
Zatsogolo lotuluka pa belo kwa Tumpe Mtaya 'Phwedo' zidziwika mawa Lachisanu pomwe Chief Resident Magistrate Benjamin Chulu wati adzaweluza pa pempho la belo 2 koloko masana. Oyimila mbali ya boma pa mlanduwu anapempha oweluza mlandu… ...