Aphungu onse amene anatalikitsila manja awo okonda kusololasolola mu ndalama za boma akuyenela kupeza mavuto. Malinga ndi katswiri pa nkhani za ndale ndi kayendetsedwe ka boma, a Wonderful Mkhutche, Boma lisanyengelele mbava zonse za aphungu.… ...
Articles By Mwayi Mkandawire
Chaka chino ndiye zonyengelera kulibe. Apolisi a pamseu akwiya ndipo nonse opitiliza chibwana samalani chifukwa mutha kupeza mavuto. Mkulu wina oyendetsa minibus wayetsa malodza atagamulidwa kuti alipile ndalama zokwana K480,000 atapezeka kuti amayenda opanda license… ...
Bambo wina wa zaka makumi atatu kudza mphambu zisanu ndi imodzi (36) ali m'manja mwa Apolisi a mu boma la Lilongwe atapha mkazi wake. Malinga ndi Apolisi, bamboyu ndi a Major Wilson ochokera mu boma… ...
Controversial legislator for Mzimba Hora Christopher Mzomera Ngwira has returned to the ruling Democratic Progressive Party (DPP) and has claimed that the party is the only hope for Malawi. Ngwira announced his decision to rejoin… ...
Mkangano mu chipani cha Kongelesi wafika pamponda chimera. Mtsogoleri wa chipani chotsutsa cha Kongelesi, a Lazarus Chakwera atenga chiletso chokaniza kuti kusakhale msonkhano waukulu wa chipanichi umene ayitanitsa a Gustave Kaliwo. A Kaliwo ndi mlembi… ...
Zoopsa kwambiri. Kaya atsale ndi ndani pa dziko pano? Kutavuta nkhani yonyansa yopha anthu a chi alubino, zamveka kuti ku Mazambiki zigawenga tsopano zayamba kuchita chiwembu anthu okhala ndi danzi. Malinga ndi malipoti a atolankhani,… ...
As Chancellor College remains closed due to a lecturers’ strike, President Peter Mutharika will this Friday address students at Oxford University in the United Kingdom. According to a statement from government, Mutharika has been invited… ...