NDIZAKUGWILIRA! A Malawi anyangala ndi nyimbo yopepela, a bungwe akufuna oyimba amangidwe

Mwiza Chavura

Ndi dzana lija nyimbo zinali zotamandila ndi zonyadilila akazi. Pano anthu ayamba kuimba za upandu ndi kuzitamandila pa uchigawenga.

Nyimbo ina yopepela yautsa mapiri pa chigwa. Nyimboyi imene wayimba ndi mnyamata wina osadziwika kwenikweni otchedwa Mwiza Chavura anthu aidzudzula kuti ikukolezela mkhalidwe ogwilila amayi.

Mwiza Chavura
a Malawi akwiya ndi nyimbo ya Mwiza Chavura.

Nyimboyi yomwe mutu wake ndi ‘ndizakugwilila’ ili ndi uthenga ochokela kwa oyimbayu kumuuza mtsikana upandu omwe azauchite.

Pofotokoza maganizo ake oipawo, pansi pansi aikapo mawu a munthu wamayi akulila kufuna chithandizo mwina pokhala kuti akugwililidwa.

Nyimboyi yadzetsa mkwiyo pakati pa a Malawi ambiri pomwe ochepa okha ndiwo sakuona cholakwika ndi iyo.

Pokambilana anthu pa Facebook zikuoneka kuti unyinji wa a Malawi wakhumudwa ndi zoyimba za upandu chonchi.

Masamba amene anagawa nyimboyi ayichotsa ndipo mabungwe osiyanasiyana aluso komanso anthu ena aluso aidzudzula.

Bungwe lina loona za ufulu wa ana limene wamkulu wake ndi majisitireti opuma Esmie Tembenu lanena kuti oyimba nyimbo ya upandu chonchi amangidwe.

Malinga ndi chikalata chimene a bungwe ili atulutsa ‘nyimboyi ndi ya chipongwe kwa anthu onse amene anagwililidwa ndipo ikutamandila khalidwe lonunkha’.

Bungweli lanenanso kuti ndi lokhumudwa kuti pali anthu ena amene akukonda nyimboyi.

 

Advertisement

292 Comments

 1. Pliz guyz this song lz no problem coz ena amaimba nyimbo zolaula like Gwaladi or Giboo so amalawi sanje basi kodi mukamange oimba y osamanga a cash gate or chaponda y ? za chamba.

 2. Maluz ndamene avuta pa Malawi pano akanakhala ndizochita sakanamakhala busy kupeka nyimboyi. panop
  o half yachinyamata mmalawi muno ndioyimba ndye asiyeni aziswa sound

 3. KKKKKKKKK KOMa yaaa amumange chifukwa chan pali amene asakuziwa kuti amuamagwilila mwasowa zopanga et ngati masowa chopanga bwanji osamakha mumanyumba mwanumo

 4. A #Malawi ake ati #opusawo omwe #anyangala ndi nyimbo ya hiphop artsist #Chavula ??? anali kuti m’mene Chapo… Anaba ndalama za chimanga???

  Zausilu et kumanyangala za nzeru

  osanyangala ndi nkhani ya #blackout bwanji kapena cashgate…

  #Chavula kamangidwa #chapon….. Amangidweso

 5. If you will have time n chance take a look at any HIP HOP CD cover you will see the log with words written “WARNING EXPLICIT CONTENT” so try to define n anylize/explore these words then deal with him

 6. Nyimbo zina ndi nthano zongopeka monga muja ankachitira makolo athu make dzana .. ndiye kuti amabungwenso mitu yawo siigwira oyimba amatha kungopeka bas zaziii:

 7. Chavura will exactly get what he said in his song , m’kati m’kati mwa nyimboyi wanena kuti… Sindikhala oyamba kulowa mu system ya police …………. Criminal, Nde olo atati ndikalowe prison ine bola ndikuziwa kuti ndadya Lib noooooo

 8. Naye Gibolantosi anayimba nyimbo ya duntuntu waphwisa, kodi inu anthu onenepa siidakunyaseni? Musiyeni munthu, amangofuna kuonetsa luso lake… Mmmmmh.

 9. AAAA sometimes l blame my self why i was born in MALAWI. is like malawi ndi dziko lomwe linapamgigwa kuti ndi dziko la mbuli zokhazokha aaaa GOD forgive us plzz nyimbo yeniyeni i mpaka kukwiya nayo aaaaa mamwazi bwaaaaaaaaa

 10. Kodi nkhani ya Magetsi idzalongosoka liti? Tatopatu ife ndi uchifwenthe umene ukuchitika ku Malawi wu mwanva? 2018 still nothing to be changed concerning Electricity what is this now? Mxiiiiii!!!!!

 11. Gwaladi aliyimba nyimbo DPP pala yaluza ine nijichekenge,uko nkhujikoma mulitondeka uli kumumanga imwe wakuona za wanangwa wa wanthu ndimwe vindele and mungayezgenga cha kumumanga chavula,muone masoka.walinangachi chavula is that a crime wachule imwe.

 12. Amalawi bwanji kodi mumadana ndi luso.Mwana akumenya art uyu,kusewera ndi mawu kuti mwina nyimbo zakwathuko nkuonako passport.Nkumanveledwako across the boulders.Fulseck,amene sakuikonda asaimvesele sizokakamiza.Ngati uli mbola izima yokha.Bwanji kodi,mwasowa ntchito eti

 13. amabungwe pls mwalephera ngati mukuona kuti ndiyolaula nyimboyi koma busy kukamiza anthu muno kuti azitaya mimba komanso kukwatirana akazi/amuna okhaokha? stupid

 14. It sound stupid zili too much kufoira zachamba zenizeni aaaa tembenu too much brabra why not kukamanga anthu aja ama actor ma porn ku18 Ku b city ndi ena tiziti Ku actor porn ndi kanyimbo ka chavuraka which is a big a challenge..

 15. Masikuano ana akukula opanda mwambo. I dont know ndipo sikuti ndi nyimbo yokhayi yomwe ili yolaula ndi zambiri nanga kale lonseli munali kuti kodi ndi mayesa inu ndi mabungwe a za ufulu. Aaaaa nthawi ya Kamuzu zopusa ngati izi kunalibe. Tiyeni nazo kulemekeza ma ufulu omwe tili nawowa freedom of speech now freedom of singing kkkkkkk koma kumeneko

 16. Ma vote ochuluka ndioti munthuyi asiyidwe BA’s ineso ndili mbali yomweyo ndi uthenga chabe tsiku munthuyu wagwirila iai ndipo nyimboyi mukavesera bwino lomwe ikukamba Zoti azimai akunyanya kumvala zovala Zazifupi kwambili omwe Ali malangizoso apadera

  Ikani WhatsApp number yanu kuti mwina nanu muveleko

 17. ambiri mbiri apanga nyimbo zolaula, muonerere nyimbo za Gwaladi monga Chikondi ndi magazi. Tumbocid. Ndi video yolawula imene ija bwanji osamumanga. Ngati mukuona kt pali vuto just enlight Him rather than giving Him a penalty of imprisonment.

 18. Olo atakuluma ndikudula chokodzeracho mtsikanayo palibe mulandu chifukwa ndiwe opusa naye alindiufulu okupanga chirichonse pa thupi lako dzukani atsikana!!

 19. ambiri mbiri apanga nyimbo zolaula, muonerere nyimbo za Gwaladi monga Chikondi ndi magazi. Tumbocid. Ndi video yolawula imene ija bwanji osamumanga. Ngati mukuona kt pali vuto just enlight Him rather than giving Him a penalty of imprisonment.

 20. Dziko kukondera local musician wina konkuno kumalawi amamuti George kafodya yiti andi mange andimange olo ndikafele ku ndende bola mwana ndamuthyolera kma osamumanga Kma Chavura kungotulutsa yake yomwe ndi hit song akuti amagidwe malawi watanikodi iwe big up chavura ngat akumange angopita nawe ku hospa ya anthu amisara paja ndiwe openga.

 21. Paja Fisi Ali Ndi Bwenzi Ndipo Bwenzi Lake Ndi M’dima.Zosadabwitsa Kuti Ena Akumusapota Munthu Wamaganizo Oipayu.Paja Ngakhale Munthu Adziipitsire Ntchentche Mkumamutsatira Amapezekabe Ena Omuimbira Nthungululu.Nyimbo Zinali Kale.

 22. Amangidwe ndipo akafere konko ku ndende sindngamuikir kumbuyo ndnyimbo yake yaucitsiluy amene mukumu sapporter ndnyimbo ya ucitsiluy nanuso ndnu ogwililira ndye ufulu wakew mukufun osokonez ufulu wadzake fu****k u

 23. Ati akwawo alengeza kt mwana wawo wasowa 2 days now sakuoneka ndipo mutamupeza muvaye naye pa Police yomwe muli nayo pafupi muzalandila chiongola dzanja cha 1 million… Kungomuona osaphwekesa ndi ndalama zimenezo.

 24. nkhani yomanga oimba yayamba liti? anthu amaimba nyimbo zotukwana pulezidenti koma samangidwa.So izizi zabweraso when? mmalo moti inu amabungwe muzipanga zot muzithandiza boma pankhani zachuma muli busy kunena zopanda nchele.Kod mthilauza mwanumo simungakuleseni? machende ambuzi ndithu.

 25. Apa zomangana ayi ngati kungatheke kulangizana basi three quarters ya nyimbo zikuyimbidwa masiku ano ndizotukwana nanga bwanji simukambakapo kanthu ma example ndiambirimbiri

 26. Ndani akuteroyo? Iyeyo olo atagwilira ndie vuto lako lidzakhala chani? Dziwani zoti pali nkhani yoti munthu amatha kulakwa pongoyankhula pokha ndie pali zina olo atayankhula ndipo ngati sanadzichite pamenepo ndie kuti kulakwa palibe.Nanga bwanji mudaleka kum’manga nzimayi uja kuti”Ndidzazimangilira likadzatha”. Iyeyo olo akufuna kutero ndie angapite pawailesi ndikukalengezetsa? Tamaganizani ngati munthu penapake,mukuwona ngati kundendeko ndikutheba? Uku kunali kuyimba basi m’mene timapangira masewero ogwilira ana kumudzi ndinso m’matauni.

 27. Mayazi axaphwekexe dhilu ya ma dada ngat zikukubowani mungovia mukayanike ufa pacingwe nkhalamb za m’mboma inu, imeneo nd nkhan yot izikutuluxan thukuta m’thalauza?, pangan zot muthane nd mabvut omwe akukuman nao a malaw oxat kumazemb nd zin2 zot ximbali yanu, ngat mwatop nalo dzko kuliyendexa acinyamat tlipo ambri anzeru ot tingaendexe, mfanau mukangom’mang zionexera2 kut muli mkat molimban nd mzika zomw zikuona ndkudzwa cilungam ceniceni.

  1. Simunammange Chadiriza Chimanga ku Zambia Chaponda ndiye mukammange oyimba nyimbo chabe? Kodi zitsilu inu mwasowa chochita mma office mwanumu eti? Mitu ngati zikho za Midoli, Mxiiii!!!!!

  2. Mbaleme za anthu izi inu dzinangokula mituyo koma sidziganiza…akuona ngati tidakali nthawi ya Kamuzu anyani amenewa eti….moti mukoze mavuto adziko mukulimbana ndi zithu za ziiih…!

  3. Iwe Waonesa Kuti Ndiwe Mwana Weniweni Wasatana I Think His First Born Son, Amene Akukuvomeleza Ndiaphwako. Zipaseni Ulemu, Azimai Ndi Asikana Nawo Alindiufulu, Vuto Ndiloti Achinyamata Ambili Masiku Ano Chamba Chimakuonongani Mitu,

 28. Yopepela ndi post yakoyi komanso Rtd Judge E. Tembenu ndi timabungwe tolimbana ndi za zii ngati zimenezo. Ayambe amanga Ras Dema ndi Maize gate Chaponda

  1. Dema mfumu saphwala mamawa wandipwala masana wandipwalanso lero supwala uzipwala wekha amachita kudyela nganja. Bwanji ameneyi sanamangidwe fotsek

 29. Nyimbo imakoma ngati uthenga uli mmenemo omvera akuulandira bwino.nyimbo imeneyi zasonyenyeza kuti olembayu satha kupeka,komanso alibe lunso.pamene anthu ali pakalikiliki kumenyera ufulu atsikana kapena amayi pankhani yogwirirdwa ndiye wina mkumati ndidzakugwirira.mchitidwe onukha komanso wonyasau usapitilire ngati mukuti ndi ufulu kugwirira ndi ufulu? Mukatengera za ku America mmalawi muno simukhalamo,ameneyu mpofunika ayimbenso nyimbo yoti pepani sindidzakugwirilirani,azimai your so special mundikhululukire ndinasuta chamba ndiye kuganiza kunandivuta.

 30. Nyimbo imakoma ngati uthenga uli mmenemo omvera akuulandira bwino.nyimbo imeneyi zasonyenyeza kuti olembayu satha kupeka,komanso alibe lunso.pamene anthu ali pakalikiliki kumenyera ufulu atsikana kapena amayi pankhani yogwirirdwa ndiye wina mkumati ndidzakugwirira.mchitidwe onukha komanso wonyasau usapitilire ngati mukuti ndi ufulu kugwirira ndi ufulu? Mukatengera za ku America mmalawi muno simukhalamo,ameneyu mpofunika ayimbenso nyimbo yoti pepani sindidzakugwirilirani,azimai your so special mundikhululukire ndinasuta chamba ndiye kuganiza kunandivuta.

  1. Mwina ulibe azilongo ako koma utakhala pansi ndikuimvetsera nyimbo muli khani yomvetsa chisoni.kwamunthu amene anagwirililidwapo ndizopweteka ngati anthu adziyimba nyimbo zot

  2. Palibe chommangila apa,anthu akuimba nyimbo zotukwana dairy samamangidwa bwanji,inu muyamba kugwililila kapena chifukwa iyeyu waimba nyimboyi?

 31. Kunotu oyimba ambiri ndi mbuli abulutu enieni amangofuna eti achuke on notorious things kungozuka eti kupita Ku studio kujambula nyimbo yopanda phindu ngati iyo

 32. Mukhaula Agalu Inu Muli Ndi Azibale Anu Aimba Nyimbo Zolaula Kwambiri Ndie Muzit Amagidwe??Musiyen Ndiufulu Wake Ngat Mufuna Musamavereso Koma Ife Tikadavera Pot Nyimboz Akadaimba Sanati Agalu Mbuzi Zawathu

 33. So stupid ena akuba ndalama za boma osamangidwa wina kuyimba nyimbo mwati mumumange mbuzi za anthu inu eti…..yambani kumanga mbava zoba ndalama za boma then muzimanga bwino enawo……Fotsek

  1. so much as we have freedom of xpression as per chapter 4 of the cinstitution of mw …this does not xplain why we shld be subjected to talk immoral ethics likely to bring threat to somebody …i heard the sonh and the message just potrays a very biggest threat ….

  2. I think music watching body is the one to blame coz it s not crious with its clients. Coz evn nyimbo ya atot manje diss to mafo n timaya I have not seen people talk abt it.

 34. Aliyese amaimba zomwe zabwela mmutu mwake, its his choice. Fuseki osamanga akuba kapena osakaza chuma boma. Fuseki 4 the second time

 35. aaaaa sinkhani yomangira munthu iyi… jus ban de song basi… anthu ayimbapo zotukwana koma sindinamveko kt munthu wamangidwa. Mwina mudikire remix ikubwelayi

 36. hahahahaha nde mpaka amangidwe osango ban nyimboyo bwanji, Kapena wagwilira iyeyo mu nyimboyo kkkkkkkk

Comments are closed.