...Bullets sinangopeza K75,000 yokha Malawi24 yapeza kuti ndi bodza la nkhunkhuniza limene a Malawi ena akulengeza lonena kuti zitagawidwa ndalama za chikho cha Airtel Top 8, timu ya Wanderers yatolera ndalama zokwana K24 miliyoni. Malinga… ...
Articles By Mwayi Mkandawire
Zina ukamva, kuchititsa nthumanzi ndi zina kuchititsa thupi kuuma kumene. Pamene a boma ndi mabungwe akuyesetsa kufuna kuteteza amayi ndi ana, Bambo wina wa zaka 21 wapha ka mwana ka zaka 4 atakagwililila. Izi zachitika… ...
Illovo Sugar Malawi Limited has raised by 9% sugar prices, it has been confirmed. This is due to national equalisations scheme, according to the company. This comes weeks after the commodity had became scarce on… ...
The Malawi Electoral Commission (MEC) has now moved to axe suspended chief elections officer Willie Kalonga and Director of Administration and Human Resources George Khaki in the wake of reports of financial mismanagement at the… ...
Phungu wa nyumba ya malamulo wa dera la pakati mu boma la Mwanza, a Davis Katsonga, aletsedwa kupita ku nyumba ya malamulo kamba kovala ka chisoti ka chikhalidwe chawo. A Katsonga amene ndi Phungu wa… ...
Ngati muli a chigawo cha kumpoto ndiye mumakhumba kukhala President ndiye kuti ndinu munthu wa chibwana kwambiri. Malinga ndi mlembi wamkulu wa chipani cha DPP Mayi Grezzeder Jeffrey wa Jeffrey, palibe munthu wa kumpoto angakwanitse… ...
Opposition United Democratic Front (UDF) President Atupele Muluzi is being warned against letting the party to be ‘swallowed’ by the ruling Democratic Progressive Party (DPP) ahead of the 2019 elections. This comes hot in the… ...