba awulere ndiye ndikuchitileni chanu? Bwana ife tili pano tikufuna mutichepetsele njala momwe akulu anu anachitila koma zimafunika inu mupitilire pamenepaja, mfundo zathu ndizotere pa nkhaniyi: Ndalama zomwe mukanatengera anduna anu kupita ku America kukanjoya. Mukagule Feteleza m’maiko ena ndikuika m’ma admac ndi m’ma dillers onse m’malawi ndikuika mtengo otchipa monga K5 000 thumba limodzi kuti amphawi ndi onse ochita bwino adzigula mofanana. Feteleza asamasowe m’malo tawatchulawa ndipo pasapezeke munthu akugulitsa feteleza mopitirila mtengo wa boma akapezeka oteroyo adzimangidwa komanso kutseka business yakeyo. Chimanga chikakololedwa chidzigulidwa ndi aboma pa mtengo umodzi ndipo anthu onse amalonda ya chimanga asagule chimanga pa mtengo opitilila wa boma oteroyo amangidwe ndipo business yake itsekedwe. Anthu adzikhala ndi ufulu okagulitsa mbeu zina kupatula chimanga’ mwachisanzo Fodya, thonje, ndizina zambiri kungopatula chimanga. Kupanga zimenezi kwa zaka 3-5 muzapeza kuti Malawi tidzasala ndi umphawi koma njala idzatha kotero anthu akadzakahala ndi chokudya chokwana adzagwira ntchito zachitukuko cha dziko molimbika. Or mutamanena kuti munthu afuna kupita maiko akunja ayenera kumapezeka ndi account bank ndipo mudzikhala ndalama zokwana K500 000 amalawi adzakhala omvetsetsa or mudzidzati passport ndi K100 000 anthu adzalipila chifukwa opita kujon or ku UK adzadziwa kuti pakhomo akusiya pali chakudya. Pomaliza muzaganizile nkhalamba, ana amasiye, olumala ndi odwalika nthenda zikuluzikulu onse adzilandila K12 000 pamwezi ndiye kuti ndalama imeneija anthu aja azidzigwilitsila ntchito kukagula zosowa zao kuti misonkho mumatidula ija idzithandizanso anthu osati boma lokha. Guys kwinako pitilizani. Zikomooo!

  1. 2019 if u wil vote again,Peter to cotinue leading Malawi,,;,U Malawians ur Idiot,,ndipovuta kut Munthu obwera aziwe Mavuto athu,,pamene ife Malawi step food is Maize kwa America amadya Bread,,,kkkkkkkk,, koma 2019 tizasankhe zika ya Malawi yoti iziziwa Mavuto,,,,My Prayer is God help us to open our eyes as you did to Hagah,,in the wildness,Amen.

 45. I think ya parking yo yangogweramo,nkhani nkuyanika mimba ya mkazake poyera kuti world yonse iwone zimene sizinachitikepo m’mbiri ya fuko la Malawi,uko nkukwiya naye Kkkkkkkk

  1. M’malawi ndimadziwa ine ndi ameneyo,amangokuyang’ana koma ukati upange zofoila zonse zimadza pakamodzi,Galimoto yo mwina nkutheka anapanga park pafupi chabe ndi ma mini bus wo koma chongomva zoti ndi ameneyo ,onse ndi ma sisitansi omwe osalephera kuponya kamwendo Kkkkkkkk

 46. Malawi malawi malawi iwe ndiwed mbuli ya mu africa ulibe chilichonse kulimbana nd mzungu udzadya doth day one

 47. We all knw hw rude n reckless tax drivers r… We owez find t hard to pass thru wenever they r to pck or drop,.. Hw many times has Dan park in this way? Thoz who doesnt knw the rules on the road r the one applaudng these road savages,,,

 48. Mmmmm nkhani yomenyela munthu ndiiti pamenepa za nsanje basi,wat kind of a wrong parking r u talkin about yet mukuti he parked his car in front of da wife saroon,basi kungomva kuti munthuyu ngotchuka mwati nanunso mutchuke chonsecho ndinu mwagunda galimoto yake, zofoila basi umbuli thoo minibus zaweni

  1. munthu ukamalimbana nchitsiru nawe imakhala chitsilu. pali zina munthu umangofunika kuzipanga avoid ngakhale ukudziwa kuti sunalakwitse. paliponseno ungapapite ma minibus drivers ndi a mwano and amakhala ngati anagula dziko lonse. iye Dan yo akanawapewa zonsezi sizikanachitika.

  2. Kkkkk iyetu walandira chilango. Even umuteteze m’mayankhulidwe, masaya ake alandira mapama kalekale ku BT

  3. Dan lu apepese kwa mtundu wa a malawi ndizomwe amawonesa mimba ya nkazi wake zija…kupanda apo aziwona even ana kumulavula…ma celeb anthu ndiye aiiii.

 49. Munthu ukakhala dolo sumalimbana ndi anthu ena like ma minibus drivers. Avoid those niggaz bro. Keep them good space away bro!!! Am serious.

  1. Only cowards r afraid of them….every place has the rules n regul…to b followed so who r they to intimidate other citizens?

  2. Honestly its better to stay away from such type people…anthu a ma minibus sayaluka .koma iweyo ngati celeb umayaluka and you cant beat them since they are in numbers…ma celeb akwathu try some kind of private life zomazionesazi ndiye aiiii ..malawi ali ndi nsanje kwambiri..

  3. Uthadi kutenga ulemu wakwanu and spit shit words on them and u expect that they wl bow down 4u, heee, at the end u get devalued urself, coz amakupanga zimene sumayembekezela, the best medicine is to just avoid them, u loose nothing, look now anthu apeza zokambilana tsopano

  4. Patrick Kamanga if you was driving, and someone crash into you, you are waiting for Police to show up, where do u live your cars? So Dan Lu did not get into a fight with minibus drivers!! Facts

  5. I get your point,that is why am saying these taxi drivers even though you are on the right side of the law just ignore them..dont rise a fight with them..they are already weired. Besides that our celeb lost value on that thing of showing his wife pregnancy now anything he can do people wil never value it..let us just be serious with our life all the time and wherever we are !! ..Spiwe Zulu

  6. Pregnancy is not something to be embarrassed about, it is something to celebrate for!!
   I honestly do not believe that in 2017 Malawians are are ashamed or embarrassed to see a Mrs pregnant women! And they have kids abwana, sichoncho ?? Patrick Kamanga ☺
   I think it just goes to show how big a celebrity Dan Lu is in Malawi, that’s great publicity for him.
   Zachisoni kuti in Malawi we still think like that!!

 50. Ndidolo-be basi,anthu olimbana ndi munthu otchuka ngati Dan-lu cholinga chawo ndikufuna kutchukila paiye.#dan_lu_ndi_dilu

 51. Mpuntheni nyani ameneyu,apart froma zapa msewuzo watichitisiranso manyazi azimayi athu achimalawi powonesa phuli ku gulu…wayika chipinda panja….

 52. Nde paja alipo anthu ena akungomuyamikira zilizonse zomwe akupanga mkuluyi..ati poti ndi Celebo nde alin ndi ufulu opanga zomwe akufuna..Tayamikiraniso pakhalidwe waonetsali apanga bwanji park galimoto panseu anzake akufunapo kudutsa…amene akufuna ka audio kake fazi ikulalata afta kumuponda drop ur # muzinvere nokha makamaka kwanonse omuchemelera Celebo wanuyi….

  1. We all knw tax drivers are reckless and selfish on the road,,, bt if someone does the same…then he z more than wrong,,, # fuck them wth their supporter’s,,,!

  2. Yah gyz mkazi ameneyu chisilu bwanji matama achiyani ndi big mn wathu ameneyo oyimba wakumalawi moti muzinyadila kuti uyimba wakwathu akutchuka mayiko akunja muli busy kuyakhula zopusa mkazi iwe sika kukamwa pako povundapo

  3. Mmmmmmmmmmmm Inu zisilu majelasi ndi luso lazanu ndimayesa athu akumalawinu muli zelu koma zisilu za wathu omwe akuti wachita bho kumenyako ndipo nosenu mulibe manyazi chomwe chikuyakhulisani zimenezo phanvu yobadwila kumweko kukulilaso kumalawiko osayende mayiko akunja ano kuti muphuzeleko chikhalidwe cholongosoka mbuzi zawathu ndipo siwachita bho kumenyeko dan lu nde ife kuno tiyamba kumenya athu ambali yakumweko wa menya dan lu kupha komwe muzinva kuti amalawi amenyedwa ku NRCS ndi amalawi azao zatikwana zomwe muyakhula zisilu zakumalawinu zatikwana kumenyaso big mn dan lu ifeso takwiya kuno ku cap town kuno tiyambaso kupanda athu amene anachokela kumeneko wachita chipogwe dan luyo

Comments are closed.