CUFF
Tsopano mukakhala mmaluzi ndi kuganiza zoyamba bizimisi ya Tchalitchi muli muzichita uneneri, musamale. Azikumangani. A Polisi ku Thyolo anjata ndi kutengela ku Khoti Bambo Sampulo Newiri a utumiki otchedwa Thamanda ati kamba kofalitsa uthenga wa… ...
CUFF
Patsepatse nkulanda. Kupalamula ndi konse ndithu koma milandu inayi ndendende kugenda ku Polisi wamkulu fodya ali mthumba. Bambo wina wa zaka makumi awiri ndi mphambu zisanu kudza imodzi (26) ali m'manja mwa a Polisi atagwidwa… ...