facebook
Saliokha a Peter. Patangidutsa tsiku mtsogoleri wa dziko lino ataopseza kuti boma lake linjata anthu onse osamalika pa Facebook, naye sipikala wa nyumba ya malamulo walangiza a Malawi kuti pa Facebook sipotukwanila. Malingana ndi a… ...
Admarc Malawi
Nkhani ya kuba kwa chimanga idakalibe m’bwalo ngakhale mkulu amene anali induna yoona za malimidwe a George Chaponda adachotsedwa. Mkulu wina ogwila ntchito ku ADMARC mu boma la Nsanje, watsekeledwa ataponda matumba a chimanga okwana… ...