Malingana ndi kukwera kwa misonkho ya galimoto m'dziko lino, bungwe lomwe limayang'anira zokhudza galimoto zowilitsidwapo kale ntchito la Used Car Dealers Association of Malawi, lati nkofunika kuti boma liunikenso misonkho yomwe bungwe la MRA likumalipiritsa… ...
Articles By Ben Bongololo
Mnyamata wa zaka 18 zakubadwa yemwe anali mu fomu 1 wafa atadzinjatilira pa mtengo ku Mponela m'boma la Dowa kamba kakuti amadzudzulidwa pakhalidwe lake lochita maubwezi ndi atsikana osiyanasiyana. Nkhani yonse ikuti mnyamatayu yemwe dzina… ...
A Malawi konzekani. Tsopano kukhala kupha makwacha kudzera pa tsamba la mchezo la Fesibuku komanso pa YouTube kuyambira chaka chomwe tichiyambe mawali cha 2024. Izi zili chomwechi malingana ndi zomwe wanena mkulu wa bungwe la… ...
Mtsogoleri wadziko la Burundi Evariste Ndayishimiye yemwenso ndi mkatolika, wadzudzula mayiko a azungu kamba kolimbikitsa ma ufulu oti amuna kapena akazi azikwatirana okhaokha. Mkunena kwake wati izi ndizonyasa komanso zamalawulo kotero oterewa akapezeka aziyikidwa mbwalo… ...
Akayidi okwana 48 tsopano akhala akusimba lokoma kutsatira mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera wakhululukira ndikumasula akayidiwa mnyengo ino yachikondwerero cha khilisimasi komanso chaka chatsopano. Malingana ndi chikalata chomwe atulutsa a Oliver Kumbambe yemwe ndi… ...
Sukulu ya ukachenjede ya University of Livingstonia (Ekwenden Campus) yalengeza kuti yakweza sukulu fizi ndipo izi zikhudza ophunzira amene akudzayamba kumene komanso omwe omwe akupitiliza maphunzilo awo pasukuluyi. Malingana ndi chikalata chomwe sukuluyi yatulutsa, kusinthaku… ...
Apolisi ku Kasungu apempha anthu oyendetsa galimoto kuti ' 'asayiponde fadah' komanso asayendetse atapapira bibida komanso mankhwala ozunguza bongo pofuna kuti aliyense alowe mchaka chatsopano cha 2024 ndi moyo. Yemwe ndi komishonala wa apolisi mchigawo… ...